Nep man filadefia....wabwera bwino kwambiri mudyangu big up Rasta.....watching from miles away from home en u alwez take as back to Malawi thanks....Flora Suya en the Team
My best actor today was music man when he said " "mwadzilakwira nokha mudzikhululikire" I laughed like a baby. Greetings from North London UK 😂that was hilarious
Nep man filadefia....wabwera bwino kwambiri mudyangu big up Rasta.....watching from miles away from home en u alwez take as back to Malawi thanks....Flora Suya en the Team
Fireeee mabomba
💥💥💥💥💥
Mukutimvetsatu kukoma Guys ❤❤❤❤❤❤❤
Keep it up.
Nepman mwaonetsa Mtima wa Utsogoleri lero zikomo kwambiri mwapereka Malangizo abwino kwa aliyense
Watching from cape town Nepman wabweratu ngati coming❤😂😂
koma eeh🔥 😂😂Nepman next aimbe ng'oma avine azimayi oyembekezela asalawo achina (Eunice) ndi wina oyamwisa (Queen) awaimbile yambwiza ng'oma avine 😂😂
Mdyangu comedy you're the best , i like your combination . Queen 👑 congratulations for giving birth to a baby girl 😂😂😂😂😂 .
I start with commenting b4 watching coz I already know it will b a nice comedy
My best actor today was music man when he said " "mwadzilakwira nokha mudzikhululikire" I laughed like a baby. Greetings from North London UK 😂that was hilarious
Zilibwino guys watching from Botswana
Guys mumakwana 🎉🎉🎉🎉 Koma Queen ndi Mayi chokochoko 🔥🔥🔥🔥
Queen umandisangalasa nsaname sumalabada zmwe amakuchita mai shokoshoko
Wow nice mayi shokoshoko phwawo wasanduka mkazi zawo 😂😂😂😂😂😂😂😂
Munyanyiwa wamabodza kulikonse kkkkk,kuja umati ndiwe mfumu
Nep filadefiya nyimbo sewero zonse mumatha🔥🔥🔥🔥🔥💕
I like it
Kikkkkkkkkk tiye kwanthu sipaziko ,usamuke bas ,,, mr chipwanya mwavara burauzi ya bho
Thanks @Flora Suya for listening 🎧 to your viewers opinion tinabwela ndi dandaulo kuti comedy ikamayamba mmationetsa zambili zomwe timaonela kale sabata lapitalo ndipo tinapempha kuti muonepo zikomo kwambili potimvela zasintha ndithu siziliso mwakale ayi #tag mdyangu #tag mfumukazi ulemu wanu guys
Koma chizungu chimayankhula sasoka😂😂😂😂😂😂😂
❤❤❤❤❤❤ I can't wait to see next episode
Ifetu nkhawa zonse balala chifukwa chainu❤❤❤❤❤
Azabeleka njomvu😂😂😂
nafilldephia ....love you broo more fire
A queen matama ,mwayamba asisi kukuwa ,usiye mwano mphwanga😂😂😂😂
Nepman iweyo sunabadwe unangogwa kumwamba....kkkkkkkk umakwana....ati mumbva m'bebe😂😂😂😂😂
😂😂😂komatu ka munyanyiwa sikakalamba bwino
Gani ndi mdyangu ndi okhaokha agalu😂😂😂
China ndi China munyanyiwa ndi nepman nso akufunika award😂😂😂😂😂😂😂
You guys you kill me with 😂😂😂😂😂😂
Koma munyanyiwa kose kumene umapanga sewero umandi pangisa kupita kwa musanga nthawi kkkkkkkkk🙏❤️❤️
Nice one mwapha
Kkkkkkkkkk km achinyakise kkkkk mariheso paliponse kkkkkkkkkkkk km dzipongwetu kkkkkkk
more fire man nep 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
More fire 🔥
Mmmmm 😂😂😂 kma guyz ili umu ndiantopola ..... Ati yafika Kuma finals.
You killed this one guys😂😂
Guys mwayamba kuchepetsa ma minutes bwanji.
😂😂😂😂 koma may mudyangu 😂😂😂😂
Ine tinkhunda tiwiri timayenda pa mpanda tija timandiwaza heavy 😂
congratulations Queen baby girl
Munyanyiwa matama😅😅😅
Munhanhiwa wayichochatu😂😂😂
Kkkkkkk Queen mwandisekesa 😂😂
Ngakhale yatipeza 12:00 tionelabe❤❤❤😂😂
Kkkkk Nepman ndikatundu I can't wait 😂😂😂
Nepman wabwera ndi moto🔥🔥
Munyanyiwa paliponse boza nakuzitama. Kuluku
Nepman we love you in this comedy don't leave us
Calling all the children 😂😂😂😂😂
Mwina abeleka Njovu😂😂😂
Munyanyiwa alindi matama, me wonetseni 😂😂😂
Km Nepman ati nchani uku wapita uku wapita 😂😂
Kkkk waposatu mulelemba
My favourite sasoka n chipwanya ❤❤❤
Mudzi wadyangu ngokoma kobasi😂😂
Nep man umakwana wayakisa fire😂
Ndikawawa mdyangu
😂😂😂 guys mmenyeni munyanyiwayo
Zilibwino mumaitha mumatichosa khawa❤
chifundo ALBINO ZEMBELE love you
Nepman ati ndiokhaokha anthu ake ndi agalu😂😂😂😂
Kkkķ munyanyiwa zina umangowona waziyamba😂
Music anakagwila sister wake😂😂
Komatu sasoka ati watalikila nepia kumwa mkaka unafika utaola
Sending love
Music sumunthu yamaseweretsa idyayo😂😂😂
❤❤mumakwana guys
Zabwno zikubwerabe 🎉🎉🎉🎉 onjezelani maminints akuchepa gys 😢😢😢😢
Komatu munyanyiwa mabodza eshi😂
Mayina mdyangu ngamwano dzedi
😂😂😂😂 nganga yo
I love you guys
Koma ndiye mwapasa Moto nepman umakwanira
Kkkk am back my people 🔥🔥🔥🔥
Mimba zikanali mimba simunachirebe eeeeeeee
Love ❤️ u gyz timakunyadirani kwambiri
Kkkk😂😂😂 munyanyiwa washosha mavu kkkk
Mumatives kukoma ❤❤
Km gani akazi awiri nde unu nep man . bwanji poti ndi mkuluwake wagani
❤❤❤❤ mumatha mai shokoshoko
I like when sasoka called nepman music 😂😂😂
😂😂😂sasoka anabwela ase kkkkkk akt iwe music😂😂😂
Koma kwa mdyangu Kuli gulu
Zomwe timadikira😅
eish mimba ya Queen yikukula mochitisamantha bwanji🤔
Muli unthenga umu🤣🤣🤣🤣🤣
Nep man wabwera kuzakhala 😂😂😂
Munyanyuwa😂😂😂
Mai shokoshoko inuyo ndi 1
Km khwini mwano chepetsaniko kwaliyese
Koma yah
NEPMAN AMAKWANIRA KOMA 😂😂😂
Agalu okha okha😂
Huuuuuu gagayu kkkkkkkkkk salibwinodi
Munyanyiwa ndi dolo
Koma masiku akumachuluka otululitsila firm guy's
Nepman fire😂
Sasoka wakumana nazo
😂😂😂😂🎉A music
Anthu inu mumandimvetsa kukoma😂
Aaàaa yathera mmalere lero😮😮
🤣🤣🤣🤣🤣🤣😂😂😂😂😂😂❤️❤️❤️❤️❤️
Queen ali ndi baby girl wina akuti ndi Njovu. Eeeeeee
Nep kkkk