Aphungu a DPP kukunthana mu Paliyamenti|Age Bill Yavuta!!!

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 11 ก.ย. 2024
  • We are reacting and commenting on what the former MCP publicity secretary is saying about Tonse Alliance Government failure to fulfill campaign promises.. Malawi is Worse off than it was 5 years ago...he admits!!

ความคิดเห็น • 23

  • @FrancesMitengo-p2d
    @FrancesMitengo-p2d 5 หลายเดือนก่อน +1

    Mai inu God bles you mai navicha

  • @KCS-vk3ce
    @KCS-vk3ce 5 หลายเดือนก่อน

    Wanzeru Akuona apa kuti vuto ndi Muthalika. Ana kufika pokunthana paguru kholo lawo limawalangiza zichani?

  • @estherkauyange6548
    @estherkauyange6548 5 หลายเดือนก่อน

    Warembembawe ndiwe wa mcp.....
    Iwe vuto siukuona kuti botomani akuombera mmanja za age limit poti akufuna kukhaulisa muntharika poti adachosedwa kuchipani Ali ngati oima paokha!

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u 5 หลายเดือนก่อน

    Achinyamatawo ndiyawo zawanyela😂😂😂

  • @FrancesMitengo-p2d
    @FrancesMitengo-p2d 5 หลายเดือนก่อน

    Dziko la Malawi chibwana chikuchuluka kwambiri

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m 5 หลายเดือนก่อน

    Parliament yalowa zibwana malo mokambilana zothandiza anthu anu muli busy kumangokangana zopusa boma lanji limeneli

  • @user-bi6pb5gc8t
    @user-bi6pb5gc8t 5 หลายเดือนก่อน

    Age limite ma mp nawonso

  • @giftphiri595
    @giftphiri595 5 หลายเดือนก่อน

    Kodi Joe Biden ali ndi zaka zingati tiuzeni tiziwe phindu la age Limit!.

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u 5 หลายเดือนก่อน

    Nayeso speaker sadziwa ntchito hule la chabe chabe

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 5 หลายเดือนก่อน

    Zamanyazi kudpp nawoso asuleman nkhalidwe alibe zoona mpaka kumenyana nkhani yongokambilana chipani cha chikwanje lero ayamba kumenyana okha okha kudpp

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m 5 หลายเดือนก่อน

    Mukupasidwa ndalama pasogolo muzasowa kolowela zitakuvutani

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u 5 หลายเดือนก่อน

    Chilenga machende ako akukutuma eti

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 5 หลายเดือนก่อน

    Ukalamba ukumupweteka Biden angoiwala zinthu uku mmalo muzipangila kampeni yekha umva akuti tiyeni timusankhe archrival wake Trump

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u 5 หลายเดือนก่อน

    Anyamatawa ndiwowa zikuwakanikawa.bwanji akulimbana ndi Peter akuopa chani?muli mavuto osaneneka mudziko akulimbana ndizaziii umbuli basi

  • @juniortsegula3847
    @juniortsegula3847 5 หลายเดือนก่อน

    Botoman ndi chirenga mboli ya manu mufa

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 5 หลายเดือนก่อน

    Nonsense shame on Malawi

  • @user-yh3dw6qu7z
    @user-yh3dw6qu7z 5 หลายเดือนก่อน

    I we achakwera ali ndi mphamvu ngati mnyamata koma boma likuwanyera.nkhanza kwa anthu anzeru oti amatha ntchito.samalani amalawi umphawi sudzatha,mbambadi.

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 5 หลายเดือนก่อน

    Akuononga parliament ndi ma speaker

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 5 หลายเดือนก่อน

    Koma Chipani chimenechiso ndi cha agalu okhaokha

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 5 หลายเดือนก่อน

    Achita bwino kumukuntha Botoman.Chilengayo nayonso he is very useless 😊

  • @PaulMvuma
    @PaulMvuma 5 หลายเดือนก่อน

    Dpp sichipani ndi nkhondo, zoona aliyese azingochokela ku thyoro mulomwe, dyakanani mwekha wa dpp, my vote to Mcp

  • @user-kk4uj8ko8k
    @user-kk4uj8ko8k 5 หลายเดือนก่อน

    Ifendi ana adadi chifukwa kovota amapita angongo nakha bwanji samawabweza
    🎉🎉🎉