I would like kuti labour team should also taken into accountable on this anthu awawa satithandizanso ogwira ntchitofe. Malawi tikuvutika dziko lathu lomwe.
Eeeeeh zomvetsa chisoni koopsa eeeeeeh. A Maliwa akufunika kulipilidwa zenizeni coz chigamulocho ndiye sizikugwirizana eeeeh mpaka kumubowolo koma mpaka munthu kulumala ichi ndi chipongwe
Muzangowasintha mademowo azachitikile ku mangochi kuno kapena ku BT azikwanjewo sangazalepheleseso angakumane nda azikwanje azawoso ku mangochi kapena ku BT kapenaso zomba basi
Ahh mukumazatifoola a Namiwa simumapezela monga atsogoleri mumayenela kukhala oyamba kufika palo amademo. Koma inu kulankhula nde mukulankhula action nde ikufunika bwana kuti tikukhulupilireni. Pano mwayamba kuti kaikitsa. Mukuoneka a mpeni walezela. Come pa ground before we completely loose trust in you
I have a lot to say that is why I use voice note to explain everything 😔🥲 just duoble tap to hear the voice.
▶︎•|၊|။||||။၊|။|||။|||။ 09:53.
That's a way to go. a Malawi tisamafinyike mdziko mwathu muno
The way I like you Mr Namiwa just because of your justice ❤😊😊
Mr namiwa ndinu munthu wachilingamo Mulungu akudalitseni, Mulungu azikutetezani kwambiri ❤❤
I'm following
Following Namia ,,, anthu okuda ndife anthu omvetsa chison 😢image kumenyedwa kotere anthu kungopondeleza just like that?
Nice keep it up
GOD WILL always protect u sir
God protect and bless you Namiwa
De great man I like u
Mumakwana namiwa tili limodz osanyengelera
265😂😂 mwabwelamonoet ayi welcome back
Namiwa❤❤❤💯💯
Cadet iwe pamsana pako
😂😂😂😂😂 munthu wa mantha uyu amabisala ma demo asanayambe 😊😂😂😂😂😂
Moyo sagula ndindalama abraz
@@SliviaJosephynde asamayankhule cos timamukhulipirira
Ndipo live
Ndipo ngati ukunama
May God, keep protecting you Sir Namiwa
Umatha aise keep it up
Big up brother Namiwa
Zikomo kwambiri bwana Namiwa chifukwa choima pa chilungamo
We appreciate your stand to fight for Malawians
I would like kuti labour team should also taken into accountable on this anthu awawa satithandizanso ogwira ntchitofe.
Malawi tikuvutika dziko lathu lomwe.
Namiwa keep it up!!!
Odana ndi Namiwa ndi mfiti
Katundu namiwa sopano
Medical Council of Malawi sinyengelera munthu, eee iwe unalemba report ili licence yako yapita, komatu school ija njowawa. Sorry in advance.
Namiwa keep it up
Cdedi mumatiyimilila
Koma m,mene ziko la malawi likuyendelamu munthu wina kumati boma ndilomweli kkkkk
Namiwa ndi munthu waserious ndipo ndiolimba ntima
Tili okozeka kupita pasewu ziko silibwino
Mulungu oziwa kudalisa adalise inu mr namiwa
Komaso fusolnga ndilakut.
Kod nthawi imene president akulumbilitsidwa pamakhala kuvomelezedwa kut anthu azigulilidwa zinkwanj kamba kosokoneza chilungamu?
Fuso mkumati Kodi kumalawi ma radio 📻 anatha?
Namiwa Allah adzikutetedzan kwambiri kulimba mtima Kwanu kupulumutsa Malawi mmanja mwa njoka
Ntchito Ndimuntengo osamatumbwamukakhala pa Ntchito
Namiwa umakwana ndiwe mundu olimbatima nga the dic bhoni kalindo osafoka osatopa osaopa tiyenawoni
Za ziii awa amangodziwa kuyankhula koma kumademo sapezekako
Mukayankhula nanumso mudzipezekako
Zoona
Mmmm Inu zisiyeni mwayankhula zosamveka
The Lhomwe people
That's way to go
Kkkk atolankhani kukanika kufunsa mafunso koma namiwa ndi dolo katatu
Timakunyadirani a namiwa
Eeeeeh zomvetsa chisoni koopsa eeeeeeh. A Maliwa akufunika kulipilidwa zenizeni coz chigamulocho ndiye sizikugwirizana eeeeh mpaka kumubowolo koma mpaka munthu kulumala ichi ndi chipongwe
Bwanji tathamangitse azipita kwawo,coz atimangir ka msewu kosalimba kaja azitizuza? I wish Bingu was alive.
Koma inuyo bwana simunthu wamba ayi chonde mubwele ku ma transporter muzone momwe akutizuzila ma truck driver ife
Amwenye aku India akupangira nkhanza anthu mu Brantyre Limbe ndi malo ena muno mmalawi. Commenting yangayi iwafike.
Kodi bungwe la CIDED,ndi lamunthu m'modzi? Nthawi ya achina Mtambo timaona kagulu,monga Trapezi ndi azizawo.koma awa amangooneka okha,kkkkkkkkk,bungwe kapena mutu wa banja?
Chingoyambisani chipani mukhale president tione ngati uzakhale president. Iwe mbuzi ya munthu
Zomwe mmapanga zimatikaikisa akulu inu
Nanenso
Amalawi anzanga khondoija yayambanotu nanga anthu obwela ayamba kutiphwelekatu Ife km nzikomomo muli police ?
Kape iwe
❤❤❤❤❤❤❤
AMalawi enadi ndi odabwitsa. Timagwirizana ndi amwene plus ma China nkumazunza aMalawi anzathu. Kupusa kwenikweni
Kodi tinene kuti amalawi ife ndiopusa kapena chani. Maka mbuzi zomwe zili mma office aboma. Nchifukwa chani timawatenga anthu oyera khunguwa ngati milungu?
Namiwa ndizomwe ndimadikila tikufuna mademo
Kod atolankhaniwo amafunako chani ngat safunsa mafunso deemete man
Muzangowasintha mademowo azachitikile ku mangochi kuno kapena ku BT azikwanjewo sangazalepheleseso angakumane nda azikwanje azawoso ku mangochi kapena ku BT kapenaso zomba basi
komano zopusa zomazuzika in our own nations ndzopusa kwambiri
Nanga mathawiranji?
Ahh mukumazatifoola a Namiwa simumapezela monga atsogoleri mumayenela kukhala oyamba kufika palo amademo. Koma inu kulankhula nde mukulankhula action nde ikufunika bwana kuti tikukhulupilireni. Pano mwayamba kuti kaikitsa. Mukuoneka a mpeni walezela. Come pa ground before we completely loose trust in you
Chikangawa asowe
Choka iweyo ifeyo tilipambuyo pa boma lomwe lilipoli we❤mcp za ziiiii za namiwa zopanda mchere.
Machende anu akulu mwamva ,mwana wachakwera iwe
Inunso ndambuli bwanji apa pakambidwa zakwentere wakoyo
Opanda nzeru ndi iweyo ndi chakwera wakoyo crocodile team imeneyo yakupha zasatanic zamagazi muchoke mcp nonse ndi ma carward mbuzi
@@ThandiweKandoje-d9j talembani zanzeru zoti tikawerenga timve chomwe mukutanthauza
@AlicksonMakata usamati ife uziti ine, Koma anthu ena simmaganiza mmene malawi wavundilamu wina nkumayima pachulu ndikumalankhula mwauchitsilu choncho? Ngati sindiwe mfiti kumanda kokha umapita kukagona
Yolamu waononga police yonse chibwana basi
Tiyeni pamuseu izizitithandiza
Namiwa ndiwe katundu
Ndipo live
yambitsa genocide tione kuti atathepo ndi ati
Mr namiwa nkhani imeneyo i mean yozuzikayo kunonso kulilongwe pal kampani inanso
Itchuleni baas osaopa
Mbambande
NAMIWA USAMATIPUSITSE TINADA NAWE KUKHOSI IWEYO
Bola zikhala zenizeni
Kutiziwitsa komanso kutiyankhula nde mmatha....koma Action nde 0/10 aaaaaah mmangowasiira ma followers
chitsiru iwe galu
Sichitsilu ameneyu
Chisiru ndiweyo
Eeeee
Welcome our freedom fighter comred namiwa
Namiwa chitsiru iwe
Machende anu akulu mwamva ,chitsiru ndiweo mwana chakwera
Koma ku Nyau camp kwawoko ndie akupusatu@@TriceBeib-e6x
Mbuzi yamunthu imeneyi umatumidwa ndi DPP
😢😢😢 😢 😢
Big up Mr namiwa
Mutinenereko anamiwa chadula chimanga