For nyimbo ndimanala basi,, zinazi ayi,, utati aaaaa from my angle,, mukungochuluka ng'oma,, voice Yako ndi mene ukuyimbira, mene zikumagundira ng'omazo, sizikumada,, ndiwe arst wa booh koma vuto I think uli pa changu.... Take your time, uvereso mabala,, ,coz utayimba mabala, nyimbo zose ija,, kwinako voice Yako inayamba kupepuka like ndimumene ikumagulira bit sizikumacha... Hop u get it,,
You are moving up from KACHINANGWA local studio now at one of the competent producers I like you Phalombe Guys you are pushing our local music fusing it with Morden beats
Fried Mw umatha iweyo ndi 1🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️
More love from Zambia 🇿🇲 you remind me of Thomas chibade bros my first artist I knew from Malawi
A
Keep it up brother u gonna havest what ever u planting
For nyimbo ndimanala basi,, zinazi ayi,, utati aaaaa from my angle,, mukungochuluka ng'oma,, voice Yako ndi mene ukuyimbira, mene zikumagundira ng'omazo, sizikumada,, ndiwe arst wa booh koma vuto I think uli pa changu.... Take your time, uvereso mabala,, ,coz utayimba mabala, nyimbo zose ija,, kwinako voice Yako inayamba kupepuka like ndimumene ikumagulira bit sizikumacha... Hop u get it,,
❤❤❤ Ine ndisaname nyimbo zako zimandisangalasa kwambili
AMATHA ADHA AWA NDI SHASHA
You are moving up from KACHINANGWA local studio now at one of the competent producers
I like you Phalombe Guys you are pushing our local music fusing it with Morden beats
Uki ndye kubwera 🔥🔥🔥🔥
Nice visual njira n sound❤❤❤
Mbambande ❤❤
❤ ulimwala njila
Ndiwe dolo aise 🔥🔥🔥
Maaaa❤❤❤
Mbambande 🔥🔥🔥
Nice Asiyatu (Mrs Ching'aning'ani) umayitha
Fred always want problem apo ndiye wamuputa ching'aning'ani zoona wamulandaso mkazi kkkkkk
Salute bro umatha iweyo kept up
Fred 🔥🔥🔥🔥🔥
Umandiombila bwin ase
Anjira 🔥🔥🔥
Fred wabwera ngat cyclone❤
Fred vote yanga ili mwa iweyo 2025 😂😂😂😂
Umakwana ase❤
Asiyatu Mayi chiphwanya in tonde wadula is a model eti
Nice Njira
Mumaitha ❤
Njira kuwalako mumatha big
Congrats brother
Mbambande njira
ndewy one
Well done ❤
Fred ur still going up respect
Umakwana 🔥
Uli bho ase
Wawa koma zikutheka big
Udabwera🎉🎉🎉🎉
Zilibho bro
Mbambande milonde
Nice one broh.....big up to you
umatha iweyo
Nice song
🎉🎉
Sumuopa ching'aning'ani Koma mbambande
Komano beat yo nde izathera ma penalty ndendende
Very true.. Mr Too froz anakopera kwambili, 😮
Big up
Koma iweyo
Nice
Thanks
Milonde maaa
Like mabala ija umayidekhera bobo, kena kalikose kanali pamalo pake,, koma kwinaku ukumathamanga heavy,, zinaso sitikumaba, tima off tikumachulukaso
❤❤❤😂
Ndiwe dolo aise🔥🔥🔥
Excellent
Thanks