Kumvesetsa kumakuvutani anthuni .. nkhani ikachitika osamadya fulumira kusutsa ayi.. Anavitcha anali ongogwilidxira koma mwini anali Chaponda .popedza chiletso chachosedwa no way and no way we can do .koma kubwedxeresedwa khumbo ndi chiganizo choti chaponda ndi leader of opposition. ndipo Anavitcha aliduuu
Osamango penyerera chiri chonse,kumaona patali,kusekerera,nkumasekerera zopusa mpamene muda votera Tonse alliance nchakwera mwaona m'menemo mwavuti kira kumeneko?thaiming'i changu pa Malo
Ma bungwe omwe tili nawowa mnga dyera zeedi inu nankhumwa a khala udindo wa u opposition leader mwachinyengo iwo pheeeee koma lero Dpp yangosintha a ayi Nav to Chaponda nyweee-nywee ngati angatithandise mzeru
Peter muthalika ndi galu kwambiri, ali ndi anthu ake omwe amafuna kukhala pa mipando kamba kaphavu zake. Chitsiru Peter muthalika. Amary kavicha mwawona kuti DPP ndi chipani cha Sankho ngati chitsiru peter muthalika galu wakulu nyani pusi nkhwele
Kodi azimai akhala angati kumeneko? Iiiii koma azimai inu muli ndi vuto. Even mmene amachitila speaker uja mmene amachitila mu nyumba ya malamulo muja amapanga zinthu zamatama zomphwanya malamulo zokondela zosonyezelatu kuti ma udindo ena safunika azimai , which means pamafunika ku parliament -ko kukhale nzimai ndi mmbamo osati onse azimai ai , koma mwina vuto ku bpp 1 asankha munthu wankulu osati wachinyamata and 2 akondela kumbali ya ntundu onse sangakhale ambali imozi apa ndizuzulepo sanaganize bwino.
Apapa zaonetsa kuti DPP sidzatheka posankhana maudindo ifeyo a Malawi tikufuna mai Mary Navicha abwelele ku leader of opposition apo bii sitidzavotelanso DPP
Inu Izi muchedwa nazo ndi mbuli zimzanu za mabungwezo, inu tidziti nthawi yomwei mwaiwala Kuti DPP inasankha a Chaponda Koma Ku parliament adakanidwa chifukwa cha injunction Yao ndi Nankhumwa mchifukwa DPP inasankha a Mary Navitcha Kuti agwirizire udindou tsopano Pano pamene Nankhumwa wavomereza zosiya udindou zakhala Ngati a Chaponda amasuka
Inu simukudziwa Chimene mukulankhula, nkhani iyi mukuidziiwa ndikale Kuti adasankhidwa pa udindo _u ndi George Chaponda Koma chifukwa cha injunction samaloledwa kukhala pa udindou mchifukwa adpp idaganiza zosankha a Mary Navitcha tsono mmene Nankhumwa wavomereza zosiya udindou zakhala Ngati a Chaponda amasuka
Sadalakwitse koma akonzano mosapereka mpata mcp kuilowaso mkwapha ngati zidalili ndi puppet nankhumwa uja because chopanda is a strong guy to opposed the mbava alliance
DPP yachita bwino, inuyo mukanakhala a nzeru mukanazuzula Nankhumwa yemwe amakakamira pa udindo ngakhale malamulo samamulora kukhala leader of opposition.
Ndipo Zoonad bro
Kumvesetsa kumakuvutani anthuni .. nkhani ikachitika osamadya fulumira kusutsa ayi.. Anavitcha anali ongogwilidxira koma mwini anali Chaponda .popedza chiletso chachosedwa no way and no way we can do .koma kubwedxeresedwa khumbo ndi chiganizo choti chaponda ndi leader of opposition. ndipo Anavitcha aliduuu
Ma bungwe opusa bwanji amamhlola nankhumwa pomwepo kwa 2rys ndiye lero bvuto ndichani
Big up brother man!!
Osamango penyerera chiri chonse,kumaona patali,kusekerera,nkumasekerera zopusa mpamene muda votera Tonse alliance nchakwera mwaona m'menemo mwavuti kira kumeneko?thaiming'i changu pa Malo
Khani yokhunza chimanga,pakadali pano chimanga chikutulutsidwa mu dziko muno,Zambi, Tanzania mavenda akumeneku akutulutsa zokolora zathu chitetezo chikhwimitsidwe pepho langa ndilimenelo
Mufuna mupeze njira yomuyika zimayi kuti muzamugule kuti muphe president Peter
Azimayi ife Mulungu anatipanga mosiyana kwambiri ndi azibambo wosamangoti 50/50 nthawi zonse kumawonanso ndimaudindo ake, positha anthuwa awona chinachake timva bwino bwino zeni zeni zake tiyeni tidekhe.
Arakwisa kwabili
Anthu amene akuzikokha zimenesi ndi a McP
Mr,mwangomba penjani🙏
Mabungwewo ngati alipo bwanji sazuzula zovunda zikuchitika kwa olamula boma
Ma bungwewo ndi auchisilu bwanji sakupanga zotheka kumbali yamavuyo pamene satana akuzuza anthu uchisilu yeti
This is is judge than ever, taking long time of cases worsting alot of money for the government. Chakakala you are doing wel thanks you br....
Anthu openga kwambiri, MCP ikulilitsa anthu m'dziko lamalawi but ma civil societies anasankha kukhala çhete osadzudzula MCP ndi chakwera, lero angoona kulakwitsa Kwa DPP? Foools😲
Kodi wa Norman Chisale bwanji sawuthetsa???ndiye kukonderatu mesa wakenso ukusowa umboni
MCP under Chakwera manyaka enieni mxiiiiiii😢😢😢
DPP apapa yakungana. Osamangovomeleza zopusa ku Parliament😅😅😅
MCP ikudziwano kuti apapa ndi Chaponda walowayi agobora zedi
Mwa yambo😮
Mabungwe amenewo anali kt nthwawi yomwe nankhumwa amakakamira mpando ndye aoneke anzeru lero zachamba
Amabungwe akayambe chipani chawo.
Achita bwino osamupasa zimayi ayi azimayi anatiphera Bingu president wabwino Joice Banda khani yake ya 50 to 50 tiyeni tidzialamura basi
Mary amaopa akut Moyo wao unali pachiopsezo😊
AAA koma apa sipanayende bwino maiyu amulakwila kaya
Sanalakwitse akudziwa zimene akuchita zisakukhuzeno ayi
Aaaaaa Inu chalakwika ndichani pamenepa koyamba muone kuti amakhala pa mpandoyu chifukwa chani ndye mukatelo ndipamene mungaziwe Zen zen
Mabungwe opusa kwambiri ,bwanji akhala akuyanganira zinthu zikuonongeka kumbali ya anankhumwa ngati mwalandira ndalama ku mcp mwauponda dpp 🔥
Inu program inalipo kale mai aja anangogwilizira mensa kunali kulimbana nthawi ija ku parliament
Kumvetsa chison kwambiri
Yayi anthu akufuna kusokoneza a Mary Navicha akuimira a mcp amenewo
Mabungwe wotu ngoputsa mitu yamawo dpp musayitsokonedze ayi agalu inu amabungwe mutsamalowelele dza dpp chaponda timakonda navicha timakondatso wotsewo ndi dpp
Apm ndi wovuta kumuvetsa🙌
Basi mulandu watha
muklufuna adzimudelela mayiyo akamayankhula
Chakwera akuzidziwa zimenezi
❤❤
Mzeru za APM ndende kalito pasuwa,dpp moto buuuuu
A zimayi nawo akhoza kuti imilila ndithu kukhala leadership ngat opos
Koma mabungwewa chomwe akufuna even iwowo eniake sakuchiziwa
Mabungwe sakamva chichewa....kuti Mai wa akugogwilizila ...koma ..Anthu muli ku mchikamwatu 😂
Milandu akuthetsa ndichakwera amene achankakala amangotumidwa chabe.chakwera ndiamene achoke.
Anthu anamkonda mai Navitcha, alakwitsadi.
Nde achotsa chigukwa chani mmesa anasankhanso okha ??
Izi sayambikazi ndizachamba kwambili addp achitazi ndi zachabe sanapange zabwino ayi akhale zimayi omweyi a alibwino kwambili mwawuze addpwo kut ine zandinyasa kwambili
Kingston Chaponda is a thief,imagine cach stack in the house,dollars in abundance abundance
Peter mutalika ndi wamisala
Zimayi amapanga nkhani ngakhaleso komwe iye aliko sakupuma bwino
Sizikugwirizana ndipo musazese chisokonezo mu dpp chifukwa iwo anaikidwa ngati ogwirizira not okhazikika
A dpp alakwisa kwambili mayiyu anapereka chiyembekezo .azibambo amakonda kulandira ziphuphu.mabanzi koma mayiyu amaoneka kuti ndiolimba mtima
Kodi ndiye Kuti muzingosankana Alonwe nokhanokha kusankhana mitundu sikuzatha
Inu mukuyikoka nkhani chifukwa chani asiyeni chaponda akwanisa wina ariyese oro ineyo nditha kukwanisa
Alakwisadi pochosa
Ndikuona ngati eni ake mai navitcha abwele okha azafotokoze kumbali yao chifukwa athu mungolumana nokha nokha ayeni ake ali chete
Ma bungwe omwe tili nawowa mnga dyera zeedi inu nankhumwa a khala udindo wa u opposition leader mwachinyengo iwo pheeeee koma lero Dpp yangosintha a ayi Nav to Chaponda nyweee-nywee ngati angatithandise mzeru
Szinayende bwino ayi,dpp mwatani kodi,this is not good after all.Wels .
Peter muthalika ndi galu kwambiri, ali ndi anthu ake omwe amafuna kukhala pa mipando kamba kaphavu zake. Chitsiru Peter muthalika.
Amary kavicha mwawona kuti DPP ndi chipani cha Sankho ngati chitsiru peter muthalika galu wakulu nyani pusi nkhwele
Nkhani ndivuto.losatsatila ,,,,, well done DPP
Kodi azimai akhala angati kumeneko? Iiiii koma azimai inu muli ndi vuto. Even mmene amachitila speaker uja mmene amachitila mu nyumba ya malamulo muja amapanga zinthu zamatama zomphwanya malamulo zokondela zosonyezelatu kuti ma udindo ena safunika azimai , which means pamafunika ku parliament -ko kukhale nzimai ndi mmbamo osati onse azimai ai , koma mwina vuto ku bpp 1 asankha munthu wankulu osati wachinyamata and 2 akondela kumbali ya ntundu onse sangakhale ambali imozi apa ndizuzulepo sanaganize bwino.
Chipani ichi chatikwana ndizochita zake mayi inu ingochoni basi
Very sorry dpp party this is shirt democrats
Apapa zaonetsa kuti DPP sidzatheka posankhana maudindo ifeyo a Malawi tikufuna mai Mary Navicha abwelele ku leader of opposition apo bii sitidzavotelanso DPP
Inu Izi muchedwa nazo ndi mbuli zimzanu za mabungwezo, inu tidziti nthawi yomwei mwaiwala Kuti DPP inasankha a Chaponda Koma Ku parliament adakanidwa chifukwa cha injunction Yao ndi Nankhumwa mchifukwa DPP inasankha a Mary Navitcha Kuti agwirizire udindou tsopano Pano pamene Nankhumwa wavomereza zosiya udindou zakhala Ngati a Chaponda amasuka
Chipanichi chawonongeka basi
Namalomba ndi chitsilu akufuna kusokoneza chipani cha dpp
Inu simukudziwa Chimene mukulankhula, nkhani iyi mukuidziiwa ndikale Kuti adasankhidwa pa udindo _u ndi George Chaponda Koma chifukwa cha injunction samaloledwa kukhala pa udindou mchifukwa adpp idaganiza zosankha a Mary Navitcha tsono mmene Nankhumwa wavomereza zosiya udindou zakhala Ngati a Chaponda amasuka
DPP mwatani?Mzimai yu mukanamusiya pomwepo. There is always next time for that madala.Mmwambadi DPP mwakondela😢
Ine wa dpp koma mwalakwisa kuikaso mbava yoba chimanga
Magulu... osowa zochita... Navicha was just acting...mabungwe ayambitse zipani zao
Pamenepo ndiye muonetsetse kuti😂dpp simalemekeza azimai pokhapa aitaya,dpp itha ngati makatani.
Wabodza iwe
@@user-qv4ko6ps4j uonatso before vote amalawi onse azalotetsedwa kuti osavotela dpp, chifukwa akabvotela dpp abale akhungu lachi albino ali pa chiopyedzo.mulungu,sangakhululukile amalawi ngati sugar tikugula K5000 tidzagula K10000 paketi.tiyeni,tingoyetsela UDF olo afford.alipowatso,ndiye nyanyi aiwala,kuti amati chani.kaya,atogonabe.kofunika,mbama kuti azuke,olo akomedwa ndi pa mphiri la kalimeli
@@HarrisonMwanga-xy4sc iweyo ndi wa Mcp
@@user-qv4ko6ps4j kodi lero ungavotele,mcp? nthawi yomweyo ukuponya vote yakoyo thembelelo diiii.ingofana,ndi dpp polaso afford olo UDF
Satana akati agwile tchito yake kungovesesana bac mayi navitcha upezeni ntima enawa ndimayeselo DPP ndichipani chanu mama
Chokani nonse mwachosesa mai Navicha
Sadalakwitse koma akonzano mosapereka mpata mcp kuilowaso mkwapha ngati zidalili ndi puppet nankhumwa uja because chopanda is a strong guy to opposed the mbava alliance
Mabungwenso ndiopepera mesa anali ogwirizira kodi chifukwa cha chiletso chinaikidwa pa Chaponda?
kod Mesa Mai wa anagwirizira?
@@sirgiftedmagalasi22 Eyaah anangogwilizira komano a MCP akungofuna kuyambitsa mpungwepungwe pazinthu zosawakhuza