Mic Mash - Superstar Remix ft. Gwamba, Temwah & Mfumu Hyphen (Official Music Video)
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 15 ต.ค. 2024
- / micmashmw
/ micmash265
/ micmash265
Superstar talks aboutchasing dreams and the burning desire to become a superstar. This song captures the excitement and determination to reach the top, but also touches on the fear of an untimely demise. Mic Mash encourages listeners to pursue their passions while cherishing life's precious moments. It's a relatable and inspiring track that reminds us to follow our dreams while staying grounded in the present.
Lyrics
Superstar Superstar Superstar
Kuwala nyenyezi mam'mawa
One day
Cause I wanna be a superstar
Heheee Yooh
Kutsegula TV Hyphen radio Hyphen
Koma a Malawi azamvelako nyimbo za ife?
Kuphusha ndikuphusha koma ngini ingonjanja
Fame sitiyanja madalitso si nyanja
Ndikufuna kutchuka mwina nkugula ka Demio
Munthune ndikukula nchoke den ya masten yo
Kuyang'ana FB ndione ngati anankambako
Koma kuti ndi trende ndimenye yanga anankabango
Koma kuphusha tingophusha sizutheka
Nyimbo zathu zogontha sizumveka
Ine nditani mulungu ngapange bwanji
Funa kutchuka ka ndikhale superstar
Ndili ndimaloto ambiri koma sindikugona
Ndimalimbikila nokha mutha kuona
Ndimakhala ndi mantha
Sizipezeka kuti nthawi yanga yatha
I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Cause I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Keep on chasing your dreams
All the times
Kumalimbikila kumaikapo mtima ndipo
udzakhala superstar
(Superstar superstar)
Hey Look!
Njira yake siyophweka umayamba ndikusochela
Kwina nkulimbika kwakukulu nkukondeledwa
Zitseko kutsekedwa osalephela opondeleza
Speak highly of yourself poti mau amalosera
Kuona komwe tachokela zoti ife tinkasekedwa
Nkanamvela bwezi loto titamezedwa
So I show up and I show out zonse zinalembedwa
Khama ndi maso mphenya pano ma level ndi ena
See you gonna feel it in you when you're chosen
Pano tinakhazikika mu game kumanga mudzi ngati goshen
I've seen doors open malo omwe tinkapempha kuti tikondeni
Heavy is the head, and it came to life everything that I've ever spoken
Don't let your spirit be broken
Ndili ndimaloto ambiri koma sindikugona
Ndimalimbikila nokha mutha kuona
Ndimakhala ndi mantha
Cause I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Cause I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Keep on chasing your dreams
All the times
Kumalimbikila kumaikapo mtima ndipo udzakhala superstar
(Superstar superstar )
for more information check out my website micmash265.com/
Ife amene tafika opanda link let's gather here 🔥🔥
😢
@@Allie196 mumakwanaaa🔥
Tonse we wanted to hear hyphens part let's gather here❤😊
Dolo hyphen ✅💪
Am here
Hyphen waika verse
Mfumu Hyphen..Munthu uyuyu ndi Dolo.
🔥
Hyphen my guy!! get your flowers! Katswiri kasanu.
Mic mash is one of underrated artist in Malawi. God bless everyone who has taken his or her part in this remix, Shout out to Gwamba apa mwa raiser Ghetto 🔥🔥
Amene taona hip ya Temwa let's gather here
Kkkkk ineo chandiwaza
#Hyphen iweyo ndiwe superstar ase🎉🎉❤
Mfumuhyphen never disappoints🎉GOATED
Gwamba ✔️
@mfumuhyphen
Temwa tunduma celebo😄
koma kuthoka facts Gwamba muli ma verse abho x mfumu hyphen 🔥🔥🔥🔥🔥💯
Mic mash iweyo ndi Dolo ase 🔥🔥🔥🔥
Hyphen hyphen hyphen hyphen hyphen hyphen hyphen hyphen 🔥🔥🔥🔥
Gwamba and Hyphen 🎉🎉❤ mwayigwira Malawi 🇲🇼
hyphen ndi amfumudi🎉❤
Ndli pano ndindan from Gwamba page 🎉🎉🎉
Wo!! MWaipha ma Guys. Big Up Mic Mash
Mash ndi dolo nde watengaso ma Dolo
MASH ndiwe dolo katatu
Hyphen yo mmmmmm😁bars.... Big Up Mash munkatiwaza life yanu pa MZUNI pano, ALL LOVE
Koma Temwa mawu kukongola Ngati waku India bwanji 🤔🤔
Live live
Hyphen amwene iih ✨✨✨✨
Superstar 🔥🔥🇲🇼🇲🇼.
Mic Mash to the world ❤
Kodi mwati hyphen you ndokwatira kale😫??
😂😂🔥🔥🔥🔥🔥🔥
What a coincidence! I was watching Davido's new song then i just jumped to this amazing hit. let's give respect to Gwamba and Hyphen for the amazing verses.
Gwamba osazamutola,the hit we needed✌️
A landlord adyedwa munyimboyi🔥❤Hyphen ndi GOAT
Gwamba, superstar GOAT
Eeeh Afumu Hyphen akudyan ma guy
Hyphen ndi akamuna. Machine 🔥
Gwamba ndi ShAsHa KaTsWiri 🔥🔥
Musandipomphoneze ndabwera kuzavela Hyphen
Ungosankhapo amene umakondayo.... Boys yapha
Asaaaaa km hyphen nde kuli uyuso muti gwambayo eee
Ati kumanga mudzi ngati Goshen.. 🔥🔥 Mfumu Hyphen
Nice tune man. Its rare kuvela nyimbo zabwino ngati izi these days
Eh APa sunganame Kt wina wapala zingotengela umafila ndan and hate yako uyika pat 😅
Hyphen nd dolo kwambir eeeeeeeh 🙌🙌🔥🔥
yaphedwa eeeeh mfumuyo eeeeh
Chi Gwamba 🐐 Chi Chimaganiza Ma Gaye 🙌🏽🍻
Koma chi hyphen mmmmmhhuu 👑🔥🔥🔥🔥
hyphen
Mfumu Hyphen ❤❤❤❤ Young kay 🎉🎉🎉🎉
Gwambizo chimfana Cha moyo💯
#Gwamba & #temwa inu ndiye ndi mado.........😂
Gwamba Goated the Song 🔥🔥 Amfumu kuyimba bwino ndikhalidwe lawo 🔥🔥Hyphen Murdered it too
Nyimbo ili bwino kwambiri
Mic Mash....you deserve four High Pineapples Ase
This is a dope song bro, I love it from its original version... Keep on Shining as a superstar my guy✊
AT FIRST, I THOUGHT YOU ONE OF THE ARTISTS WHO ARE IN THE GAME CUZ KWANU KULI NDALAMA KOMA I WAS WRONG GUY, MUSIC IS IN YOUR DNA ....RECEIVE YOUR FLOWERS ASE
Mfumu hyphen katswiri
Eeeeeish yaphedwa 🔥 🔥 🔥
Gwamba mn mmm yes
Hyphen!!!!😮😮
Amfumu Hyphen ndi Goat yawo
Koma gwamba adhaa🙌🏾🔥
We here waiting till nditavera mfumu hyphen kuti ayika ma bars anji
Ine kaya Gwamba anandipanga chani kaya..koz nyimbo yonse ndikangoona lake Dzina ndimapanga download
Dolo kwambiri 🔥
Good vibes 💯%
Ndee banega analiobeba alifanatu😂😂
Mmmhuu Massive Tune 🙌🙌🙌🔥🔥❤🙌
My mesho Mic mash❤
Superstar mic mash broo🔥🔥🔥
Ase Mic Mash, Eeeeh 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Hyphen ujayo eeee number 1
Remix ili poyenera❤
G.O.A.T met real G.O.A.T
Dolo kwambiri 🔥❤
Mfumu ndiyemweyo 🔥🔥🔥
Temwa's voice is so soothing! Once I have the means, I'll definitely book her to sing lullabies for my future children at night❤😅
Edit : Hyphen's verse, goated🐐
All in all, this song is extraordinary
Team hyphen where are you 🎉🎉❤
Hyphen eti🔥🔥
Young K eeeeh🔥
My brother....🔥🙌
Okay hyphen is the king who he thinks he is 🔥🔥
Dolo🔥🙌
Hyphen is always on fire he never disappoint
Hyphen ndi dolo amwene eeee
Superstar Remix ft Gwamba, Hyphen, Temwah now out on all streaming platforms! Subscribe to my channel , use the sound on Tik Tok and stream it on Spotify and all streaming platforms #superstar
One word for superstar remix?
open.spotify.com/album/7aF8ABf82LClPNauX5bQWC?si=qNPXEQEOS1yAEm4snF7jVQ
Hyphen eeeh💯🔥
Much power broh 💡💡
Bigup bro
#ma Superstar🤩
Hyphen Kodi bwanji iweyo umangotha All the time mmhh why you ?😂😂😂
Maguy ahiphop'wo Gwamba and Hyphen anali serious kwambiri 🔥🔥🔥
Lit 🔥🔥
A gwamba ma tatoo😂😂😂🙌
Eeh hyphen nd mfumu.di
Chaka chinochi ngat kwatuluka Hit ndiyiyi 🔥🔥
Okay mash ✅
Chigwamba chija cha chabe
Gwambixo again🔥🔥🤟
Shoo🎉
This truck is on fire 🔥
Dolo🔥🔥
Well created song 💪
I used to love macheza but this one eeeeh 🎉🎉🎉🎉 inspired
Komatu 🔥🔥🔥
Big moves madhala Mash🔥🔥🔥
Gwamba and hyphen 🙌🔥🔥
I wanna be a superstar
Superstar 🔥🔥❤