ZIFUKWA ZIMENE BON KALINDO WAMANGIDWA KAWIRI MU TSIKU LIMODZI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 25 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 28

  • @WilsonLimited
    @WilsonLimited 6 หลายเดือนก่อน +5

    Apolicewa bwanji tizingoponda tokha guys kumalawi kulibe police kuli mcp security machende abambo wao chakwera

  • @FloneyKawina
    @FloneyKawina 6 หลายเดือนก่อน

    Aaa alibe zochita apolice awa zaziii, kalindo ndi dolo ndipo GOD is always with you be strong brother

  • @robertbanda765
    @robertbanda765 6 หลายเดือนก่อน +2

    Ine ndifunseko Inu abon kalindo chimene mukupondulapa nichani pamenepa, komaso ma audio Anu amene mumatulutsa aMalawi amapindulapo chani akamawavera, Kodi simungayambe kutumikira mulungu monga amachitira mtumiki twaibu yemwe anali mkunja kwazaka zambiri ,koma pano akupulumutsa miyoyo yaanthu kupereka chiyembekezo kuwanthu , mumudziwe yesu lero ,yambani kutumikira mulungu noti kulimbana ndizadziko nzachabechabe kulibe chimene muzapindulapo.

    • @Jermah51kennias
      @Jermah51kennias 6 หลายเดือนก่อน

      Ulibe nkhani zoba iweeee

    • @williammenard48
      @williammenard48 6 หลายเดือนก่อน +1

      Utumiki sufana

  • @DwartNgona
    @DwartNgona 5 หลายเดือนก่อน

    Nkhani zabodza, mawu ngatiwathimbidwa ndi mbatata pakhosi. Za ziiii

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 6 หลายเดือนก่อน +2

    Mbuzi zawanthu a police akumalawi

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly 6 หลายเดือนก่อน

    Ku Malawi mmmmmmm mm tiyeni nazoni tionenso mu Holy Bible. THE MOST IMPORTANT COMMANDMENT

  • @LuciusMowa
    @LuciusMowa 6 หลายเดือนก่อน +3

    apolisi zigwilani ntchito yabwino osati kumamvera BOMA pa nkhani ya abon kalindo chifukwa chimene mungadziwe ndi chakuti bon kalindo sakulakwitsa ayi komanso sanaphe munthu ayi ndi ufulu wake kuyankhulira amalawi ndiye BOMA LA mcp musalimbane ndi kalindo ,mulimbana ndi anthu omwe akuba ndalama zaboma bwanji simukuwamanga ,

  • @JusticeKawilira
    @JusticeKawilira 6 หลายเดือนก่อน

    M"malo molimbana ndi mavuto a njala, ma passport, driving licence, katangale muli busy kulimbana ndi Kalindo MCP imeneyo

  • @jonathanmalanda7742
    @jonathanmalanda7742 6 หลายเดือนก่อน

    Tapitani mukayambitse church mulungu akulankhuleni mwapadera isanafike poipa misala

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 6 หลายเดือนก่อน

    Aboma ndizisuru makhoti anawo akwendera Chakwera mwina titi anagulidwa ndi Chakwera

  • @williammenard48
    @williammenard48 6 หลายเดือนก่อน

    Chitsiru chili ndi mwini
    Born Kalindo ali ndi anthu omwe amamuyamikila pa zomwe amachita kotelo ngati Chakwera ndi anthu ake angapange mistake yomuponya mundende Kalindo kwa ka nthawi, Malawi anunkha utsi komanso magazi.
    Ma galimoto ena tiziwawotchela mma parking mwawo pomwe nyumba zina ziziphya kuzela mu mphanvu yocholuka ya magesi a masenga omwe tizikonza tokha. Ndipo yemwe ayesele ku pitilira ndi plan ofuna kupha Born Kalindo, timukonzera ngozi ya mmadzi chingakhalenso ya panseu kudzera mu pemphero lathu la 00:00 monga ife achi slamu.

  • @GanMapira
    @GanMapira 6 หลายเดือนก่อน

    aaaah zopusa et

  • @MatolasiReginaKasote
    @MatolasiReginaKasote 6 หลายเดือนก่อน

    Palibe chomumangila born kalindo.nkhanza timangomva kut mcp inali nazo tisanabadwe.koma pano tikuziwona nafenso ndimaso athu.kodi ma audio akut chani?akungoti audio koma osanena audio yakeyo ndali zanji izi?

  • @BerthaMkwinika-e7s
    @BerthaMkwinika-e7s 6 หลายเดือนก่อน

    Ponena bon kalindo aziti ndimamenyera ufulu Amalawi ena, not kungonena kt Amalawi chifukwa enafe sitiona chanzeru mwa iye

    • @GiftFrancesco
      @GiftFrancesco 6 หลายเดือนก่อน +1

      Achisulu inu

  • @GiftFrancesco
    @GiftFrancesco 6 หลายเดือนก่อน

    Nkhan ya mfut yo ndyaboza coz yatenga thaw yaytalikomaso munga ngat alind mfut opanda chilolezo bwanj samawamanga

  • @JusticeMakwinja
    @JusticeMakwinja 5 หลายเดือนก่อน

    Khani yaboza ya mfuti yo iyaaa

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 6 หลายเดือนก่อน

    Iwe sumandiwelengela bwino nkhani msaname!, aaaaaa.

    • @Gwedeza-oz3jv
      @Gwedeza-oz3jv 6 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂komaaa

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 6 หลายเดือนก่อน

    Mcp nkhaza

  • @AliajoeAliajoe-vv1wo
    @AliajoeAliajoe-vv1wo 6 หลายเดือนก่อน

    Chekwala ndiwaphwala

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 6 หลายเดือนก่อน

    Chakwera mabatile ake ndithu

  • @GidionJonas-sr4zr
    @GidionJonas-sr4zr 6 หลายเดือนก่อน

    Ndale bc tidzigomenya apolice bc asamatipatse busy

  • @ElizabethNali-e8w
    @ElizabethNali-e8w 6 หลายเดือนก่อน

    tingo mupemphelela atuluke basi mcp siboma koma satanic bas