ZIMENE WAYANKHULA PRESIDENT LAZARUS CHAKWERA KU ZOMBA STADIUM LERO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 3 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 418

  • @FosterChinzimuBanda
    @FosterChinzimuBanda 4 หลายเดือนก่อน +6

    Empty ground mmmm ayi kulephela kuzazisa ground iwe paulendo basi,mwatitopesa muzipita basi.

  • @WilliamKawaza
    @WilliamKawaza 4 หลายเดือนก่อน +9

    UTM my vote

  • @fredericknamaya7248
    @fredericknamaya7248 4 หลายเดือนก่อน +4

    Thank you my Zomba people

  • @DorotyMussah
    @DorotyMussah 4 หลายเดือนก่อน +25

    Ubwerenso kwathu ku thyolo tikuponde uone

    • @AnnieBanda-rb2dk
      @AnnieBanda-rb2dk 4 หลายเดือนก่อน +2

      Mupondeni anyamata iyaa anthutu tinalusa kkkkkkkk galu ameneyu abweleso ku nkhatabay galu uyo

    • @JoyceBanda-k8t
      @JoyceBanda-k8t 4 หลายเดือนก่อน

      Chisiru ameneyu adzaone tidzamucitire a kuthyolo thekerani

    • @aaronguwechakwira
      @aaronguwechakwira 4 หลายเดือนก่อน

      Akumangila ndan . Ndalama Za aMalawi ndie uziti chakwera wàamangila

    • @ConfusedAstronaut-qv6wq
      @ConfusedAstronaut-qv6wq 4 หลายเดือนก่อน +1

      Arise galu ameneyi waukape kwa basi

    • @YoseDivaison
      @YoseDivaison 4 หลายเดือนก่อน

      Makape inu

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 4 หลายเดือนก่อน +1

    Mapazi ako chakwera, utsongoleri opanda matso phenya ngat uwu sindinawuwone😂🤣

  • @BlessingsRodgersPhiri
    @BlessingsRodgersPhiri 4 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂😂iwe nde uli ku oxygen basi yooo
    Nsonkhano wa president kapena wa pa sukulu😢😢😢

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo 4 หลายเดือนก่อน +9

    Alomwe siyathu ochitanawo zibwana 😂😂😂😂😂 osangosiya bwa

    • @Stevekatiwa-tp3oq
      @Stevekatiwa-tp3oq 4 หลายเดือนก่อน +2

      Many akowo uzipangila ku central Region komko😂😂😂😂😂😂🎉😊

    • @ThomasChisapula
      @ThomasChisapula 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂🤔

  • @ipmkanda4755
    @ipmkanda4755 4 หลายเดือนก่อน +16

    Ati kuli chani kod? Kungokhala ngat ana akulembetsa sukulu

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂

    • @HannahSalimu
      @HannahSalimu 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂😂

    • @ThomasChisapula
      @ThomasChisapula 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂🤔

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉nyekhweeee

  • @AdiniKhama
    @AdiniKhama 4 หลายเดือนก่อน +10

    Ukuwona ngati amalawi tikugonabe since 2020 wapanga chani zopusa basi

    • @DeenesNurudMeke
      @DeenesNurudMeke 4 หลายเดือนก่อน

      Ndipo zaugalu kwabas mm

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 4 หลายเดือนก่อน +5

    Anthu akuzomba aliphee nyumba zawo kkkkk.alipo ndi achipani bas ndi mkazi wake 😂😂😂😂😂 wagwanayo bs

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 4 หลายเดือนก่อน

    Apm my vote

  • @AiwaMedia-sh6vx
    @AiwaMedia-sh6vx 4 หลายเดือนก่อน +6

    Ine ndimaganiza kuti ndi meeting ya anthu obvuwula mchenga😂😂😂😂😂😂

  • @vanessafbanda3913
    @vanessafbanda3913 4 หลายเดือนก่อน +11

    Ali busy kuyang'ana yang'ana kut anthu achokera kut kma kuli ziii 😂

    • @HannahChingwalu
      @HannahChingwalu 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂vele thafuu

    • @ZamazamaKatatu
      @ZamazamaKatatu 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂

    • @ThomasChisapula
      @ThomasChisapula 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂🤔

    • @fyopokappata9738
      @fyopokappata9738 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂 koma abale iiiii

  • @RodgersTchuzi
    @RodgersTchuzi 4 หลายเดือนก่อน

    Dr Laz my golden vote..❤

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 4 หลายเดือนก่อน

      Ufiti basi. Anthu ngati iwe dindingawathandize.

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 4 หลายเดือนก่อน +1

    Kungoyakhula kupanda manyazi 😢😢😢

  • @PililaniChingo
    @PililaniChingo 4 หลายเดือนก่อน +9

    Chonde anthu Aku zomba pitilizani Moyo uwu 😂😂😂😂😂

    • @DeenesNurudMeke
      @DeenesNurudMeke 4 หลายเดือนก่อน +1

      Ndipo kwambiri kkk

  • @RuthRaphael-k2j
    @RuthRaphael-k2j 4 หลายเดือนก่อน +7

    Mzimu wa chilima uzayakhura apa km wakwiya

  • @pemphokatembe443
    @pemphokatembe443 4 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂kwathu komwe ukoooooo ku Zomba.,,koma nde kunali unyinji wa anthutu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣hahahahaha uziona

  • @doreenchimombo
    @doreenchimombo 4 หลายเดือนก่อน +10

    Kkkkk ,Yakwiya ndi Mizimu😂😂😂

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga 4 หลายเดือนก่อน

    this is the only president in malawi history ,that has terribly failed malawians......

  • @JohnstonNyirenda-zw6jd
    @JohnstonNyirenda-zw6jd 4 หลายเดือนก่อน

    Olo kulimba mtimako 😂😂😂😂 aaaaah 😊

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 4 หลายเดือนก่อน +7

    Anthu akenso ndi azimai okhaokha 😂😂😂😂😂Koma ziliko eeeeeeee

    • @SigereAckren
      @SigereAckren 4 หลายเดือนก่อน

      Pajatu azimayife tili ngati ntchentche zomangoteka ndi zina zilizonse

    • @ShakiraJackson-x8w
      @ShakiraJackson-x8w 4 หลายเดือนก่อน

      Ndipotu atenga kunjila amenewo

  • @chimwemwechathapo6405
    @chimwemwechathapo6405 4 หลายเดือนก่อน +6

    stadium inayamba nthawi ya dpp iyo ndipo yamangidwa ndi dola za boma la dpp osati awa kuzipaka zinthu zokuti sizawo komanso zitukuko zawo ndi kumanga anthu basi

    • @RaymondKaumba
      @RaymondKaumba 2 หลายเดือนก่อน

      From 2017 mpaka kutuluka m'boma osamaliza just maintainance 😂😂😂😂😂

  • @NelsonWaiti
    @NelsonWaiti 4 หลายเดือนก่อน +1

    Zomba ndi mzinda waukulu, ndipo kuli anthu ambiri, kodi achakwera anthu aku Zomba akulandirani?? Mukamakhala muziziyika pa sikelo!! Nduna zanu zikukunamizani, ndikukhulupilira kuti mwazionera nokha, anthu mdziko muno alibe ndani chidwi ndipo ndiokwiya.

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 4 หลายเดือนก่อน +7

    Komatu ndiye kunali khwimbi la anthu lolapitsa, moti Zomba yonse inakhamukira kuchinsonkhanoku watii😂😂😂😂

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 4 หลายเดือนก่อน +1

      😂😂😂😂😂😂😂

    • @AiwaMedia-sh6vx
      @AiwaMedia-sh6vx 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂😂zopatsa mmanyazi. Akungoyenda obvulabvula

    • @aggogokina8992
      @aggogokina8992 4 หลายเดือนก่อน

      @@AiwaMedia-sh6vx ndipo chimene sakukhalira pansi kusiya zoyendayendazi, munthu wayaluka uyu bas😀😀😀😀

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 4 หลายเดือนก่อน +1

      Ndipo zopasa manyazi kingokhala ngat msonkhano wa khansala.

    • @aggogokina8992
      @aggogokina8992 4 หลายเดือนก่อน

      @@JonesChingaya-yf4gg 😀😀😀

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 4 หลายเดือนก่อน +1

    Ine ndimaona ngati kuli chinamwalitu ndiye namwali wakeyo anali wa mwano😢😢😢😢

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani 4 หลายเดือนก่อน

    Anthu amu Zomba kunalibeko awa ndi achewa okhaokha ochokera ku Nsalu😂😂😂

  • @MustaphaChimangeni
    @MustaphaChimangeni 4 หลายเดือนก่อน +4

    Eeeeish komatu ndekunali nyanja nyanja chakwela woyeeeeeeee😂😂😂😂

    • @pemphokatembe443
      @pemphokatembe443 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @LysonKandaya
      @LysonKandaya 4 หลายเดือนก่อน

      😂

  • @VictorSiwale-d1h
    @VictorSiwale-d1h 4 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂 chakwela never soo it coming😮😮

  • @EdnahShantell
    @EdnahShantell 4 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂amaweva chani kwinako ngati kunali anthu 😂😂😂😂😂😂

  • @GoodsomSaires
    @GoodsomSaires 4 หลายเดือนก่อน

    😂😂 Ndiye ndikumati ukuyakhula ndi ndani

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 4 หลายเดือนก่อน

    Chimwendo i know you working hard,what i can tell you is that nothing you will get 2025

  • @RoseRose-w8r
    @RoseRose-w8r 4 หลายเดือนก่อน

    Akuzomba khalidwe lapamwambali akakuuzani ndani keep it apatu mwaonetsa ukadaul ovuta😂

  • @MarcosDjussa
    @MarcosDjussa 4 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂koma kuli anthu koma 😅😅😅😅😅😅😅

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 4 หลายเดือนก่อน +1

    Mcp mbava inuu

  • @SiphiweTonnyChidumayo
    @SiphiweTonnyChidumayo 4 หลายเดือนก่อน

    Zomba yakuonetsa kuchita kuyenda mobisalabisalatu😅😅 aching'ambira zima t-shirt zake kuno😂😂😂😂

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly 4 หลายเดือนก่อน +2

    Eeeeeesh koma ndiye kunali Anthu ambiri mpaka Anthu kusowa po🎉 khala stadium kudzadza ZOMBA IMAKWANA

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo 4 หลายเดือนก่อน

      Kudzadzatu everywhere very empty kusowa poponda 😂😂

    • @PeterChilombo-ou2cd
      @PeterChilombo-ou2cd 4 หลายเดือนก่อน

      kkk

  • @PeterGabriel-uh2lh
    @PeterGabriel-uh2lh 4 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 kwasuzga ku zomba 😊

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga 4 หลายเดือนก่อน

    what an embarrasment ,ukuku MCP...EXPECT ZERO VOTES😂😂😂😂😂

  • @EdnahShantell
    @EdnahShantell 4 หลายเดือนก่อน

    Koma kunali chinamtindi eeeee🙆😝😝😝😝😝🤣🤣🤣🤣🤣

  • @RoseChiphiri-ts8jx
    @RoseChiphiri-ts8jx 4 หลายเดือนก่อน +1

    Ndemwati ndi sonkhano wa president? 😂 Sorry mwatipeza tili ku phiri kowotcha makaka tigulise tikagule ufa 😂😂😂

  • @DennisDonework
    @DennisDonework 4 หลายเดือนก่อน

    Meya umakwana akumbuseni kuti inayamba2017😂😂😂😂😂😂

  • @Dellingsmunthali
    @Dellingsmunthali 4 หลายเดือนก่อน +1

    Kodi achimwendo ndio a bordgard akungot zunguli zunguli😆😆

  • @fundoniccoo-fk4ld
    @fundoniccoo-fk4ld 4 หลายเดือนก่อน

    Ndi nsokhano wa khasala or president zoona zomba yense anthu okhawo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @PaulineKamwana
    @PaulineKamwana 4 หลายเดือนก่อน

    Izi zokha ndie zandisangalatsa amayesa nkwa achewa ku zomba😂😂😂😂🤣🤣🤣🤣🤣 wagwa nayo chikangawa😂😂😂

  • @adelinekumvanakauka9997
    @adelinekumvanakauka9997 4 หลายเดือนก่อน

    Mayor wathu ndakunyadirani. Stadium inayamba kumangidwa 2017. No lies

  • @LukaJohn-q7y
    @LukaJohn-q7y 4 หลายเดือนก่อน +1

    Okupha ameneyo

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 4 หลายเดือนก่อน +3

    Panyopanu nonse, Zomba siwamaselatu, makape kulibe.

  • @EvalistoDarwins
    @EvalistoDarwins 4 หลายเดือนก่อน

    Nsonkhano wa bank mukhondee chani?? 😂😂😂🤣🤣🤣😂😂

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 4 หลายเดือนก่อน

    Hahahahahaha....kumeneku ndi kulandilidwa kodi? 😂😂😂😂😂😂😂😂...shame!!!... achimwendo mwamunamizatu munthuyu....taonani zamanyazi...😅😅😅😅😅😅😅

  • @FrankSimfukwe-w1s
    @FrankSimfukwe-w1s 4 หลายเดือนก่อน

    Amene akukuwayo kuti boma boma mapazi ake stadium imaoneka choncho tapitani ku bingu stadium mukaone osati podyetsela mbuzipo

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 4 หลายเดือนก่อน

    Za ugalu basi mbuzi zakupha munadya chilima inu tsiku lina mudzatsadza nyama yake ndukuudzani Continue Rest in peace My Chilima misonzi yosatha kwa ife 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @ShaffinhoKazembe
    @ShaffinhoKazembe 4 หลายเดือนก่อน

    A bambo asikono mpaka anayang'ana stadium yakeyo after chimwendo kuyankhula😂😂😂

  • @christjahseenmusic2362
    @christjahseenmusic2362 4 หลายเดือนก่อน

    Kķkkk stadium imeneyi or ground? Kķkkk

  • @HopeNgalande
    @HopeNgalande 4 หลายเดือนก่อน

    TIKUFUNIRANI UTSOGOLERI WA MPHAVU MULUNGU YEKHA WODZIWA KUSAMALA KUSALIRENI PAMODZI NDI A VICE PRESIDENT DR USI AMEN AMEN 🙏 AMEN

  • @KhondanKhondan
    @KhondanKhondan 4 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkk zawuchisilu bs😅😅😅😅😅

  • @GodfreyAwali
    @GodfreyAwali 4 หลายเดือนก่อน

    Koma Zomba nde inasonkhanatu kkkkkkkk.anthu a Zomba ndi oyamika a mayor atero🤣🤣🤣🤣

  • @EstherBonga
    @EstherBonga 4 หลายเดือนก่อน

    Bwanji ndiwawelenge anthu kkkkkkkk😂😂😂😂😂 dpp my vote

    • @GloriaKaduya
      @GloriaKaduya 4 หลายเดือนก่อน

      Ndiyamba ndine 1😂😂😂😂😂

  • @ernestphiri3723
    @ernestphiri3723 4 หลายเดือนก่อน

    Koma nde kuli thousands of people eeeeeee😂😂😂😂

  • @Uncle_B265
    @Uncle_B265 4 หลายเดือนก่อน +3

    Iwe ife tikufutika ndi njala palibe angapite ku mpira asanakhuteee wamvaa

  • @dingiswayojere5320
    @dingiswayojere5320 4 หลายเดือนก่อน

    Kodi anali kunali msonkhano wa mp 😂😂😂😂😂

  • @GibsonLackson
    @GibsonLackson 4 หลายเดือนก่อน +2

    Zaziii 😎😎

  • @PrinceGodfrey-vc5vn
    @PrinceGodfrey-vc5vn 4 หลายเดือนก่อน

    President kufika pamalo athu 100 osakwana 😢

  • @MikeKanyaza-bm5tp
    @MikeKanyaza-bm5tp 4 หลายเดือนก่อน

    Ayi zikomo 😅😅😅

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 4 หลายเดือนก่อน

    Stadium ya Peter ija mwati ndiyanu afiti inu. Inayambidwa kumanga 2017.

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer 4 หลายเดือนก่อน

    Kufuna ndalam osat chakwera uku 😂😂😂Km 😂

  • @PatrickLungu-hq2tz
    @PatrickLungu-hq2tz 4 หลายเดือนก่อน

    President uyu ndiwakutiko abre😢😢

  • @MuhammadInack
    @MuhammadInack 4 หลายเดือนก่อน

    Wasala ndi miyezi I ngati galu iwe😢😢😢😢

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 3 หลายเดือนก่อน

    Ku zomba ndie munaonetsa kukwiyatu kwambiri simunawapatse mpata anakhalako okhaokha Mbalame za anthu.

  • @tomasmtunduwatha-bl6ix
    @tomasmtunduwatha-bl6ix 4 หลายเดือนก่อน +2

    zomba ndi mangochi kuli athu osanyengelela zopusa tazionela tokha

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p 4 หลายเดือนก่อน

    Kulije munthu Kuli ziiiii😂😂😂😂

  • @VirginiaMafenda
    @VirginiaMafenda 4 หลายเดือนก่อน

    Anthu kod kuzombako simumaziwa kut kukubwera pre😊

  • @Hassankazembe-d3o
    @Hassankazembe-d3o 4 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkkkkk anthu anakwana 100 koma?😂😂😂😂

  • @AlinafePililani
    @AlinafePililani 4 หลายเดือนก่อน

    Amalawi samatha iucheza😂😂😂😂chonchi galawundi kunakakhara adadi bwenzi mwazazakotu

  • @jrculdickson6629
    @jrculdickson6629 4 หลายเดือนก่อน

    kodi anangobwera motutumutsa kapena😂😂😂😂sindikuona tu anthu

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 4 หลายเดือนก่อน

    Kuchita kumukakamiza Meya alankhule zotamandila Chakwera

  • @HassanJameskananjie
    @HassanJameskananjie 4 หลายเดือนก่อน

    Unyamuke uzipita mwatikwana iya dikila kenya ikubwela mpaka ku state house wooo

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 4 หลายเดือนก่อน

    Zonsezo apanga liti akuchoka awaaaaaa mark my words 2025 nkhondo ilipoo

  • @dingiswayojere5320
    @dingiswayojere5320 4 หลายเดือนก่อน

    Kwacha yagwa😂😂😂😂

  • @ChrispinNkusa
    @ChrispinNkusa 4 หลายเดือนก่อน

    Ndipo mumuuze chakwelayo machende ake akandifuna andipeze muthu yemwe wagwetsa dziko la malawi even maiko akuja or vote imodz sangapeze

  • @geraldgomati9624
    @geraldgomati9624 4 หลายเดือนก่อน

    Ka deputy president kafupika sikangawone za kutsogolo

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 4 หลายเดือนก่อน

    Tsokhano wa apule ngati ku show ya Jetu zoona? Tiyendereniso kuno ku Phalombe 😂😂😂😂😂😂

  • @ChikumbutsoTsalangu
    @ChikumbutsoTsalangu 4 หลายเดือนก่อน

    Akulu awa ndi Achisilu kwa mbiri Zomba kuli chani cha zeru chomwe chili ko cholodzeka
    Meya ameneyu ma Chendeake kwa basi
    Za yambikapo achimwendo Banda ku zutsa a pule
    Usi ali popo

  • @ClementbWatches
    @ClementbWatches 4 หลายเดือนก่อน +4

    Zomba sisunga makape. Anthu ali manyumba mwawo pheeee

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂

    • @modestamhango7737
      @modestamhango7737 4 หลายเดือนก่อน

      Zoona anthu akwathu sasekelera zopanda pake. 😂

  • @ChrispinNkusa
    @ChrispinNkusa 4 หลายเดือนก่อน

    Musamunamize president cholinga chongofuna ndalama muuze chilungamo nd galu wa pasi pa nyanja uyuu

  • @AiwaMedia-sh6vx
    @AiwaMedia-sh6vx 4 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂
    Kodi mukuyankhula ndi anthu akufaaaa, kapena amoyo anzeru zawo?

  • @it3788
    @it3788 4 หลายเดือนก่อน +1

    Abwerere kumavotes

  • @FavourLukanga
    @FavourLukanga 4 หลายเดือนก่อน

    Kudzadza stadium nde akungoti chewuchewu apule kuyang,ana khwimbi la anthu😂😂😂😂

    • @MasterBlack-r2n
      @MasterBlack-r2n 4 หลายเดือนก่อน

      kkkkkkkkkkkkkk Koma ndaseka. kuyang'ana khwimbi kapena kut chinamtindi cha anthu🤣🤣🤣🤣🤣
      Wakameraso naye analibe tyming.

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂

  • @henrymbalame222
    @henrymbalame222 4 หลายเดือนก่อน

    Kumwalira kwa Chimwendo Banda uku!,,,
    Wafa basi!,,
    After kunva voice yako!,,
    Zikomo kwambiri!,,

  • @LloydJamesMlanje
    @LloydJamesMlanje 4 หลายเดือนก่อน

    Zamanyazi😮

  • @Moudsmw
    @Moudsmw 4 หลายเดือนก่อน

    Koma aku zomba 😂😂😂😂😂

  • @HarrisonKalonga-k7p
    @HarrisonKalonga-k7p 4 หลายเดือนก่อน +5

    Chisiru iwe chimwendo anayamba ndi a dpp stadium imeneyo

    • @tasmania527
      @tasmania527 4 หลายเดือนก่อน

      A DPP amangoyamba zinthu mowaphimba anthu mmaso koma osamaliza, ndalama zitadyedwa. Amangokhalira kuyika ma foundation stone kuti anthu aziti akupanga chitukuko. Achina Mombera university anthu kumalipiridwa ndalama ngati aphunzitsi koma university palibepo. Pali zitukuko zambiri zomwe DPP inapanga chinyengo. Kodi anthu inu a DPP chifukwa chani mumasapota munthu chifukwa cha mtundu? Lozano zomwe anapanga Pitala. At least Bingu anatenga ngongole ku China nkumanga stadium, parliament ndi university ya MUST. Segulani maso ndipo muyamike zinthu zabwino wina akachita. Musakhale anthu ongomuda munthu. Chakwera has a vision ya patsogolo, and you will prove me right soon.

    • @PrinceBlessings-bv5bs
      @PrinceBlessings-bv5bs 4 หลายเดือนก่อน +1

      Ukunama iwe

    • @pemphokatembe443
      @pemphokatembe443 4 หลายเดือนก่อน

      ​@@tasmania527hahahahahahahahaaa

  • @JoshBranquinho
    @JoshBranquinho 4 หลายเดือนก่อน

    Kkkkk😂😂😂😂😂 malawi

  • @JerryUnyolo
    @JerryUnyolo 4 หลายเดือนก่อน

    Waziwa yekha kuti zomba yamukana 😅😅😅

  • @AminahMussah
    @AminahMussah 4 หลายเดือนก่อน

    koma Zomba ndilibe nayo mau 😂😂😂😂 ulem wanu ndithu

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 4 หลายเดือนก่อน

    Hi iiiiii koma ndiyetu msonkhano wakeyo ngt wa anatu, mukuona ngt anthu akuzomba ndowosaganiza eti? Nthawi yonseyi munali kuti?

  • @DumisaniMhango-e4i
    @DumisaniMhango-e4i 4 หลายเดือนก่อน

    Anthu 4😂😂😂

  • @ShalomShine
    @ShalomShine 4 หลายเดือนก่อน

    Koma ndiye kunali zi anthu😂😂😂😂 ngati ku birthday🎉🎉🎉🎉

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 4 หลายเดือนก่อน

    Palibe zonsintha zomba apa chitukuko cha mzani ichi ndichifukwa chake mizimu ya anthu 9 yakwiya

  • @lindaphiri3543
    @lindaphiri3543 4 หลายเดือนก่อน

    Kodi ndevu za white zi zili mfasho?