Amen father, powerful message 🙏 However, we are very surprised in these four years of this administration, only few of you who are fighting for our freedom, I really agree with you father, where are the bishops, where are the pastarol letters which used to be there even when things were not as worse as they are at the moment? Why are the bishops just watching pamene nkhosa zanu zikuzunzika? You should be serious kuti mupulumuse a Khristu anu. Mukumbukire ndikutengera nthawi ya ya Kamuzu, mabishopu anzanu sanaope kuphedwa ai ndipo anapulumusa mtundu wa Malawi kuphatikizapo inuyo, now this is your time to come out not tomorrow. Kapena Inunso ndi agalu osakhulupirika amane mwaponyeredwa mafupa kuti mutseke pakamwa? Tiuzeni zoona, tikudabwa nanu.
Mulungu wayika Mau mwa Inu For Mthalika Amen 🙏🙏🙏🙏
Ambuye apitilidze kukutetedzerani father Nthalika
Amen father
There is power in this message. Christians are too now. Sunday masses should be conducted with Malawi problems at heart. Thank you Father
Chilungamo chiziwawa Powerful massage amen
Amen.W need prayers
God bless you father amen 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Yes
Powerful message from God
GOD BLESS YOU AMEN
God bless you
Indeed amen ❤❤❤❤❤❤
Amen Fr
Amen ❤
❤❤❤❤❤
Powerful 🙏
Amen 🙏🙏
Amen amen
Mulungu akundaliseni
Amen
Zikomo FR mwati pansa uthenga wa phavu
Ndidakusowani
Zoona Father zimine mukunenazi. Ndipo ine ndi kudabwa kuti mumbuyo monsemu mumapanga ma Pastoral Letters lero mwagotizi. Auzeni Ambuye Msusa kuti atimeme tonse tipite ku Kwacha tikapemphere tonse.
Zoona tiyeni tidzuke
Amen and amen father
Zikomo kwambiri Fr chifukwa Cha Uthenga wachenjezo. Ine ndaulandira ndi mtima wa chisoni chifukwa chakulephera kuwuma ngati galu okhulupirika
Amen father, powerful message 🙏 However, we are very surprised in these four years of this administration, only few of you who are fighting for our freedom, I really agree with you father, where are the bishops, where are the pastarol letters which used to be there even when things were not as worse as they are at the moment? Why are the bishops just watching pamene nkhosa zanu zikuzunzika? You should be serious kuti mupulumuse a Khristu anu. Mukumbukire ndikutengera nthawi ya ya Kamuzu, mabishopu anzanu sanaope kuphedwa ai ndipo anapulumusa mtundu wa Malawi kuphatikizapo inuyo, now this is your time to come out not tomorrow. Kapena Inunso ndi agalu osakhulupirika amane mwaponyeredwa mafupa kuti mutseke pakamwa? Tiuzeni zoona, tikudabwa nanu.
Kalata imatuluka nthawi ya rent, February
Wakuva aziva osava asave uthenga fr nde mumatipatsa ,,,ndipo apa agalu osauwa ndiopanda phindu kwambili
Zowona kuli ziiiiii zodabwitsatu
Tikudya mafupa
Zikomo
Mipingo inalandila ndalama za anthu andale
Zilibwino kwambili mulungu apitize kukudalitsani
Kkkkkkkkkk koma ndiye kuponya mafupaa. Mwina kusauuwaku tikudya mafupa omwe ena aponya... Pakamwa pauma.
Mapempherodi akufunika koma vuto atsogoleri amipingiwo aikidwanso mu system yoononga Malawi kamba kadyera. Asankha ndalama osati kuonetsa chilungamo.
Ndipo mulungu awapiphite atsogoleri amipingo akudyesedwa ndalama
Ndili ndi chisoni kwambiri kwa ma Bishop anthu, Ndi anthu amene anatilakwisa kwambiri akhristu fee munthawi ya zisankho mu 2019 kukolezera kuti Boma ligwe kuti Boma lilipoli lilowe. koma pano tili pa mavuto azaoneni iwo ali ziiii, kapena ndizomwe mumkafuna kuti ankhristufe timzumzike chonchi?. Tsiku ndi Tsiku mumakamba moyo odzidalira potukula mpingo wanthu komaso amsembe, amsembe kuti adye zikusowekera akhristu fe kupisa thumba molowa manja, koma thumba mwathu mukhala bwanji molowa ndi mavuto alili dziko munowa?.
Ndikhokoze mulungu potipatsa galu awuwa(Fr. Elizeo ) , mulungu akudaliseni ndikukupasani mzeru zotiongolera komaso azikukutetezani nthawi zonse chifukwa ndikudziwa kuti muzigendedwa poti galu owuwa amagendedwa ndi okuwidwayo.
Ma Bishop anthu ambiri anakalamba chimene amaganiza ndi ukalambawawo basi, zikana khala kuti u Bishop amavota bwezi enawa atakapuma, ali mu bungwe la PAC koma akuikira kumbuyo Boma lomwe likuzumza anthu kuti lipitilize kumzuza amalawi. Mayooo mulungu wanga. God have mercy to us.
God bless you
Amen fr
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
amen
Amen Father
Amen