Am a Zambian I first heard of zeze when I was Game mall Lilongwe. I said this is the man that will bring Malawi Grammy. You really kill the Amapiano genre
JH re fjrgijrsbyaho BBB l GH lllllllllllll GH o GH osjsksl4hadkdjoshskskslshjshdhshskjshsjajelllshsjdjakhsksjslsooshsoskskgsoshpsosbdkuitugfufhjfkhigjhkhkyuoshiwosi😊❤
Alamu anu Lyrics
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
(Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu)
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
(Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu)
Ayiwala zonse, tinakambilana zija
Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Apeza wanyowani, avuta mma status
Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Apeza wanyowani, avuta mma status
Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Ngati ndakutopetsa Vuto ndi chani, osangondiuza
Koma kungochoka osanena, unangondiyuza
Ngati ndakutopetsa Vuto ndi chani, osangondiuza
Koma kungochoka osanena, unangondiyuza eish!
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
(Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu)
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
(Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu)
Ayiwala zonse, tinakambilana zija
Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Apeza wanyowani, avuta mma status
Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Apeza wanyowani, avuta mma status
Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Ngati ndakutopetsa Vuto ndi chani, osangondiuza
Koma kungochoka osanena, unangondiyuza
Ngati ndakutopetsa Vuto ndi chani, osangondiuza
Koma kungochoka osanena, unangondiyuza eish!
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
(Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu)
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
(Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu)
🔥📌
Wow
💃💃💃💃💃💃
Unapha Aixe ndiwe katundu
Umatha 🔥🔥🔥
Malawians let us normalise streaming local music, this tune deserves to get to a million views
Makfd
Makifd
Billions bruu
@@yamikanidavidKwanjanaMMJ; n I; 😅tvbgb ru by vyholll
. 😢imvvvc🧡🤦🍟🌶️🌶️;)B-):-!}:‑):-P}:‑)8-):-P:-$;😅(*_*)(*_*)(*_*):-[(TT):-\:0(っ.❛ ᴗ ❛.)っ(づ ̄ ³ ̄)づ😅😅jbojkllnlm LTL oeuk
1.1 million views !
As a South African where piano sound originated I APPROVE THIS! 🔥 🔥 🔥 🇿🇦
Thank you sooo much my king 🫶🏽🫶🏽
Zeze Kingston nd dolo his talent is appreciated beyond Malawi 🔥
You rock the guy.... today is a day i dig up about you... you made it boy.... takuladi movutika aaa.. i loke the song
Wooow
❤
Zambia 🇿🇲 approves sweet neighbor
It's only through music like this that i can travel the whole Africa upto Malawi from Uganda 🇺🇬🇺🇬.
Thanks Zeze
Can't get enough of this song 🔥🔥🔥 the beat is on point. Make more songs like this.
Alamwanu si nyimbo wamba 🤝🏿😃
Umakwana
Amayi anga ati ndiwe dolo Zeze!!!!! Tiyeeee Tiyeeee TIYEEEEEE
Tiyeni Tiyeni Tiyeni
I can't get the language but this is surely a hit
If u know u know
alumwanu alumwanu
2024 , and im watching this video for the first time. Genius
We have a star on our hands, Zeze to the world!
Bless up my guy 🙏
mutimaliza boss ehh
Zeze utipweteka eeh🔥🔥
hehehe
🇿🇼 Zimbabwe🇿🇼
Approves
Maita basa!!
Umakwana king zeze
Iweo sumphweketsa.... Haibooo
Am a Zambian
I first heard of zeze when I was Game mall Lilongwe.
I said this is the man that will bring Malawi Grammy.
You really kill the Amapiano genre
Mbambande
Amapiano Landlord uja ndi uyuyu 💃
Umakwana
Yomweyo galu iwe!!🙌🙌
O yes we are proud to have you may Man
Umatha aise. Big up
hit iyiyi ndi yachabe
umatha bro
Zeze kingston ke star***, I really like this song Alamu anu
Met Zeze at Queens Club in Mzuzu, what an incredible guy. Very humble and extremely talented. Malawi to the world 🔥🔥🔥
Nice meeting you bro. Thank you
JH re fjrgijrsbyaho BBB l GH lllllllllllll GH o GH osjsksl4hadkdjoshskskslshjshdhshskjshsjajelllshsjdjakhsksjslsooshsoskskgsoshpsosbdkuitugfufhjfkhigjhkhkyuoshiwosi😊❤
@@zeze_kingston❤
Nave 1 ❤❤❤❤❤❤❤😊🎉🎉🎉🎉😮
No😢😢
Chi Zeze adah🙌🙌
Eeeeh komatu Zeze ulibwino kwambiri & tsogolo lilimo ❤🔥
zikomo bwana
Welcome bro
Ipatse 🔥 zeze tikudikilaso Ina man
Zeze atisunga kwambil💣
Have no words now,,, munali kuti inu nthawi yonseyi Mr President!
Long live my bro , salute u🥰
Nthawi basi thank you
Zeze chipeza changachi ndavula umatha ase Malawi yonse King amapiano ndiweo 👏👏👏👏👏
Mulimbwanji
zapamwamba zeze..your bringing Malawi music to the world..big up breda
We are pushing fam thanks
Zeze munabwera... video nd audio zonse zili sexy
Umawkana
Ya nyimbo
From Zimbabwe❤❤❤ the vibe is dope
Mbambande!!!
Mmbale wabwera iweyo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Umakwana
Kayisibunandi bayo. Well done 👏 I'm proud of you
Big up zeze mwabwera inuyo osakomedwa ndi achina licias mupita
Galu iwe ukubwera bho🔥🔥🔥👌ipatse fire
Tiye nayoooo
I used to be a fan but after this masterpiece I'm now an air conditioner 😎
Zeze
Zeze Kingston wadza wabwera iweyo💥💥💥
Kuzakhala fada zikomo
Zeze Malawi Moto buuuu
Timvine za kwa2 kuno basii unabwela ngati coming
Yomweyo galu iweeee🔥🔥🔥
Lets gooo
Adha zeze utipwetekatu
South Africa Approves.... Had this banger from a friend`s car, damn Malawi goes hard on Amapiano
🙏🏽🙏🏽🫶🏽
Chaka Chino chako ase🔥🔥🔥💯
Blessings
Unaza zeze man🔥🔥🔥🔥🔥
Big up
Fiiiiirrreeee 💥
Tiyeni tiyeni tiyeni tiyeni brother
Inu tamupatseni Zeze chi thick mamie😩🔥🔥🔥
Chi Cash Madam😂
Was this a prophecy? 😂😂
Zed approved 🇿🇲🇿🇲 🔥🔥
#NyasaPianoTotheWorld 🚀🚀
Zanda zakuza
I grew up here in South Africa.. But am Malawian and I really love your songs bro
South Africa approves ♥️💃👌
Koma iwe aise...unali kuti kodi🥵🥵🥵🥵🥵🥵
Ndinalipo haha
@@zeze_kingston Ndiwe shata
My 3 year girl favorite song ,mamie yikani alamu anu
Seriously???
Mwaiponya kosafikira ana broo nice🇲🇼🇲🇼
Yomweyo galu iwe🤗🤗🤗
Usampatseee ndimpatsaaa
This man Zeze has true love 😘🥰. U deserve an award.... continue loving ur wife..
Mpatseni bwalo zeze wabwera kudzakhala 🔥
Fire team zeze paliponse
Mozambique approaves this banger
Iweo Zeze adha..uli fayaa🔥🔥
Umakwana
Yomweyo galu iwe🔥🔥🔥🇲🇼🔥🐐
yomweyoooo
@@zeze_kingston mumakwana fadar
Zeze you are the best really love your songs great job
ipase moto Zezé
Lero tikalezere malume
Katundu wabwino.. eeeh the alamwanu melody 🙌🙌🙌🙌
Zeze ipatse moto Rasta 🔥.... chi mfana chaku Malawi chiku chita kusangalasa kuchiona ...
Kingston malawian young stunna
Okay Kenny 🔥
From now onwards I declare this is the king of mapiano in Malawi has ever produced.
Aise umatha kwambr ndipo umandiwaza, ndipo its my dream kut this year tiweke one song
For sure bro
Wabwera iweyo
More fire🔥🔥
Daily ndimabwera kuzaonera alamwanu🌿💜💜💜💜💥
I like you voice brother and your sounds keep it up more fan's on the way one love
Zeze iweyo unabwera aise
Zeze for president 🎉
Love it haha
My future...our future....Malapiano💥
ichichi koma munapha madala zeze palibenso
tkumana pa waka waka
This is faya bwana
Na wow🥰
Watching from Johannesburg
Alamu anu alamu anu anangochoka alamu anu🎶 🎼 🎼🔥🔥🔥🔥..
Kenya Love
this is massive
Thank you Kenya
Yomweyo galu iwe usampatse ndimpasa 🤩🤩
Iwe wekha ndamene umasata how Amapiano vidz have to be like, mwaipweteka video🔥🔥
the guy has everything for piano since he was in South Africa so he knows how groove works like coz jonz everyday is a party day
Umakwana
Keep up the good work🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Zikomo
Kingz
Umakwana Zeze, wabwela kuzakhala iweyo. Nyasa Piano on repeat...🔥🔥🔥
Zeze Katswiristone.💯
USA 🇺🇸🇺🇸🇺🇸 approves!!!
Wayikokomeza zeze
Yaphedwa track
Zeze🔥
Zeze wabwera kuzakhala🔥Bar man mpatse 4 zeze, utatu ubwerere🥳🥳
Umakwana