Koditu anthu akumpoto ine mnanena kale iziii 😢😢😢anthuwa mulungu sangalore choipa chiwachitikire no president amene angaime pachulu mkumati ine mnaganizira anthuwa nono😮😢😢tinazolowera basi ife bola mulungu akutisunga😢😢
We are in a neo-colonial era. Africans colonizing Africans But change is in process. Redemption is not coming from greedy politicians; but from patriotic Malawians who hate corruption.
ndipo Malawi 😢.... tafika pomayenda ndi convoy ma allowance bweee a anthu omwe a Vice president akuyenda nawo kumakaphika zibwente , anthu ena akufuna the same amount kuti angodya chabwino olo kamodzi patsiku zoona?
Bomali lakanika zoti alibe current zamaboza izi dziko likudandaula kuti kulibe ndalama komanso nduna za boma zili busy kumagula ma bus komanso kumanga manyumba mosasamala kuti amalawife tikudusa njira zotani, komanso nkhani ya zisankho zomwe zachitika ku Mozambique it will happen 2025 cz za smartmatic izi it's not the way to go
Koma anyamata inu mungovutika ndi kutuluka thukuta kukambirana zimenezo, ine ndinakuwuzani kuti dziko la Malawi, anthu andale ndi ogwira ntchito za boma ndi amene amalitenga dziko lija kuti ndi lawo, kaya ndi olamura kaya ndi osusa onse aja muwatenge kuti ndi chomozi-mozi, inuyo ngakhale mutawadandaulira chotani palibe chimene angachite chifukwa ndi anthu opanda chisoni, ma service aboma inuyo popanda kukapereka ziphuphu sangakufikireni, ubeale uzachitika nthawi ya campaign basi, ndipo musalembese kuti mukavote asiyeni azapite okha.
Msewu nyika national park hewe mpaka pano kulibe koma nthawi ya compan adzanena Kuti tifuna kukonza kuyamba kare kare mpaka pano kulibe kaya tsopano azanena mwamtundu wanji tizamvetso kkkkkkk ndimamva Ndi makutu angawa Ndipo tamvapo koma pano kaya...
Times TV ndi anyamata awo a HOT CURRENT ndi Opposition Party. TTV Party! Panopa afika poposa a DPP. Journalism sakuitha. I wonder kuti Management ya Times imalora zimenezi bwanji? Angopanga register chipani
Koditu anthu akumpoto ine mnanena kale iziii 😢😢😢anthuwa mulungu sangalore choipa chiwachitikire no president amene angaime pachulu mkumati ine mnaganizira anthuwa nono😮😢😢tinazolowera basi ife bola mulungu akutisunga😢😢
Watching from south Africa Cape town but from mzuzu you guy's you always do the best
Is it possible for journalists to rule the country?? You guys can be good leaders if you put action in what you say.
Macbride Nkhalamba president then ma journalist kukhala ma minister Nkumapanga zomwe amanenazi ndekuti basi we can see Singapore uja ku Malawi kuno
Zelensky of Ukraine is an example of such leaders
Komatu ansukuluziwo mumawapondereza chifukwa mumawapatsa nthawi yochepa kuyakhura and mumawadula chifukwa ninji???
Watching from Blantyre Malawi, you are the best journalist
Kodi ndalama ya ma tollgate zikugwila ntchito yanji ine ndikufuna amabugwe alakhule kapena sakuona inu a CB mulikuti Kodi balizomwe inu mumakonza zilibwinobwino mwafatsatu ayi zikomo ife tilibe
Timakunyadirani guys keep it up powayankhulira a malawi
Watching from Johannesburg in south Africa but from machinga we support you guys all the best
Ndikumva dpp pansipasi
Watching from bononi Johannesburg bt from dunduzu malawi ❤you guys
Iñu mumayakhula zanzelu but point tikuvutika Ife
We are in a neo-colonial era. Africans colonizing Africans But change is in process. Redemption is not coming from greedy politicians; but from patriotic Malawians who hate corruption.
Always love watching you guys you are second to none
Watching from Ressano Garcia Mocambique
Mukunama vuto la malawi ndi tulo chakwera ndi banja lake walemera mukuona shame malawi
ndipo Malawi 😢.... tafika pomayenda ndi convoy ma allowance bweee a anthu omwe a Vice president akuyenda nawo kumakaphika zibwente , anthu ena akufuna the same amount kuti angodya chabwino olo kamodzi patsiku zoona?
Kuba kopanda nako manyazi basi,dziko lomvetsa chisoni nkhani ndi atsogoleri
Malawi singasithe unless kuzachitike khondo, ndiye anthu tizasithe kaganizidwe
Anyamatanu mumatha kumbali yanu, koma vuto ndi akapondo andalewo onse palibenso wabwino, ophunzira amadigiri, dipromer koma akuba kwambiri! Muntu wakuda kwake ndikuba basi.Ndikanakonda dzikolo libwerere kwa atsamunda.
Keep going ...
Good job guys,osiyiwala nkhani ya anthu amene anachotsedwa mumastate residence
bingu yekha amene anali tate samafuna zopepha kapena kuvomeleza zopusa
Guys
I have come to realise that those are not potholes but fish ponds and swimming pools that our governments have planted on our roads
Opusa ndife amalawi....
Its stupid to believe that a politician will transform malawi...only the military can save us
Msewu wa Tsangano ku Ntchewu watha zaka 11 kumanga 11 kilometres basi
Bomali lakanika zoti alibe current zamaboza izi dziko likudandaula kuti kulibe ndalama komanso nduna za boma zili busy kumagula ma bus komanso kumanga manyumba mosasamala kuti amalawife tikudusa njira zotani, komanso nkhani ya zisankho zomwe zachitika ku Mozambique it will happen 2025 cz za smartmatic izi it's not the way to go
You guys, mumakamba chilungamo
Koma anyamata inu mungovutika ndi kutuluka thukuta kukambirana zimenezo, ine ndinakuwuzani kuti dziko la Malawi, anthu andale ndi ogwira ntchito za boma ndi amene amalitenga dziko lija kuti ndi lawo, kaya ndi olamura kaya ndi osusa onse aja muwatenge kuti ndi chomozi-mozi, inuyo ngakhale mutawadandaulira chotani palibe chimene angachite chifukwa ndi anthu opanda chisoni, ma service aboma inuyo popanda kukapereka ziphuphu sangakufikireni, ubeale uzachitika nthawi ya campaign basi, ndipo musalembese kuti mukavote asiyeni azapite okha.
ndiye amsisya nkhwenda viwi ndiye abare angatu mwandisangarasatu Koma ndevu zamwayi 😂😂😂😂
A wonder Msiska,mwayiwala eti?Ndi Chakwera delivery.Boma ndi lomweli
Pajatu chitukuko Chakwera ndi ku Lilongwe basi
Malawians must change some bad roots of our culture national wide.
ulemu wanu azibambo osamba oyanjana ndi madzi pitilizani ku ng,alula basi
Anyamata awawa amapeleka malangizo aulele koma nkhutu kumve kuboma uku zosayenda kuboma uku kukufunika complete overhore
Kungoti azitsogoleriwa akungokomedwa ndimisokho ya amalawi m'malo moti athandizile wanthu mudziko
Guys M5 from Dwangwa to Salima mavuto ndipo ngati tilibe atsogoleri
Matsiku otsiliza anthu azakhala ozikonda okha ,okonda chuma osalabadira anzawo. Azitsogoleli athu aphunzilepo kanthu akukhala ngati mbuli zosapita ku school kapena ku church osaopa mulungu. Akuiwala kuti chuma ndi Michigan wa buluzi chimatha ngati makatani. Za dziko lapansi ndi zakutha izi .
Anyamata awa akung'alula
Ndinu maso komanso mulomo wa dziko , keep it up guys
Nkhope ya Chithyola yikuoneka yakuba kale kkkk
Kodi magayz awa akamalankhula mbuzi zolamulazi zimanva koma?
Ndizoona zamsewu wachiweta sulibwino or pang, ono madriver akumachita kuimakaye kusankha poponda , ukapachila nkhawa biiiii
Ndipo kwavuta ku malawi akuti tizipereka mupaka ma ld zoona a mcp ku matitengera akuti tikupasani chimanga zoona
Bolani lapano koma limene linachoka 10 year nothing komalero tikubulema boma ili tiye ni nazo
Watching from nkhotakota
Auzeni agaru a ndale .kodi tolgate blantyre lilongwe apangapo chani
Balaka road mabvuto kwabasi
Msewu nyika national park hewe mpaka pano kulibe koma nthawi ya compan adzanena Kuti tifuna kukonza kuyamba kare kare mpaka pano kulibe kaya tsopano azanena mwamtundu wanji tizamvetso kkkkkkk ndimamva Ndi makutu angawa Ndipo tamvapo koma pano kaya...
Akabwera nafeso tizango genda
Feedback or background voice
We will die trying am with you,mseu wa karonga kuçokera ene ndingot kasungu ai ndima potholes komaso ndikakang'ono that's why kumakhala ngozi kawiri
Komaso anyamata awa mmm pali kenakake chifukwa msewu wakaronga ukukonzedwa koma sanamalize koma amaliza
Sizingatheke dziko kuyenda bwino atakhala kuti mtolankhani ndi mtsogoleri wadziko aChakwera adayesera kuwatenga awiri awa; Brian Banda ndi Gospel Kazako akuluakulu amawayilesi odziwika adalephera ndipo atawachotsa adayamba kumakamba zoyipa zokhazokha za boma chifukwa cha manyazì makamaka Brian ndiyesa ankakanika adakwiya
Wanthu awo wakuvota wakukhala kumuzi sonu ivyo imwe mkuyooya palivi icho iwo wakupulikapo ndicho ntchifukwa chakhe wakusekulera ndachilichose kwali ndisalu kwali ndichipewa kwali ndi Tshirt mukavu alive chisankhu
Gotan . Zikhare . Ajacob Hara tapangani zanseu wachiweta pls
Nde akumveraso msonkhano wa DPP bwanji kkkkkkk😂😂😂😂😂
Times TV ndi anyamata awo a HOT CURRENT ndi Opposition Party. TTV Party!
Panopa afika poposa a DPP. Journalism sakuitha. I wonder kuti Management ya Times imalora zimenezi bwanji?
Angopanga register chipani
Ndinu achitsiru
Iwe umaziwa chani za ndare😅
Seu wachiweta ndi manyaka aseu wonder ukunena zoona
Kumalawi nkuvuta chinyengo palipose
Pansipo ndikungonva kt a Peter woye
Yaaa
ife tilibe loya
Mkapempha mzatsitse fertilizer bas kupempha kwatha
Wawa macadet apawayilesi
Aaaaaah inu muli mbuuuuu
Chifukwa ndikwanu zopusa chakwera akukoza misewu yose
Mmakwana mabwana
Kugula yake yomwe kkkk
Mobutu was a journa 0:28 list before he he joined Zaire Army by then
Pathako panu ma cadet mboli zanu
Galu opindika msana iwe... Mbuli yamunthu nyawu wachabechabe
Ndizoona zamsewu wachiweta sulibwino or pang, ono madriver akumachita kuimakaye kusankha poponda , ukapachila nkhawa biiiii