This was is insane. The UTM leaders dont need Usi's endorsement, they needed the endorsement of the delegates. This coward run away from the convention to avoid shameless defeat. He is an outcast, irrelevant and a confusionist
Michael Usi ndikape kwambiri, he is being a states man. If he doesn't want to be associated with the party, he would have just paved way for others. This mayhem will just bring division
Kodi Anthu opita Ku Israel apita bwanji, ? Ku Israel kuli nkhondo mabomba aku phulika pena paliponse komanso eniake a Ku Israel akuthawako kupita kumaiko ena ,Anyamata muyenda bwanji? Mukafikira kuti?Nanga mukakhala pati? Chonde kuli NKHONDO Ku Israel pepani
Where are the factories and industries? Zitukuko is based on National planning and funding by the treasury using Misonka zathu. Not funding MCP Chakwera 70 trips.
Michael usi akupanga ngati sanapite ku xul pena bwanji. This is not TIKUFERANJI when you are not happy with UTM why using their brand. You could have also stopped people wearing their colours and using their brand. You are fueling the downfall of the party.
Mkwezalamba you have spoken very well indeed and that's true don't bite about the bush
Iwe Usi ndiwe osokoneza Kodi mmesa iwe ndiwe wa mcp, Uli ndi Dyera munthu oipa iwe
Yusadi uyu akusunga ku mcp chifukwa akufuna kuti akoke anthu ku UTM kupita nawo ku mcp nde kwatsala miyexi ingati tiwona ngati atansungenso
This was is insane. The UTM leaders dont need Usi's endorsement, they needed the endorsement of the delegates. This coward run away from the convention to avoid shameless defeat. He is an outcast, irrelevant and a confusionist
Iwe ngati ndani kodi??
Ine ndine waku karonga kma zoti chikangawa azapeza voti ku karonga ndi kukayika ndi munthu modzi yemwe waononga dziko la Malawi
Kuli nkhondo ku islael please ma islael eni ake akuthawa please umphawi sumatha mukafera za eni
Mutu sukugwila iweeeee
Usi lino ndidziko samalani
Uyu akufunika kumangidwa basi
Tangotuluka basi,,,,ngati uli ndi dzeru uyambitse chipani chako , otsati zowasokoneza anthuzo
Munthu osokoneza. Kukakamila UTM pomwe muli Ku MCP..ndi dzikotu ili..kuyaluka nazo izi
Uzifunse kt kwasala medzi ingat kt udindo unyadila iwewo kt uthe uli ndisoka manganya
olo us zomwe akupamga ndizamisala koma uzalota saulosi akukukodolo ndalama walandila za mcp ndimasoka 😢
Usi zikuvuta uwasiye anzako wa MCP iwe
Akuluwa ndi achitsulu
Usi ndichitsiru, udf, afford, pp, etc ndilama adalandira adalemba
Following
𝕄𝕒𝕟𝕘𝕒𝕟𝕪𝕒 𝕡𝕒 𝕟𝕪𝕖𝕣𝕠 𝕡𝕒pako
Manganya akupanga zimenezi chifukwa akuziwa kuti nthawi yake yasala pangono kuntha Azanyela ameneyu ndi Lazaro wake 😅
wekha ukt sanalembe aiwara ndiye ukufuna akuuze chani
Chitsilu iwe
Aaa mesa a usi thawi imeneyo iwowo ndamene anali president wa utm ?
Koma chakwera waononga ziko ra malawi zingozi izo tikuziona anthu akufa ningozi zamazi njara ndiyimeneyo tikuyiona fetereza wakwera mutengo ndeno ndarama tizipezakuti kuti tikagure fetereza odurayo bolani tiza votere pita mutarika
Tutsarire chilungamo, ndipo chiyende ngati madzi
Kkkkk komatu kuli zobisika
Michael Usi ndikape kwambiri, he is being a states man. If he doesn't want to be associated with the party, he would have just paved way for others. This mayhem will just bring division
Sibwino
Wadyela iwe panga chimodzi asiye a utm panga za mcp zakozo dyela mkufupikako mutuowumawo
Amanganya tasankhani chipani chimodzi mukutibalalitsa ife, nokha mukumati boma ndilomweli boma lake ndi liti?
Kodi Anthu opita Ku Israel apita bwanji, ? Ku Israel kuli nkhondo mabomba aku phulika pena paliponse komanso eniake a Ku Israel akuthawako kupita kumaiko ena ,Anyamata muyenda bwanji? Mukafikira kuti?Nanga mukakhala pati? Chonde kuli NKHONDO Ku Israel pepani
Where are the factories and industries? Zitukuko is based on National planning and funding by the treasury using Misonka zathu. Not funding MCP Chakwera 70 trips.
Manganya nde wasinthiratutu....uyu analidi wa kongiresi mkale komwe, ndatsimikiza
Koma ndiwamisara using basi
Okuba uyu
Usi let those people go and be productive instead of that nonsense. I thought kuli njala?
usi ma battery Ako , upange zako ndi chikangawa party yakoyo, zolimbana ndi utm usiiletu pamtumbo pako iweeee
Ndipo manganya akubowa he always over exited
Kodi yeyu akuyikakamila utm bwanji chonsecho Ali kale ku mcp koma nama drama
Basi kutuluka basi
Tangopitani ku MCP ko bwana usi mwatikwana ndi ma drama anawaaa aaa
Michael usi akupanga ngati sanapite ku xul pena bwanji.
This is not TIKUFERANJI when you are not happy with UTM why using their brand.
You could have also stopped people wearing their colours and using their brand.
You are fueling the downfall of the party.
Komaso bwanji athu mukulimbana ndi Muthu openga inuo simuona kut manganya mutu mwake simugwila bwino
Ndipo.manganaya ukutinyasamo chosecho iwe umkadandaula kut chimanga ndimadula nthawi ya APM ilinali pa 12,000 lero chilipabwanji chimanga iwetu mulungu azakulanga ndisaname ndipo ndiwe wadyera osati masewera
Munthu wopanda nzeru
Iwe wa channel, you should learn to stick to your headlines. Are we entirely watching times TV? You can do better 😊
Apatseni Malaya a kongiresi anthuwo achotse I mu chgoba
Kom nde us ndionjoyat
A usi nthawi yoseyi anali kuti? Kuti pano azinena za kumaliro a vp
Koma maganya dzimu wa Saulos ukukathe iwe,kutembenuka kwa bwanji uku
Usi please leave utm alone pitiliza zako kaya ndi umodzi party or wodya zake alibe mulandu ur boring us futsek
Limbo yakenso yaifupingati iyeyo akagwele
Ngalu iwe yudas usi
Following