Ambuye azikhala nanu
❤❤ yachuta
❤❤
❤ Mereka ndi nyooo
Moto kuti BUUUUU
Inuyo ndi mbambande, pitilizani kutisangalatsa, we love ur music
Yashutadi❤😂
Moto 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nyimboyi muli matanthauzo obisika ikufunika kuinvera modekha Evance meleka ndi katundu
Mwaikwapulatu mbuyache
Iyiyiii ND 🔥🔥🔥
Ukutiyimirira
mwaipha fadah
Praise the Lord ❤🤝👏🙏
Koma abwana inuyo inuyo inuyo, mumayitha,pitilizani kutisisimutsa,we love u
Yashuta we love brother ulemu