Prophet Austin Liabunya: Chimene Chinapha a Chilima Cheni Cheni - Malawi Latest Prophecy (part 1)

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024
  • Izi ndi zomwe anayankhula #ProphetAustinLiabunya:
    -Chimene Chinapha Dr Chilima
    -Explaining My Journey With Dr Chilima
    -Mulungu Akuti Chani Pa Tsogolo La Malawi
    -Zimene Mulungu Akufuna Dr Laz Achite Kuti Atengenso Boma Mu 2025
    -Umboni Wanga Pa Mphekesera Za Kumangidwa.
    -Ndi Nkhani Zina Zambiri..

ความคิดเห็น • 51

  • @BenNkhoma
    @BenNkhoma หลายเดือนก่อน +3

    PALI NGOZI YAIKULU, KUSIYA ZA YESU KUYAMBA KUTUMIKILA ZA NDALE,

  • @RUSTOYOTA-k3d
    @RUSTOYOTA-k3d หลายเดือนก่อน +2

    Only God knows,may the souls of our beloved ones rest in peace

  • @GiftShugah
    @GiftShugah หลายเดือนก่อน +3

    Mulungu akukhululukireni Man

  • @Aqiec09
    @Aqiec09 2 วันที่ผ่านมา

    Za ziii ngati pali cha nzeru chamvekapo kumangobwereza

  • @user-tj1ms3bg3x
    @user-tj1ms3bg3x 24 วันที่ผ่านมา

    Heey man of God; U may preach a million times.
    Nothing will b gained
    But what I know of my God that I save is that ;;; THE BUTTLE IS HIS...... Ngati chinthuchi anachivomeredza kuti chichitike; mwina wake yekhayo ndamene atachimalidzenso since he has all the powers for revenge.
    Mean time it's not over .....untill it's over.
    Let's all pray for his soul to rest in eternal peace.
    For we all ...... Shall head to the same direction .
    No matter what....
    Pangatalike mwazi wa munthu supita paulele...
    With God ; the truth shall always prevail.

  • @user-rk3jx3kg8i
    @user-rk3jx3kg8i หลายเดือนก่อน +1

    Mbuzi ya munthu, mulungu wasala pangono kt akutopele,

  • @WilfredKalirani
    @WilfredKalirani 15 วันที่ผ่านมา

    U pulofeti Wafika popereka chikaikiro pa banja anthu a Mulungu. Zimafika pochititsa manyazi ndi unfulfilled prophecies. Chonde tisayankhule maganizo athu. Tidikire Mulungu atiuze zoyankhula.

  • @user-eu5wo5kt9u
    @user-eu5wo5kt9u หลายเดือนก่อน +1

    Mulungu adzachilangaichi

  • @MaryMlongoti
    @MaryMlongoti หลายเดือนก่อน +2

    Chilima sanaphedwe thaw unamukwanila

  • @Sheillamponda
    @Sheillamponda หลายเดือนก่อน

    Ok prophert of God

  • @TuntufyeKalambo
    @TuntufyeKalambo 8 วันที่ผ่านมา

    Mr prophet sir my quation is do you mean that tonse alliance ndiyomwe yapha a presdent ? Komanso tonse alliance ili ndi msogoleri so man of God be specific and let us know the other thing is amos 3:7 the bible tells us kut God does not do anyrhing unless he reveals to his prophet nkw God reviewed it to you why disbt you go abd meet him to the appointed time he gave you because thats a presdential office you cant just go at anytime you want thats why anakukanizan and give you the date to come and you wanted the vice presdrnt to follow you to your house just because God has reviewed to you ? Ok look at the old prophets in the bible they could go to the king and tell the king that danger is coming and maybe when the king want to meet tge prophet he calls for him to the palace so man of God tifotokozeleni bwino bwino i dont understand ineyo whats happening kwen kwen

  • @michealmzumara8471
    @michealmzumara8471 หลายเดือนก่อน

    Ndiopenga akufunika mankwala

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili หลายเดือนก่อน +1

    Koma ngati ndizedidi zimene mukuka.bazo kt mudapanga prophesy kt atuluke Avice president mu tose alliance ndiye kt mudolosera chifukwatu adadfa imfa yowawako.aso yosaiwalika

  • @LonjezoAkacharlie-r2q
    @LonjezoAkacharlie-r2q หลายเดือนก่อน

    Tayankhula zomveka iwe ukuti chani kwenikweni

  • @Jeremiahchalombanthu
    @Jeremiahchalombanthu หลายเดือนก่อน +1

    Kod mulungu wake ndi wa major 1 kod panopa mulungu amangonena zandale

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr หลายเดือนก่อน

    Tizikasaka ma Post amiyezi imeneyo, koma tigwira ntchito?

    • @EliasApofu
      @EliasApofu หลายเดือนก่อน

      😂😂😂

    • @MeniaMikaya
      @MeniaMikaya 14 วันที่ผ่านมา

      🤣🤣🤣🤣

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 หลายเดือนก่อน +1

    It seems like this MAN don’t know what he is saying. “Everything is I think “

    • @philemontitusnkhoma7740
      @philemontitusnkhoma7740 หลายเดือนก่อน

      Yea, I also noted that. U know the reason? Here, the repeated use of 'I think' is due to his reluctance in mid speach to divulge what he realy knows. So he is trying to remain calm, careful, and at the same time, inoffensive.

  • @PeopleOfYah
    @PeopleOfYah 29 วันที่ผ่านมา

    Milungu ndi yambiri. Ina imamuwuzadi munthu zimene akunenazi. Pajatu satana ndi mulungunso wa dziko lino.
    Mulungu wathu satenga mbali mu ufumu uwu wa kumapazi kapene kuti ufumu wa chilombo chopanda dzina

  • @GiftChitsulo
    @GiftChitsulo หลายเดือนก่อน

    Iwe ASE usamasewele ndimulungu mulungu si abambo ako chonde chonde usamana ize anthu kuzela kwamulungu musiyeni mulungu akhale mulungu ,,,,tchito zaboma zimafanana ndindale ngati wasata zaziko wasephana ndimulungu man musatichimwise,,Kodi mulungu akuuze iwe ndindani iwe baibulo lake liti

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma หลายเดือนก่อน

    Koma zoti chilima wachita kuphedwa ndi chakwera simukunena bwanji

  • @innocentmanyamba5042
    @innocentmanyamba5042 หลายเดือนก่อน

    Kape uyu osauka akuona ngati atola chikwama oputsa uyu

  • @EliasApofu
    @EliasApofu หลายเดือนก่อน

    😮

  • @lulukunkeyanih8271
    @lulukunkeyanih8271 28 วันที่ผ่านมา

    Komatu iwe

  • @ABMWALEBorder
    @ABMWALEBorder หลายเดือนก่อน

    Komano ineyo zomwe mukufuna kunena, sindikuvetsa kuti mufuna kunena kuti chani.

  • @ClifordBwwanali
    @ClifordBwwanali หลายเดือนก่อน +1

    Now you stop preaching jesus .everyday stories we arw tired

  • @Deborah-b3k
    @Deborah-b3k 8 วันที่ผ่านมา

    Musamunyoze munthu,vuto anthuni simuwelenga Bible just go and read the Bible Deuteronomy 18 v22 kti mudziwe what God really says about prophets mudzango nyodzapo otumidwa ndi Mulungu be careful!!

  • @PaulNtonya
    @PaulNtonya หลายเดือนก่อน

    Ndikufuseni mukutumikila utitiuti Mulungu wake 🤔

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg หลายเดือนก่อน

    Chilima penapake anali wamwano born kalindo wakhala akunena

  • @yowasschitsosa5348
    @yowasschitsosa5348 24 วันที่ผ่านมา

    A prophet ndnu andale kapena muchita zamulungu kkkkkk zamanyazi a prophet mwasiya zamulungu mwayamba za ndale

  • @CharlesKalua
    @CharlesKalua หลายเดือนก่อน

    I saw your prophecy they is no that condition pliz and you say it with confidence that chilima Will be a president,,chonde venselani kwa mulungu osalankhala za mumaganizo anu

    • @user-ql8sj4jj3y
      @user-ql8sj4jj3y 3 วันที่ผ่านมา

      I doesnt matter kuti anayskhula with confidence koma ngati mwini uthengawo is stubon wonsanvela it goes like this

  • @scoltenroma6240
    @scoltenroma6240 หลายเดือนก่อน

    False Prophet in the last days,repent & turn to God.Kufuna kutchuka eti,tisiyeni tikulira maliro ife.SKC RIP😭

  • @user-ye7fv4yo9f
    @user-ye7fv4yo9f หลายเดือนก่อน

    Aaaaaa

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q หลายเดือนก่อน +1

    YOU DON'T KNOW WHAT YOU PREACHING.
    DZIKOMO MULUNGU MWANDIONESA ANENELI ONYENGA.

  • @alicelukiyo9265
    @alicelukiyo9265 23 วันที่ผ่านมา

    Koma AMBUYE ATITHANDIZE NDITHU MMM GOD SENT YOU TO DELIVER THE MESSAGE YET YOU DD NOT WANT TO GO AND MEET HIM WHILST WHEN GOD SENT ISAIAH TO DELIVER THE MESSAGE TO HEZEKIA OF WHICH HE DD IT HE DD NOT SEND ANYONE BUT HE HIMSELF WENT AND DELIVER THE MESSAGE I DONT THINK HEZEKIA COULD HV ALIVE MULUNGU ANAKUTUMANI INU SIMUNAPANGE ZOMWE MULUNGU ANAKUUZANI MWAZI WAO ULI PAINU HE CALD U TO MEET HIM KOMA INUSO MUNAFUNA KUONATSA UKULU WANU POSAPITA POFUNA IYE AKUENDERENI SO IN MY OWN OPINION MUNALAKWITSA M NOT JUDGING YOU MAN OF GOD KOMANSO MOPEMPHA MUKALANDILA MA MESSAGE AANTHU ANDALE SIZINGATHEKE KUTI MUDZINGOWAUZA ALIESE PAEKHA PAEKHA NDIMAONA KUT ONLY PIPO WITH STATUS NDIOMWE MA PROPHECY AWO AMABWERA APA OSATI ANTHU OPANDA MAINA. KOMA ITS BAD PAMENE ACHIBALE AKULILA ADZIMVA MA UTHENGA OPWETEKA LIK THIS ONE KUTI ANACHITA KUSAMVERA ZILIBE PHINDU PANO ONLY GOD CAN JUDGE

  • @masautoMalunga
    @masautoMalunga หลายเดือนก่อน

    Is good to look something to do not to lies to the people that your poster Kodi ubusa wanji ongokamba zandale

  • @peterkampira7613
    @peterkampira7613 หลายเดือนก่อน

    Your are operating under the power of money

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde หลายเดือนก่อน

    🙄

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q หลายเดือนก่อน

    Achibale a munthu uyu chonde mutengereni ku mental hospital.
    Am crc.

  • @johnmsona8845
    @johnmsona8845 หลายเดือนก่อน

    Kodi satana uyu. Ndindani siyeni chilima mzimu wake uuse muntendele

  • @GabNice-rp8mt
    @GabNice-rp8mt หลายเดือนก่อน

    Vomelezani kuti mwaphonya prophecy,false prophet exposed in false prophecy.

  • @user-jm8kw9gw2d
    @user-jm8kw9gw2d หลายเดือนก่อน

    Sir you don't know how to communicate or deliver, God is not using you because we can't get you at any point

  • @masautoMalunga
    @masautoMalunga หลายเดือนก่อน

    Most of poster they busy to lies

  • @GreyKwenje-td2uy
    @GreyKwenje-td2uy หลายเดือนก่อน

    He is not a man of God manof chakwera

  • @madalitsokalima8533
    @madalitsokalima8533 หลายเดือนก่อน

    Musakambe ngati Mulungu ndi brother wanu, that accident was very painful to everyone get something to get famous with, what you are saying is just nonsense remember this CHILIKWANZAKO CHIGWIRE NYANGA you will remember this proverb , Mark my words. Musagwiritse ntchito dzina la Mulungu pachabe.

    • @jamesjanuary5423
      @jamesjanuary5423 หลายเดือนก่อน

      Aaaa kaya mwina enanu mukumva ine ndepalibe nditolaine