ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Rest well legend Chibade, your memories are still flowing over us in your music.
I have been looking this song for so long, Thank u guyz. Rest well Thomas Chibade😢😢
Mwaguila n'chito kutibweletsela nyimbo za Chibade zikomo kwambiri🎉🎉🎉
Powerful message chibade rest in peace
Uthengau wabwera munthawi yake zikukhala ngati ali moyo chibade 😢😢😢rest in peace chibade
hie bro thanks so much ndimazisowa yikani zonse nyimbozi plz 7 11 yose ujabyikani plz
Malemu awa tizawakymbukila Mpaka kale lelo si izi😢😢😭
Thanks bro timazisowa nyimbo izi tiponyeleni zonse 7 11 yo❤
Mmmmmm what a song! Rest in peace
Mumkaimba achimwene, may your so rest in perfect peace 😢😢 tayamba kuziona ndithu MCP itipha, koma ambuye akuona.
Great song,great message 😢😢😢 respect
Man awawa anali machine eeeeh🫡
Rest in peace thomas chibade we real love u
What a nice song Rest in peace Brother
😢😢😢😢 Dolo legend never die 🎉😭😭😭
This guy was something else
I love you 😭😭😭😭😭😭😭 continue to Rast in peace 😭😭😭😭😭😭😭😭😭
😂😂😂😂😂😂😂 Boa tarde como solicitado envio 😂😂😂❤❤❤
Keep resting in peace Thomas che nkhumba chibade
Koma ifa eeee kaya
Eeshii nyimbo ya mphavu,RIP
Much respect, Chakwera ukumva izi, kamangeni malemuwo basi 😂
This guy was talented 😢 RIP
My favorite artist rest in peace
Mmmmm m'mdima ujatu wagwa
😢may Your saul still rest in 😢😢
Chibade may your soul rest in peace my brother
Tikangoti tatenga boma amphawi nonse kumakako eee adah awawa rest well sure
Rip Thomas Chenkhumba chibade
Chibade anali Star ⭐
Musician uyuyu adali opasa chidwi paluntha lake loyimba...
Very Brave msg rest well.
Ndikuyedza kuzisaka Kuti ndigule koma zikukamika Kodi ndipange bwanji
Nice music🎉
please upload Thomas Chibade mwatenga nsambi from Mbenjere collection volume 1
Good song
Rast in peace chibade vuto ndilakuti anthuwa akunthandizidwa ndiphavu zakumidima pali vuto lalikulu
Koma na nyimbo iyiyi aaa ndikuswakuswa ndithu
Great song eashh❤
Good job guys kee so🎉🎉🎉
i ll nver foget thomas chibade
Kuimba koma uku Rlp
Thomas tudo certo estará disponível ❤❤❤❤😂😂😂😂😂😂 Emiliano 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Thomas chibade RIP
Good Messnge Zoona
koma mukanamuikila chithunzi chabwino osati ichi
Nyimbo izi sindinazimvepo kodi ndi new album ?
Yes zanyowani
Ai ndi zakale@@user-fv9rh6cv1n
Name the producer please
😢😢😢😢
Rest in peace
Kofusila banja sumapita utamvala zikwanje
Nyimbozi are from which album ?
Yes new album
@@AleksaWilliams-qc6cn first heard this song in 2009 in album he did with Nkasa it was a collection
This album is called 7 11 and it was released in 2007/008.This was after Zatukusira, Mufatse and Kuno Nkumanda albums
When did he released this song guys?????
somewhere in 2009
Album yomwe imayenera kutuluka asanatisiye,,,
@@user-hh4xg4hf2k that song is very old,, released before the 2009 campaign, you can mark words as well like the chorus " Bingu " ,somewhere amkakambanso za "celtel"
Inu munayamba mwayimverako?
It was released in 2007/2008 chimbale ichi ndimomwe mukupezeka nyimbo ya Our Love will never end