Symbol ya UTM ya kandulo ichoke pansalu, candle umayatsa pa nthawi yachison if simukusamala aliyense otsogolela UTM adzifa tragically coz of Symbol. Save this message. It's better muike bulb or lump not candle, This is spiritually revelation
Munthu chifukwa chot ndiwachipani cha DPP Basi wapezeka pansonkhano wa a president n akupempha ndandizo la anthu akudera lake walakwitsa? Ai Basi akupatsa ndalama kut apange indonse chakwera?? Mmm inu Nde andiinu achitsiru kwambiri
Mr president bon kalindo will trust you all over more god bless u 🙏 DC
Bon kalindo God ahead u my bro
Bwana Kodi simutipatsa ng'alulaization ya madzulo???😅
❤❤❤❤❤❤
Mbambande
Awuzeni bwana kalindo uthengawu upite kwa peter muthalika ndamene tikumufuna boma pano batsi
The Dc
Shame on u mr kalindo
Symbol ya UTM ya kandulo ichoke pansalu, candle umayatsa pa nthawi yachison if simukusamala aliyense otsogolela UTM adzifa tragically coz of Symbol. Save this message.
It's better muike bulb or lump not candle,
This is spiritually revelation
MCP ili Pa ground kutipula osayamba zomanamizira kuberazo ayi….Kodi team ya APM, Mukhitho ndi Chisale ingathamange kampeni? Be serious guys 😂😂
Munthu chifukwa chot ndiwachipani cha DPP Basi wapezeka pansonkhano wa a president n akupempha ndandizo la anthu akudera lake walakwitsa? Ai Basi akupatsa ndalama kut apange indonse chakwera?? Mmm inu Nde andiinu achitsiru kwambiri
Chakwera mapwala uyu satana kwambiri kodi amalawi ife kungona koteleko chifukwa chani
Yamikirani zomwe president akupanga inu osat kumangopa opposi owez mmmm tamankhalaniko ndimanyaziii, DPP ikupusitsani don't b racism alomwe inuuuu
Ayi tiyamikile anagwila ntchito yotamandika ku chikangawa president wakoyu. CHIPHE chakochi. Gwape komwe uli iweko kaya ndiwe mtundu wanji wamunthu
😂😂😂😂😂😂😂@@Kabwilachikangawa
Koma nawe galu Kala chethe apa mbjnzi yamunthu iwe