Estiner Katengeza -Zokoma ndi Zakuyanja (Lyric video)

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 15 ก.ย. 2024
  • Declare along that goodness and mercy follow you
    Intro
    Zokoma, Zoyanja
    Zokoma, Zoyanja
    Verse 1
    (Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine) x2
    (Everything is alright)x3
    Zanga zimayenda
    (Malire a Yehova pa moyo wanga
    Anagwera pabwino)x2
    When I look to the left
    Everything is alright
    When I look to the right
    Everything is alright
    Lero langa, mawa langa
    Pansi pano ndi kumwambanso
    Changa ndi ichichi
    Yahweh Wandipatsa
    Anga ndi awawa
    Yahweh Wandipatsa
    Cholowa changa ichichi
    Yahweh Wandipatsa
    Wanga ndi uwuwu
    Yahweh Wandipatsa
    He eh, he eh
    Yahweh Wandipatsa
    He eh, he eh
    Yahweh Wandipatsa
    Verse 2
    Ntchito za manja anga
    Nzodalitsika
    Ine kulowa kwanga
    Nkodalitsika
    Olo kutuluka kwanga
    Nkodalitsika
    Ah he eh eh
    Zanga zimayenda
    Ndikakhala pa nyumba
    Zanga zimayenda
    Ndikayenda kwao kwa azungu
    Zanga zimayenda
    Ngakhale kwathu kuno ku Malawi
    Zanga zimayenda
    Zanga ndi izizi
    Yahweh Wandipatsa
    Anga ndi awawa
    Yahweh Wandipatsa
    Cholowa changa ichichi
    Yahweh Wandipatsa
    Umboni wanga uwuwu
    Yahweh Wandipatsa
    Verse 3
    Londo londo londo
    Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
    Londo londo londo
    Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
    When I look to the left
    Everything is alright
    When I look to the right
    Everything is alright
    Lero langa, mawa langa
    Pansi pano ndi kumwambanso
    When I look to the left
    Everything is alright
    When I look to the right
    Everything is alright
    Lero langa, mawa langa
    Pansi pano ndi kumwambanso
    Londo londo londo
    Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
    Londo londo londo
    Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
    Londo londo londo
    Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
    Londo londo londo londo eh!
    Zokoma ndi Zakuyanja zimanditsata ine
    Outro
    Zokoma, Zoyanja
    Londo londo, kunditsata
    Zokoma, Zoyanja
    produced by OBK Beatz

ความคิดเห็น • 35

  • @aichungboi..
    @aichungboi.. 8 หลายเดือนก่อน +1

    A good song for generations to come😊❤

  • @ovilhelha
    @ovilhelha 3 หลายเดือนก่อน

    I have a very powerful testimony. God changed my story in the same week this song was on repeat on my playlist. Love you your music Estiner. God bless you and as the songs says zokoma ndi zakuyanja zizikusata in all the days of your life.

  • @mphatsogondwe1836
    @mphatsogondwe1836 ปีที่แล้ว

    Beautiful mam, yes indeed zokoma ndizakuyanja zimandisata coz when i look back my life i have been through alot, i dont mean i'm rich no but the life i have i dont take it forgranted, nyimbo iyi imandisuntha kwambiri ndikundilimbikitsa pa moyo wanga wauzimu, this is Queen Gondwe from Lilongwe

  • @trinitykamgwawochaweza
    @trinitykamgwawochaweza 6 หลายเดือนก่อน

    Nyimbo mwayikwapula Asisi, Ambuye apitilize kukudalitsani

  • @anitamlauzi6037
    @anitamlauzi6037 2 หลายเดือนก่อน

    Zokoma ndi zakuyanja! Such a beautiful piece ❤

  • @EmmanuelChunga-sd3un
    @EmmanuelChunga-sd3un 6 หลายเดือนก่อน

    Zokoma zikuyayanja , ndi zikupitirabe kutiyanja !

  • @LloydLuwis
    @LloydLuwis หลายเดือนก่อน

    Keep it up 🎉

  • @chekie458
    @chekie458 5 หลายเดือนก่อน

    Yaa loving this one❤❤

  • @chisomothonje1245
    @chisomothonje1245 8 หลายเดือนก่อน

    Powerful song🔥🔥🔥🔥🔥

  • @toweranyirenda3833
    @toweranyirenda3833 11 หลายเดือนก่อน

    The voice....superb!!

  • @WezzieGondweHara-kd6ho
    @WezzieGondweHara-kd6ho 11 หลายเดือนก่อน

    Zoona zokoma ndi zakuyanja Yahweh wandipasa

  • @nelliemakanjira3932
    @nelliemakanjira3932 6 หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤ beautiful piece 😍

  • @MoreenBanda-hy6qb
    @MoreenBanda-hy6qb 9 หลายเดือนก่อน

    My favorite song, zokoma ndizakuyanja zimatitsata

  • @KwamecMnthali
    @KwamecMnthali 2 หลายเดือนก่อน

    Londolondo kundisata ndithu( zokoma , zoyanja)❤

  • @promisepachanyamwafulirwa3051
    @promisepachanyamwafulirwa3051 8 หลายเดือนก่อน +3

    How can I like this a million times? 🔥🔥🔥 This song is deep! Thank you for this one.

  • @tisunganechilale3653
    @tisunganechilale3653 7 หลายเดือนก่อน +1

    🎉🎉🎉🎉🇲🇼

  • @ianmwalungila5423
    @ianmwalungila5423 ปีที่แล้ว

    Powerful

  • @brenmwanza
    @brenmwanza ปีที่แล้ว

    zokoma ndi zakuyanja 🔥

  • @user-zk9zw7uf1y
    @user-zk9zw7uf1y 6 หลายเดือนก่อน

    My favorite song

  • @suemchekeya8501
    @suemchekeya8501 8 หลายเดือนก่อน

    my favorite😍

  • @therealshamie
    @therealshamie ปีที่แล้ว +3

    Zokoma ndi zakuyanja🔥🔥Lord our portion and inheritance 🙌 🇲🇼

  • @SerahMoyo-wk4lm
    @SerahMoyo-wk4lm 6 หลายเดือนก่อน

    Beautiful

  • @tiwongeluhana9272
    @tiwongeluhana9272 ปีที่แล้ว +2

    Nane zokoma ndi zakuyanja zimanditsatanso psalm 23 🙏

  • @ELIJAHWILLARD-pw3bk
    @ELIJAHWILLARD-pw3bk 5 หลายเดือนก่อน

    Amen

  • @CarolMwangomba
    @CarolMwangomba 4 หลายเดือนก่อน

    Munamenya nyimboyi mama

  • @harveychisambo9513
    @harveychisambo9513 6 หลายเดือนก่อน

    Zongofunika kuleza

  • @lezlinamtumodzi5635
    @lezlinamtumodzi5635 ปีที่แล้ว +2

    ❤️💯🔥 this is a beautiful song ❤️❤️ ilove it

  • @patricknyirenda2369
    @patricknyirenda2369 ปีที่แล้ว +1

    This is powerful💥. There is anointing in the song. Estiner, keep it up. You are a blessing.

  • @mervimissolo3430
    @mervimissolo3430 6 หลายเดือนก่อน

  • @alicechigamba1751
    @alicechigamba1751 ปีที่แล้ว

    ❤I love this song estina nyimbo imandisuntha mtima wanga iyi mmmmmmmmmmmmmmmmm
    Ambuye mulemekezeke

  • @joneskwangwani3142
    @joneskwangwani3142 ปีที่แล้ว +1

    this song is powerful

  • @cembuchie2953
    @cembuchie2953 ปีที่แล้ว +1

    Zili bwino kwabasi

  • @monicanamonde7231
    @monicanamonde7231 ปีที่แล้ว

    My favourite artist

  • @beatricegovati4656
    @beatricegovati4656 ปีที่แล้ว

    🔥 🔥 🔥 ❤

  • @danielmwakasoko3647
    @danielmwakasoko3647 ปีที่แล้ว +1

    Powerful