NDIDZAULURA KALATA YA GRACE ZAYAMBA KUCHITIKA TSOPANO KUNO KU MALAWI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 11 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 63

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 20 วันที่ผ่านมา +9

    Ndimunthu yenkhayo odzazidwa ndizimu wadziwandi yemwe agayime ndikunena kuti kalata iyi sikuphelezela pazose zomwe zikuchitika ndinthu ndiyenkhayo nayeso akusowekela mamasulidwe nkunthekaso nayeso Ali mugulu limeneli ndamene agabwele ndikutsutsa chifukwa izi zikuchitikazi diso nkhuti lilirose lakuuzimu wamulungu likuwona komaso likuva tiyeni amalawi koooooose muli tipephele kwa mulungu kumwamba achitile atimenyele nkhondoyi

    • @RaffickAllie
      @RaffickAllie 7 วันที่ผ่านมา

      Vuto amalawi ife ndiokanika.kungotipatsa Gayiwa 50 kg basi .bushir bushir .kumuchemerera

  • @UncleBusy-c6l
    @UncleBusy-c6l 20 วันที่ผ่านมา +6

    Mutumizeni bushiri ku south africa azikayankha milandu yake mwina tipumeko kuona imfa zaabale athu iiii ntundu wamalawi ukutha kaziko kake komweka kamanjaka koma zochitika pwilikiti mmmm tisalekelele izi amalawi titha ndithu

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j 19 วันที่ผ่านมา +3

    Ziko la malawi mulungu amalikonda koma ife ena ambilife sitilikonda chifukwa chadyera tikukakamirabe anthu omwe akulitha ziko lathu pamodzi ndiife tomwe tikuona ndikumati sazachoka pampando amalawi olimba tiyeni tipemphere chikhululuko kwa mulungu kuti alowelerepo chifukwa anthu ena adakalibe ndi khungu ndichifukwa akuti chakwera yemweyo

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr 20 วันที่ผ่านมา +5

    Lelo chipani chake ndichimenechi cha chakwela chamwanzi mix bushiri mulungu achite nanu mukumphetsa anthu osalakwa

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 17 วันที่ผ่านมา

    Grace chinga was a true servant of the Lord and a prophetess. Whatever she prophesied many years ago it has come to pass. May God destroy the wicked rulers I hate chakwera and bushiri big time

  • @RabsonMatope
    @RabsonMatope 20 วันที่ผ่านมา +4

    Chili chose chomwe chinanenedwa umu chikuchitika chabe anthufe kumvetsetsa zimatimvuta

  • @Elida-z2p
    @Elida-z2p 12 วันที่ผ่านมา

    Grace chinga mzimu wanu uziusa mumtendere lelo ndiizi chakwera ndinzake bushil akungopha anthu ngat nkhuku zimenezi ofunika mumtumizile azinvere ekha bushil 😢😢

  • @EllahEllah-hu7hi
    @EllahEllah-hu7hi 20 วันที่ผ่านมา +2

    Amene akuti sakukhulupilirayo ndi mwana wake wachikagawa

  • @DanJohn-ws5gl
    @DanJohn-ws5gl 20 วันที่ผ่านมา +2

    Ulosi ukukwanilisidwa magazi daily akukhesedwa kuchoka pakhomo nkubwelelanso wamoyo ndi chisomo

    • @louismagongwa
      @louismagongwa 20 วันที่ผ่านมา

      eee sukunama ase ukamachoka khawa biiii kut ndikafika kma ulendowu

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika 20 วันที่ผ่านมา +1

    May heavenly father remain my lawyer...eish chonena chagwera mkati.

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 20 วันที่ผ่านมา +1

    Vuto la anthufe ndi kusakhulupilira.
    Grace chinga sadaname

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 20 วันที่ผ่านมา +1

    Joyce Banda milomo ngati odya nyama za kuufiti

  • @user-cn3gi2vf5n
    @user-cn3gi2vf5n 20 วันที่ผ่านมา

    Let's pray for our nation Malawi God will answer our prayers

  • @YankhoGuza
    @YankhoGuza 20 วันที่ผ่านมา

    Amen ukukayikilawe abambo ako ndi chakwera mfiti yokutha ntchito mutu wako dziko mmene likuyendelamu ungamanene zimenezo umbuli eti ukumvera kukamwa kapena

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq 20 วันที่ผ่านมา +1

    Ndizoona ananena kale grace chinga

  • @onesterabayo1871
    @onesterabayo1871 19 วันที่ผ่านมา

    I pray that Malawi be safe against evil plans

  • @ShazidaAlfred
    @ShazidaAlfred 20 วันที่ผ่านมา +1

    Rero ndiizi zikuchitikati

  • @user-em1qi8kj9h
    @user-em1qi8kj9h 20 วันที่ผ่านมา

    Mau ako aphelezera grace...lero zikuchitikadi kuyambila pa june mpaka pano magazi okhaokha Amalawi muno

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 20 วันที่ผ่านมา

    Ndipo live thaw yake nd yomwei chakwera wakwanilisa😮

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 20 วันที่ผ่านมา

    Chipani chake ndichimenechi tilimochi abale ngozi kumalawi chonchi mmmm why god😢😢😢😢 ambuye tilanditsen ife ana anu tathodwa tasowa nzeru

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 20 วันที่ผ่านมา

    Wow khani wozwizwista MHSRIP,ambuye mulungu azititeteza ameeen

    • @Atheeeefire
      @Atheeeefire 18 วันที่ผ่านมา

      Everything happen so fast but we can connect grace was a gift from God...when dpp loose 2019

  • @TressLuka
    @TressLuka 20 วันที่ผ่านมา

    Zililokutu ndipo za malodza 😎🇲🇼

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp 20 วันที่ผ่านมา +1

    Malawi

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 17 วันที่ผ่านมา

    Kalata iyiyi eeeeish

  • @DanPhiri-gn1rp
    @DanPhiri-gn1rp 20 วันที่ผ่านมา +1

    Ndizoona

  • @WisdomBlack-uu7zt
    @WisdomBlack-uu7zt 20 วันที่ผ่านมา

    Nditangonva dzina la bushir ndi skeffa chimoto ndayamba kukukhulupililan

  • @HastingsPaul
    @HastingsPaul 19 วันที่ผ่านมา

    Sopano akulankhurai ninda😮

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 20 วันที่ผ่านมา +1

    Ndizowonadi zikuchitika ndithu

  • @samsonmtumbati4855
    @samsonmtumbati4855 20 วันที่ผ่านมา

    Izi ndizoona zokhazokha mulungu landitsani dziko la Malawi kudzanja la woyipayo

  • @Ghama-k4i
    @Ghama-k4i 20 วันที่ผ่านมา

    Malawi flash back

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 20 วันที่ผ่านมา

    Joyce Banda ndi Bushiri akukunamizirani ngati

  • @juniortsegula3847
    @juniortsegula3847 20 วันที่ผ่านมา

    Amen

  • @user-mi3ot6ms8x
    @user-mi3ot6ms8x 17 วันที่ผ่านมา

    Ulosi wakwanilitsidwa

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 20 วันที่ผ่านมา

    Koma mulungu atithandiza ndithu dziko lathu

  • @louismagongwa
    @louismagongwa 20 วันที่ผ่านมา

    malawi wafikapo iiiish

  • @user-mv8vy3ht3n
    @user-mv8vy3ht3n 20 วันที่ผ่านมา +1

    Zooonadi

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 20 วันที่ผ่านมา

    Mulungu salakwitsa kalikose apanga jira ina

  • @emmanuelalbertbotolo
    @emmanuelalbertbotolo 20 วันที่ผ่านมา

    Mzimu wako uuse muntendere ndipo uzitimenyera nkhondo anafe kuti nafe tizalowe mu umfumu wakumwamba

  • @user-xj9uy6wz7b
    @user-xj9uy6wz7b 20 วันที่ผ่านมา

    Esh skefa wandikhumudwitsa kan zoonad 😢😢😢

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 20 วันที่ผ่านมา

    Apadi ndiye zayamba kuoneka ndi maso

  • @SiboPaul
    @SiboPaul 20 วันที่ผ่านมา

    Zoona zake

  • @user-pc3jg6pd1h
    @user-pc3jg6pd1h 20 วันที่ผ่านมา

    Ndizaulula

  • @phillkaunda5623
    @phillkaunda5623 20 วันที่ผ่านมา

    Koma guys moyo ukuwawa

  • @ClementMinyanga
    @ClementMinyanga 20 วันที่ผ่านมา

    Pope vs malawi

  • @beatricenkhoma1109
    @beatricenkhoma1109 20 วันที่ผ่านมา

    Mulungu atipatse maso auzimu

  • @daviechinthengaofficialcha7190
    @daviechinthengaofficialcha7190 20 วันที่ผ่านมา

    Agiling'ande yalakwatu pamenepo basi kkkkkkk

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 20 วันที่ผ่านมา

    Zikukwanilisika sopano

  • @chisalengondo4530
    @chisalengondo4530 17 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😮

  • @ronaldordinga6537
    @ronaldordinga6537 20 วันที่ผ่านมา +2

    Ndukayikira ngati zili zoonaa

    • @LamieTiger
      @LamieTiger 20 วันที่ผ่านมา

      Ndizoona kalatayi tinaimvera grace chinga alimoyo bwana and ananena zambili anantchula Maina ambili Koma athu ena amatha anaidula kalatayi

    • @ronaldordinga6537
      @ronaldordinga6537 20 วันที่ผ่านมา

      @@LamieTiger ya full ilikutiko tiyimvere nafeso

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o 20 วันที่ผ่านมา

      Kalata iyi I atuluka ndikale Grace atangotisiya kumene ndithu izi ndi Zoonadi kwamene simunamve nthawi imeneyo zinangokudusani koma kunena moopa mulungu kalata inatuluka chaka chomwe chinatisiya Grace the same wk

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o 20 วันที่ผ่านมา

      Mmene ndinayumvera ine inalekezera pomwepo chifukwa owerengayo anauzidwa kuti asiye koma imapitilira ndithu komabe nthawi imeneyo inalekezera pomwepo

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq 20 วันที่ผ่านมา +1

      Ananena kale izi grace chinga

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 20 วันที่ผ่านมา

    Zoonad

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 20 วันที่ผ่านมา

    Ndizoona