MMALO MOTSITSA NFUNDO CHIMWENDO AKUNGOLIMBANA NDI DPP - WAKU 2025 ZILIKO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 4 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 43

  • @BonganeZulu-i6w
    @BonganeZulu-i6w 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    A aaaaa inu a chikangawa mulibe mfundo, mamina mmutu Ali thoo ooooh, makape

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Amalawi Ake womwe agwilizanawo NDI akum'nyini kwakoko

  • @LimbaniNyika
    @LimbaniNyika 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chimangacho chikugawidya kuti kkkkkk koma malawi will never change

  • @francismuwa2535
    @francismuwa2535 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Chabwino nthawi ya DPP economy simayenda bwino koma nanga Sugar ndi Fertilizer zinali pa mtengo wanji?? Leroli munthawi yanu Sugar ndi Fertilizer zili pa bwanji??

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    MAYI MWAKALAMBATU MUKULANKHULA MOBANIKA

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mcp sikungona tulo chifukwa cha DPP ndipo muziwe kuti simungamake mwachepo ndinu ana kwambiri

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mwandikumbusa adadie mulilongwe town ataima pa mzikiti eee kunali gurutu size 😢

  • @LimbaniNyika
    @LimbaniNyika 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chikangawa party mmmmmm ulendo wanu obera amalawi ukutha chaka chino

  • @LimbaniNyika
    @LimbaniNyika 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Nkhani ya ku chikangawa siinathe mzikumbukira msaiwale

  • @FrankPhiri-k6y
    @FrankPhiri-k6y ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndachitsirudi awa dpp sikukugonetsani tulo

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndipo mufunemusafune DPP ikuwinaso ife ndi ana adadi chakwela simuthu wabwino ayi wamupha chilima tikuona ife

  • @edsonndalama2334
    @edsonndalama2334 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Moti zoona wina lero nkumati nthawi ya DPP economy siimayenda bwino koma pano ndiye economy ikuyenda bwino eti? Mwina mbali imeneyo ikuyenda bwino koma kuno ndiye sikuli bwino.

  • @robenallie6985
    @robenallie6985 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ngongole bwanji yachuluka, amai inu ndi chitsiru kwambiri

  • @PreciousSteven-e5s
    @PreciousSteven-e5s 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Mmai iwe panyini posasapo

  • @fatsankapitikitsa
    @fatsankapitikitsa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    shemed and shemed

  • @Martinmkapangakapanga
    @Martinmkapangakapanga 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    anthu ambili akunthawa ma koma mulibe chakudya ana akuwavutisa mwina angapeze zakudya zakudya zonse zinapita ndi munthalika ndiye uyu zakudya zonse wayika nyumba yake

  • @LimbaniNyika
    @LimbaniNyika 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Tikufuna commission of enquiry osati nyasi zanu a mcp muziona 2025

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi nyamata okuvotela inuyo asisadikila chani kwainuyo kwacha yongogwa dayile

  • @CorneliousKaliat
    @CorneliousKaliat 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi Kani ndi athu aja mumawatenga mmagalimoto

  • @ConfusedFlamingo-tu9gz
    @ConfusedFlamingo-tu9gz ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mcp ndiyomwe ikulamula ndiye sikugona bwanji.DPP ndiyomwe sikugona ndi zitukuko za Chakwera.DPP mfundo nje nkhani chirima basi

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Manyazi mulibe mai Mulungu akuona ndithu. Mukachoka pamenepo muzikaonetsa maliseche .

  • @FrankKabichi-f5e
    @FrankKabichi-f5e 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Athu okuphaa

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbuzi za amalawi.....i hope onsewo akhuta....panya panu

  • @GumuleKandawala-g7k
    @GumuleKandawala-g7k 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kupusa dziko mmene likuwawilamu Inu mkumayankhula choncho

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mcp boma ndipo yasitha dziko ndipo zozembetsa ciment zimatha chitukuko chimakhala kimwera kokha pano sakusakha

    • @LimbaniNyika
      @LimbaniNyika 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Koma amalawi muli ndi nzeru?

  • @MoosaSidrick
    @MoosaSidrick 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zautsilu zamanyi

  • @ChrispinBanda-s9p
    @ChrispinBanda-s9p 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Jese kabwira Mai onunkha kumatako komaso mavuzi sadziwa kumeta

  • @WisdomJeremiah-s3y
    @WisdomJeremiah-s3y 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Palibepo chanzeru pa chakwera

  • @SleepyBurger-ry4ti
    @SleepyBurger-ry4ti 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akazachoka pampando onsewo ku prison bas atitora kwambiri panyero panu anyani 😜😜

  • @RodgersKawonga-c1i
    @RodgersKawonga-c1i ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uzavota wekha mbuz iwe uzaziwona kuwawa thaw ikazakwana 90mis pa ground

  • @emmanueljelemani4203
    @emmanueljelemani4203 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Dikirani 2025 you will be ashamed

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Eweyo yako idzathana ndi ya mdzukulu wanga koma yanga adzawinira

  • @dymonikwanga-fq2hz
    @dymonikwanga-fq2hz ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zopusa kungotithera bundle.tingadye musewu kapena magesi ? .pangani kale. Za omwe akudya chitedze uko

  • @UmaliIshmael
    @UmaliIshmael 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akulu awa ndioyipa kwambili

  • @atuswegheKabangoAkayce
    @atuswegheKabangoAkayce 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dziko la anthu odzindikila ochepa

  • @BenitoBanda-e6j
    @BenitoBanda-e6j ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nanga njala

  • @KennethMugabe-f9l
    @KennethMugabe-f9l 4 นาทีที่ผ่านมา

    Zaziiii

  • @jackalview7491
    @jackalview7491 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mudzadziwa Chaka chamawa

  • @UmaliIshmael
    @UmaliIshmael 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inu nde mulibe mabodza

  • @ChizzaNkhonjera-k8y
    @ChizzaNkhonjera-k8y 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zauchisiru basi

  • @SleepyBurger-ry4ti
    @SleepyBurger-ry4ti 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pamtumbo panu anthu a mcp nonse mulibe nzeru