Nkasa walosera zoona palibeso.Joseph Nkasa ndi machine! nyimbo wayibandula munthawi yake.Dr Lazarus maccarthy (Deliveror) ndi chipani cha MCP wachizozelathu Joseph Nkasa ndi mafuta amzimu woyera,zipani zosusa ndi zongoperekeza,Amalawi avomeleza muziko la uzimu ❤❤❤❤❤❤❤
Mkasa asanenedwe iye ndi WA business yoyimba ngati dpp udf afford alephera kumupanga ambassador mkumupatsa salary ngati kontalakiti iye Ali ndi ufulu opanga business ndi anthu ena ndipo posangalatsa kasitomala ayenera kuyimba zokomera kasitomalayo ,voti ndi mumtima bola iye akalipire fees ya ana ake
Nkasa km mumaganiza ? bwanj amwene nyimbo imeneyi achibale anu km akusangalala nawo? Mulungu akuyendele mwapadela ndipo mulape kwa mulungu mwaimba nyimbo yokwiyisa mulungu akulangani ankasa mwalakwa anllah sanakondwele nawo nyimbo yanuyi akulangani ankasa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Great composition. Zinazo tikidziwa tokha kkkkll
Ndimaona wina aliyense akulira😢😢😢
Ndikamvela nyimbo zamafumuwa Oro nditagona ndinjala ndimazuka ndimphavu
Nkasa ndi machine ❤😂Nyimbo ndaikonda
Kodi akuti chani munkhaniyi sindikumvesa bwino bwino.David wake yuti nawe nkasa
Nkasa walosera zoona palibeso.Joseph Nkasa ndi machine! nyimbo wayibandula munthawi yake.Dr Lazarus maccarthy (Deliveror) ndi chipani cha MCP wachizozelathu Joseph Nkasa ndi mafuta amzimu woyera,zipani zosusa ndi zongoperekeza,Amalawi avomeleza muziko la uzimu ❤❤❤❤❤❤❤
Mkasa asanenedwe iye ndi WA business yoyimba ngati dpp udf afford alephera kumupanga ambassador mkumupatsa salary ngati kontalakiti iye Ali ndi ufulu opanga business ndi anthu ena ndipo posangalatsa kasitomala ayenera kuyimba zokomera kasitomalayo ,voti ndi mumtima bola iye akalipire fees ya ana ake
😂😂😂 nkasa ndi mfana othananga.
Ndpo zoonadi
😅😅😅
Mkasa sayankhula zaboza, Mkasa amawerenga mita.Chakwera wachitadi chitukuko.
Listening to a song from Lusaka Zambia, it's a good song though
Beautiful song chabe Kut waimbila mfiti mmanja..😜😜😜
Chosadziwa anaimbira mfiti mmanja😂😂😂😂
Nkasa yemweyo
Let's call a speed a spede Mkasa is a musician with his own unique lyrics worth appreciating! Keep it up Bwana Nkasa
The Music Ambassador Of Malawi Phungu Josephy Nkasa the Great Conqueror ❤
Komatu athuno ndinu panda chino waona athu Amene akulha chitedze kumeneko. Ndalama zikuonongani azinbambo 225 mulungu asitha zithu.
Very honest truthful song .koma poti kumalawi kuli ndale osati politics enawo sangavomleza
Chakwera ndi Davide❤❤❤
Ankasa nsabwe yoyenda yenda imakumana ndi chala tithokoze kuti mumatenga mayina a bible kufaniza ndi zinyawu😂😂😂😂
Ndipo abale
Mkasa uzitenge bwino potchula maina a aneneri kumapaka nkhumba zachabezi
Ndipo iwe nkasa mmm
Koma ichichi ndi machine komanso Yudasi... He is just doing business osamutengera
Well done Mr.Nkasa keep it up!
Mkasa ukutenga ma chase,,,,agula chakwela yemweyo nyimbo imeneyo
Ndipo azigulana wokhawokha a mcp
Uyu wapweteka oposition ndipo mabala ake ndiovuta kupola❤❤❤
Ndalama idampachika mwana wa mulungu osalakwa zowona 😢😢😢😢😢
Phungu Joseph ndiwadyera what's why athu anamumenya poyamba
Ndipo anamuswa pangono but this time atibulidwa zeni zeni@@andrewchirwa2193
Uyu akafuna kuyamikira amatha ndipo alibe jerasi.
Kodi a nkasa mwaiwara zija munayankhura pa cruise 5 ndi Joab chakhaza? Ndinu nokha munatemesa nkhwangwa pamwara kuti simzaimbaso nyimbo yochemelera andale poti ndiomwe akusaukisisani ndikukuonongerani sogolo lanu
I like the song brave #mkasa boma ndilomweli❤
Kwanuko otsati kumalawi zigawenga za MCP 😏
Nkasa km mumaganiza ? bwanj amwene nyimbo imeneyi achibale anu km akusangalala nawo? Mulungu akuyendele mwapadela ndipo mulape kwa mulungu mwaimba nyimbo yokwiyisa mulungu akulangani ankasa mwalakwa anllah sanakondwele nawo nyimbo yanuyi akulangani ankasa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nyimbo yabwino kwambiri
Boma iloooo
Nyimbo beat yabho kumayimbila za chipani😂😂😂
A Nkasa musaiwale momwe kuliri kumudzi Kwathangala kuja pano anthu Ali ndi njala mutumize chakudya pano akukumba mzimbe
Mutu wake ndipachabe uyu akufuna ndalama ndamuona ndimantenga ngat oimba wa mkulu koma network inathawa
Koma Nkasa😂 amatha kuyimba.... Samakwela yokuphwa...
Nkasa umatha kutamandira andale Mr change golo. Uladi musa weniweni
A Nkasa sakudziwa kuti ma plani a zitukuko zomwe akutsekulila a chakwera kapena manga ndi za DPP ndi APM
Nanunsotu ndinu osokoneza, abwere uyu, muli komweko, akabweranso uyo, muli komweko, muli mbali iti kodi
Mwatiyankhulira kwa anthu osachedwa kuiwala😢anzathu ankachita kusowa mtendere ngati dziko silawo ili😢pano akukhala ngati aliyense 🎉 4:55
Mutsamamulakwire peter,timaphana tokha tokha shupt people
Nice song, koma chakwela sakuwinanso😊😂😂😂
Mukulota big. Mavoti a Chakwera ndi migolomigolo. Ubwino wake voti ndi pa ground osati pa internet.
Mmmmmm, osiya ndale aja, nkasa ndi wa dyera
Koditu anamuswa pangono
Umphawi unakukwana mkasa uthera mu ndale momwemo palibe tsogolo apa.
Nice song mkasa
More fire munthu wa mkulu
Nkasa God may bless you ( machine)
Mzafa ifa yopweteka inu a nkasa ndinu achisilu
nkasa machende ako
Washing from Cape town nice song
Mkasa koma uliboh❤
Madala madala a wawa sadzatheka!
Wamasagwidi wapenga misala uyu
Pansana panu boss
Nkasa iliyonse kukwela ukufunsa kusochelesa anthu
Live Nkasa alone
Ngati zakuwawani pekani yanu nyimbo
Uyu akanachosedwa manu ,wanati asogoleli ndi osafela lelo chamuona ndi chani ndalama makwacha 3 ponyela pako mkasa akusowesa iwe , Dr chikangawa
Nkasa vuto siweo komano umphawi wakowo ndi kupepela kwakoko
Koma Ada mumatha
Nkasa ndi dolo man. Kuti azivutika simungamuthandizenso ayi.
Ndi davide chakwela wapweteka wotukwaba wose nkasa mcp woyeeeeè❤❤❤❤❤
Kkkkkkkķkkkkkkkk mwana wamamuna kuzisaka pa capital
Awa ngosata ndrama bas
Kaye kusamufanira zomvala za China hhhhhh😅😅😅😅😅😅ichoooo
Iwe wausilu kwabasi 😂😂😂
Uyuu ndichifukwa amamenyedwa 😅
Uyutu ulendo uno anthu akangogwira apha otsati anachotsa dzino zija
Iwe ndi mbudzi yamuthu Maka umasaka chani mdzibambo oputsa
Honesty. More fire
kodi akumapeleka zigati nane diyimbe yanga
Chosaziwa ijanso unapha ase
Zaziii chitsiru chamunthu pita uko ndi chikangawa wakoyo achitapo chani pa malawi kumapha anthu basi
Ndipo misewu akambayo yopita kumatako machende ake ndithu mkasa
I love this song❤❤
Chikangawa ndi chakwera davite
Uyuu ndi galu uyuu alibe mbali iyee bola ndalama uja ankati chakwera munthu wamulungu walowa ndale pano akungowelenga manovero uja ndiyemweyi uyu.
Nkasa ngati ukufuna kudedwa ndi anthu ulimbikire kusapota chikangawacho,iwe sungamve chisoni mmene anamuphera chirima mmmh,usogoreri okanidwa ndi mulungu mulengi ngati usogoleri sanauvomeleze amango peleka ziphinjo wazichulazo,siukuziona
Koma nkasa okaramba akudandaura iwe akt kod siungaimbe nyimbo yomuzuzura chakwera chimene ukuyamikira iwe ndichan
Nkasa machende ako!!
Wayiwala ako
Achitsilu awa amangochemerera zilizose alibe mbali uyu chifukwa amangomenyebwa be like Dan lu
🎉🎉🎉🎉😂😂😂😂Ndipot live mbuzi yamunthu
Take it easy mwabwana munthuyu ndiwoyimba zandalezo tazisiyenikaye uko
Nyimbo chaswa🔥🔥🥰
wawonjezatu koma 😂😂😂😂😂😂😂
I don't agree koma I just like the song 😂😂
Ulibho
Mabatile ako iwe akupatsa dola kuti uyimbe zopepelazi apa et
Phone yanga sikumveka sound nde ... No comment
Ndimaona ngat mkasa munthu mwake zimayenda Koma iyaàa uyu sigwila
Mutu wake ndipachabe akufuna ndalama bas
Munthu uyu amandisangalasa ndipo posachedwa ayimba yoyamikila dpp ndipo izatisangalatsanso
Amkasa muzalira sure
Ndi chifukwa chake amamenyedwa akulu akulu
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Man nyimbo imeneyi sitchuka kamangati lilikwilu yandalama koma mwayiponda😂😂😂
Ndiyomwe ndimadyela
Mesa mumat andale diwoyipa kod 😅
Kkkkkkk kmno this track muli bodza kkk
Mkulu maganizo anu adakali pompaja kapena mwasintha chifukwa nde zinthu zasolobanatu yakwiya ndi mizimu
Kusendedwa zikopa ngat mbuzi 😂😂😂
Katswiri Nkasa ❤❤🎉
Achisiru awa nzeru alibe
Dzeru alibe uyu,,akufuna kufa ,,koma ine ndimadabwa ndi anthu oyimbawa lutso lawo limathera kundale ambiliwa why
Dyela nkulu uyu amangofuna ka ndalama azikadyela panyumba ndi ana basi
Ndani safuna ndalama
Mkasa ndioipa
Eya wabwino ndiwe
Yooo david
Ndalama zizakuphetsa akasa
Kkkk koka mkasayo
NKASA Dyera
Ankasa umphawi ukuphesan
Komano malume. Apa ndiye mwasokera. Aaaaaaa😅😅😅😅
Mkasa njimbo imeneyi atagure Ambwiyako ndinthu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Nkhani ndi 50+ 1
Azakhala davite gat njala igathe
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 km awawa nde kufuna ndalama kwawo kwaonjezatu kkkkkkk
Yakubayanitu yimbani yanu basi
*Mose wa lero* ija ndi 1, izizi nde ayi