Honor to Mr President Doctor Lazarus MCathy Chakwera I this case I would like to appreciate the idea of His excellency Dr Lazarous Chakwera for he has really shown spirit of Humbleness and honor the rights of Malawians citizens for they are seeking for the truth of what causes the plane crush which killed late vice president Dr SKC and 9 others on board For He has allowed and support the ideas of many Malawians to have this commission of inquiry So this is so Good Mr President Really appreciate 🙏🏻
Anayeneranso ena kuchokera kuzipani monga UTM. Sanayenerenso kutenganso wa nsembe wa mtundu wa a chewa ayi. Izi angoopa ma demo basi. Akumabanja anayenera akhalemo kuti aziona chilunga chikuchitika.
Why the president is choosing what or who must be involved in the committee, it should have been the Malawi eni ake and all non governmental institutions, why Jabba alide out of all the pple as a chair? Awagula kale kale
Chilima anagwa ndi ndege basi may his soul rest in peace Ngati anaphedwa anaphedwa ndi ndege, Kafukufuku wa nzelu ngoyamba uja azibusa amayidziwa ndege?
Mmmmm izi sizithandiza olira y anthu Ena ofunikila mulibe, Mai kaliati, Mai chilima, etc chakwera usatipusise anyway ngat si ili live PA TV mungotulusa black box bas tingopangapo mademo Chimwendo banda timumveso akuyankha Live kutiuza yemwe anamulesa kut ndege yazaza. Ndipo ngat mu bwere ndi mbwerela mutimva madzi
Anamiwa chonde ife amalawi maso athu Ali painu gwilani ntchito imeneyi motsogozedwa ndi mulungu musalole kuti chilungamo chibisike mdzina la yesu tumikilani amalawi
Ndi maganizo abwino kwambiri poika a Civil society komanso Retired Officer wa MDF izi zimathandiza kutheza zokambakakamba. Komanso time frame zakhala bwino kuikidwa kuti 2026 itsakhale ndi nkhani zochokera ku 2025. Tiifunire zabwino zonse committee imeneyi.
Boma limasaka amene ali ovuta mugulumo cholinga kuti ampatse ndalama then iyeyo poti mumakhulupilira inu muvomereze,but we will never trust them anymore till this government comes out
inu akufuna atinameze uyu Kalu wakupha uyu anthu amene anapha chilima tikuwaziwa ena ndi akunja ena ndiyamalawi omwe Ali asikali komaso chilungamo chikubwela 2025 ndi chipani China osati MCP ayi
Patatenga zaka tufuna zoona zokhazokhatu namiwa kumeneko mafuso omwe unkafusa ma press briefing ako aja ukafusenso uko apo ai tizangogawanapo malawi basi from Cape Town,, south Africa
Always acting under pressure Mr. President! Commission of enquiry not fully convinced. I discredit a Modise and a Namiwa , thus your do or die . Your reputation is at stake. My wish kuti final report lisadzakhaliridwe komanso altered.
Honor to Mr President Doctor Lazarus MCathy Chakwera
I this case I would like to appreciate the idea of His excellency Dr Lazarous Chakwera for he has really shown spirit of Humbleness and honor the rights of Malawians citizens for they are seeking for the truth of what causes the plane crush which killed late vice president Dr SKC and 9 others on board
For He has allowed and support the ideas of many Malawians to have this commission of inquiry
So this is so Good Mr President
Really appreciate 🙏🏻
Akungofuna alepherese mademo akupusitsa anthu chabe MCP simukuidziwa mwina
Zoonadi
Kma sivikuveka kd anali kut nthawi yoyesi pangengo yose
Kma nizoona anthu awa aya nkhula nthawi yaitali ndye kuyankhapo kwawo kwalelo sikoveka pati tasowekemala mayankho awo nthawi yaitali ndye tatumizaniso zithu zoveka kwamalawi
Namiwa akundigwira mtima kwambiri. Namiwa uwonetsetse coz amene wakuika kumeneko nd Mulungu kut uliuze dziko chilungamo chenichenj❤❤❤❤
Ku Malawi 🇲🇼 kulibe president ayi!!! Koma mbava ndi okupha anthu chikangawa
Km atulutse. Black box ndiyomwe ikufunika umboni uli mmenemo. Zopusa ayi osamatiputsa ife😢😢😢
No
@@DicksonGomani Black Box ndiye mwini nkhani, zoona ayibweretse poyera
Asa khe anthu ochekela zipani zonse.ma church.kubanja la ofeledwa.ndi mabungwe osiyana siyananso komanso mukhale atola nkhani amaradio osiyana siyana ndi mamfumu osiyana siyana
Yabodza imeneyo nthawi yonsei amadikira chiyani?😭😭😭😭💔💔💔
Too late it will not change anything
Ngati ili ya Fake Commission Of Inquires imeneyo Malawi ayidziwa kudzera Ku BAKILI MULUZI TV NDI Limpopo FM WITH Mtanyiwa.
Ntanyiwa wanena kale dzulo kuti akhazikitsa enquiry imeneyo chifukwa chothawa ma Demo.
Chakwera wakhazikitsa bwanji commission of enquiry koma wopha chilima niweyo usamale kwambiri
Bwenziso anaonjezelamo anthu ena ma family representatives omwe abale awo anafa pangozi ija
Zabodza izi cz it's part of campaign so tisamale kwambiri chifukwa asankha anthu ni iyeyo
I think the air which chakwera breath is mixed with weed
😂😂😂😂
@@Chancenyangulu 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 bro serious am not lying why asakha commission of inquiry amayembekeza chan weed is breathing by chakwera
😂😂😂😂😂😂
Ayiwala kuyikapo mai mary chilima pa commission of inquiry
Komaso why have they prioritise kumanga Patricia Kaliati then nkumatulutsa Commission of inquiry. Why??
Koma Dingiswayo madise akhoza kutithandiza amenewo
Muikemoso abanja komaso fr elizewo mtalika komaso timothy mtambo
Aaaa anthu amene asankhidwawo sindikuonamo chilungamo mwaiwo.
Anayeneranso ena kuchokera kuzipani monga UTM. Sanayenerenso kutenganso wa nsembe wa mtundu wa a chewa ayi. Izi angoopa ma demo basi. Akumabanja anayenera akhalemo kuti aziona chilunga chikuchitika.
Wakopakopa athu omwe wasankhawo ameneyo
Kaliati alowemo mugulumo
Koma mademo alipobe palibe kusintha coz zifukwa zopangira mademo ndizambiri
Ikhala commission yafeg sitilora chifukwa chilungamo tikuchiziwa kale
Very good Mr president zigawenga za maboza zija ziziwike amawona ngati abisala
Palibe chomwe Chitaphulepo inu izi ndikukuuzanitu
Aku banja mulibemo Aku mpingo mulibe Aku chipani mulibemo and Mr kalindo mulibe asakheso bwino
Madam chilima, brother wa chilima, mafumu aku tcheu
Wina akuopa ma demo uku
Enawo akufuna ndalama pomwe akubanja, akufuna chilungamo. iyi osayikhulupilira ayi. koma boma lidziwe kuti God he's watching you.
Why the president is choosing what or who must be involved in the committee, it should have been the Malawi eni ake and all non governmental institutions, why Jabba alide out of all the pple as a chair? Awagula kale kale
Amupatsa kale dollar ameneyo mai Chirima alowe
Mmmmm si machawitu awa mose muja zinali kuti ndipo palibe kutsika mitima koma mizimu ya anthu 8 ija kuphatikiza abiyeni ikuona chirichonse chomwe chikuchitika samalani pochita zinthu. Si lero si mawa koma tsiku lina liri mkudza limene zonse zidzatha ndipo pansi pa dza nthunthumira samalani pochita zinthu
Ayakhure chilungamo basi osati anamezo chifukwa athu akuziwa zonse zinakhalira ndiye akazakamba zaboza azainaso
Popeza Mr Comrade namiwa Ali momwem ndiye Maso athu amalawi tiyang'ana kwa iwo Mr namiwa basi
Osaopa osatopa osafooka Allah alipo
First they must find the black box before starting the investigations
Ine Kawanga Makwacha from KU pamenepa apre apanga chiganizo chabwino kwambiri kuti nkhani ifufuzidwe mwamachawi chilungamo chiyende ngati madzi.
Chilima anagwa ndi ndege basi may his soul rest in peace Ngati anaphedwa anaphedwa ndi ndege, Kafukufuku wa nzelu ngoyamba uja azibusa amayidziwa ndege?
Mmmmm izi sizithandiza olira y anthu Ena ofunikila mulibe, Mai kaliati, Mai chilima, etc chakwera usatipusise anyway ngat si ili live PA TV mungotulusa black box bas tingopangapo mademo
Chimwendo banda timumveso akuyankha
Live kutiuza yemwe anamulesa kut ndege yazaza. Ndipo ngat mu bwere ndi mbwerela mutimva madzi
iwowo apresident asankha bwanji komite yoti afufuze zirongosoka apa ndizowona koma akunama murungu simunthu
Anamiwa chonde ife amalawi maso athu Ali painu gwilani ntchito imeneyi motsogozedwa ndi mulungu musalole kuti chilungamo chibisike mdzina la yesu tumikilani amalawi
Dziko musalole bwerera izo Viva mademo basi
Akufuna ampake ndan ife tikuzwa kut ndiyeyo2 anapha
Km bwanji wachedwetsa chonchi ife chilungamo tinachiziwa kale zoti anapha
Brack book ibwere apa
Zompusa bsi commission yanji yopandamo akubanja aathu omwe anafawo kungosakha athu oti sitikuwaziwa akanatenga akubanja ose aathu omwe anamwalilawo komaso akulu akulu achipani cha utm komaso a opposition akhale nawo mu commission imeneyo osati zimenezo zaziiii kufuna kupusisa amalawi bsi tizapanga commission yathu yeniyeni tikasitha boma 2025 pano musatipusise
Ndi maganizo abwino kwambiri poika a Civil society komanso Retired Officer wa MDF izi zimathandiza kutheza zokambakakamba. Komanso time frame zakhala bwino kuikidwa kuti 2026 itsakhale ndi nkhani zochokera ku 2025. Tiifunire zabwino zonse committee imeneyi.
Osaika azipani zinazo bwanji poti nkhondoyi amathandizana anamiwa ndi amzawo
Ndiyamika Mulungu pakukhazikisidwa kwa commission imeneyi, bola anthu amenewa asagulidwe posokoneza choonadi. anthu mwasankhidwanu
Ngati simugwira ntchito ya ambuye muyembekezere chilago chosatha.
Namiwa usakhale Kuti akugula osalola Kuti upite wekha Aku banja ,Aku mpingo ,Aku chipani ndi zipani Zina atengekoso anthu
Paribe anganene true pamenepo
Ngati pali judge wa corrupt. Wokhalila milandu ndi amene akamupezayu kuti atsogolele commission of enquiry. Abale anga, musayembekezele zambiri. Mau anga mudzawakumbuka.
Tsono kafukufuku achitikabwanji popanda black box ?? Amakawi mukupusabe Kodi ?? Komabe mademo akhalepo ,chifukwa mavuto alipo ambili siandege okha .
Shabwino. Ine pheee kumastand kudikila report
😂😂😂😂
Odi ndipite mkauluke ine
Voice ngati cardinal 🎉
Palibe chilungamo Spa, family iri kuti?a utm Ali kuti, sunati chakwera Malawi akudziwa kuti unapha ndiwe,
Tisaopsyesedwe osapanga mantha tione chilungamo
Zaziii!!!!!!! Mbuzi zawathu,,,kutiveka chijuzi kumaso chofiira cholemba nambala 2.mwatitola.
Bwanji achita izi kutsatila atamumanga Kaliati?
Adzifufuza atamumasula chifukwa pamenepa Pali ?
Maganizo anga ndikuona ngat pena pake pakuchepekera amayeneraso kupasa mpata akubanja asinkhe owayimilira aliyese munthu mmodzi ngat Lowyer owapasira zotsatira
Azipani akhalemo,akubanjanso akhalemo ,winiko akhalemo amabungwewo akhalemo okwanila nt Anamiwa ndi akariwa okhao ai,even antolankhani akhalemo
Osalola ayi adikile mademo kenako ikwaya yanuyo zopusa kuona kuti sizikugwilizanaso continue mademo asathe
Boma limasaka amene ali ovuta mugulumo cholinga kuti ampatse ndalama then iyeyo poti mumakhulupilira inu muvomereze,but we will never trust them anymore till this government comes out
inu akufuna atinameze uyu Kalu wakupha uyu anthu amene anapha chilima tikuwaziwa ena ndi akunja ena ndiyamalawi omwe Ali asikali komaso chilungamo chikubwela 2025 ndi chipani China osati MCP ayi
Thawi yonseyi amadikila chani 🚮🚮🚮zikutathauza kut madandaulo ayise a Malawi tikamadandaula kut ife a Malawi tikuvutika amamva et
Kuopa mademo kumeneko, president opanda mnzeru.
Iwe umaganiza mopepera inquiry yakhazikitsidwa monga momwe anthu timafunira pano wayambapo kulubwalubwa nzeru ulibedi
Patatenga zaka tufuna zoona zokhazokhatu namiwa kumeneko mafuso omwe unkafusa ma press briefing ako aja ukafusenso uko apo ai tizangogawanapo malawi basi from Cape Town,, south Africa
Osaikapo achibare bwanji kt akhaleso
I'm happy kuti Anamiwa alimo mwina winiko akhoza kuchita manyazi pamenepo
Achita bwanji
Ayikemo inkosi ya makosi Gomani komanso akubanja a wina aliyense amene anafa pa ngozi ija otherwise ndi zopepera zeni zeni
Tikufun akubsnja ndi achipani cha UTM akhalemoso
Nthungwa ilibomala nkhata bay
Don't put your people of MCP mugulu
Too late for that.
Zambiri tinamva kale zikungofunika chilungamo chioneke omangidwa amangidwe kaya kuphedwa naonso aphedwe mmene anawwphera anzao basi
Afufuza bwanji opanda black box, akuthawa mademo omalawi osalora zopusa
Zoti ku Malawi tili ndi mtsogoleri ine ndimatsutsa koma tilindi Mbava,chigawenga,Satanism Chakwera
Nanga anafedwa aikidwemoso kut pasakhare chinyengo
Zankhala bwino multi anthu achita manyadzi
Pakanakhara mabugwe okwana ngati atatu komanso amipingo akanakhalanso okwanila kuchitira kuti anthu omwe asankhidwawa ndiochepa pathabe kukhala chiwembu kuwachitila anamiwa awa ndimaganizo anga.
Ndichifukwa chiyani sanayikemo aku Banja komanso a zipani zosusa
Ndichifukwa chani sanayikepo akubanja kwa anthu omwe anachita ngoziwo ? Akuyenela kuti atengeso banja lirilose munthu modzi chifukwa sitikufuna za chinyengo
Zikukaikisa be Kom zimafunika a takhala athu osiyansiyan
bwanji akubanja ra anthu ofedwa muikepo akuba rachirima osati mafumu ai mungawagure mafumu kuti akukonde mbava iwe
Mu Africa muno ngati muli atsogoleri ombwambwana uyuyu ndi oyamba akena kuti ombwambwana wamkulu
Watulusa dala commission of inquiry cholinga athu asiye kukamba za kaliyati
Akuopa ma demo galu ameneyu nthawi yonseyi amadikila chiani
Zaziii musiyeni mulungu ndamene akudziwa
Always acting under pressure Mr. President! Commission of enquiry not fully convinced. I discredit a Modise and a Namiwa , thus your do or die . Your reputation is at stake. My wish kuti final report lisadzakhaliridwe komanso altered.
Aaa zamanyi basi awopa mademo akubwerawo pantumbo panu nose a MCP
Apule akutilokota bs ndawi jao nambo ayi yaunami osopewa watupileo wasala tusamale
Wa utm, dpp,udf,afford, akubanja a khalemo. Apo biiii, deeeeee
Kkkkkkkkkkkk km chakwel ndigalud srs thaw yosey munalikt kuwop maden kumenek
Anthuwo achepa komaso posankhapo amaganizila kuti anthuwa athandiza nanga amabungwe enawa
Anamiwa musavomereze munthuyu Chakwerayu ndi mfiti
Nkhani yabwino mwina tipumuleko nanga tizingova zachikangawa nthawi zose
Ndukaika zoti anena chilungamo
Ndiye nanga buanj sanaikemo osusa boma kma chakwera akutitora kwambiri kma mulungu akuona chilichonse
Anakasiya akumabanja nawoso akhare ndianthu awo momwemo afufuzire rimozi
Nthawi yonseyi amatani? Ndipo wasankha anthuwa ndindani?
Wakubanja wina aliyense mulibe namiwa ngati ndi ochokera kubanja? How can we trust him
Komanotu chinyengo chilipo akubanja alimony nanga akupingo alipo komaso nanga chipani chake boma Lisa pereke masiku kwa athuwo chinaso mapasi mong brake box ayikepo aboma chifukwa chifukwa sangamayende mulibe
What about achibare