ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Having these messages on TH-cam is a very good development. Glory be to God in heaven
Amen pastor mulungu apitilize kukusungani tiwuzeni kuti tiziwechowonadi and wakumvawave.
Amen 🙏🙏🙏 umboni uwu wanibaya kwambiri Ambuye alemekezeke 😭
Amen powerful massage ineyo tere mutu wanga pachaka umakonda kuwawa kawiri koma zenaya out indeed
Zinthu zochitikadi koma odziwa kuti ndi ziwanda, tatseguka maso zikomo Kwa mbiri Mulungu apitirize kuku gwiritsani ntchito. Amen
Ndipo satana wayaluka zake zada zikomo pastor mumatithandiza Ambuye azikudalitsani
Amen 🙏
Mwainu ndaphudzirapo kanthu abusa🙏🙏🙏🙏 koma chonde ndimasuren ine pankhani ya kumaloto pena ndimathadi kulota ndili ndi mimba koma podzuka ndimapezeka kt ndili pa period😭😭😭 koma chonsecho mwana ndilibe
chat.whatsapp.com/JCJdMsSiiRn3Tk4IXjyf8n Iyi ndi link ya gulu la WhatsApp pomwe mutha kufunsa ndi kuyankhidwa mwachangu. Zikomo
Zikomo kwambiri ndaphuzilamo zochuluka mautumiki Anu God bless u
Always God is great
okay
Amen
😢
Ambuye adimenyele nkhondo
Abusa tipemphereni ndikudutsa munyengo zowawa kwambiri
Mulungu akuze malire Anu a Twaibu
Zikumandipsa coz anthu timaona nga zimene tikupanga ndizabwino kma palibe chi mene tichita nothing tingopepha molimbika kut tikule muuzimu
Mulungu akudalitseni Abusa athu a twaibu mwatsegula maso mulungu akudalitseni kwambiri Abusa anga
ATI adayambitsa mpingo,,,, is this true
No, this is not true.
Zikomo kwambiri ineo ndiye ndaphunzirapo kwambiri ineso ndinali mbuli ambuye akudaliseni
Sda
That's true people repent pliz
Having these messages on TH-cam is a very good development. Glory be to God in heaven
Amen pastor mulungu apitilize kukusungani tiwuzeni kuti tiziwechowonadi and wakumvawave.
Amen 🙏🙏🙏 umboni uwu wanibaya kwambiri Ambuye alemekezeke 😭
Amen powerful massage ineyo tere mutu wanga pachaka umakonda kuwawa kawiri koma zenaya out indeed
Zinthu zochitikadi koma odziwa kuti ndi ziwanda, tatseguka maso zikomo Kwa mbiri Mulungu apitirize kuku gwiritsani ntchito. Amen
Ndipo satana wayaluka zake zada zikomo pastor mumatithandiza Ambuye azikudalitsani
Amen 🙏
Mwainu ndaphudzirapo kanthu abusa🙏🙏🙏🙏 koma chonde ndimasuren ine pankhani ya kumaloto pena ndimathadi kulota ndili ndi mimba koma podzuka ndimapezeka kt ndili pa period😭😭😭 koma chonsecho mwana ndilibe
chat.whatsapp.com/JCJdMsSiiRn3Tk4IXjyf8n
Iyi ndi link ya gulu la WhatsApp pomwe mutha kufunsa ndi kuyankhidwa mwachangu. Zikomo