2024 it's a year in my life ndinakumana ndizokhoma, but God did the best part 🎉🎉now 2024 at this time I can testify that alot has happened best n fruitful in my life, ndithudi ndizoona kuti satan amaona zapatsogolo kuposa Ife, ndithudi if he won the battle chaka ichi chikanakhara chaka choyipitsitsa mmoyo mwana. Malawi Dzuka tipemphere ndithudi Ambuye anakumaniza chosowa changa😊. May God bless you all, mwa Yesu muli mtendele komaso madalitso.

I love this song too much and it bring me closer to God
Nyimbo ya mu bus usiku from Mzuzu-Chingeni-BTz and vice versa. I love it.
2024 has been one of the best year for me
Lord help me to stand in prayer 😭 yehova I love so very much.
Amen king zooona zake kumeneku ndie kuimba ndipo ndimatsitsimuka ndimakumbukira kwathu misozi ili mmasaya kumva nyimbo za kwathu zothyakuka.
Ester Queene where are you my dear
Mulikuti asisi???
Amen!
Amen king tikusisimuka nazo nyimbo zanu
Dzuka yona tipemphere......God bless you brother king James phiri
Im blessed when I hear this song
Malawi rise its time to pray God bless you king james phiri💥💥
amen. ndimadalitsika, komanso chilimbikitso chauchicrisutu yanga
I love this song
Powerful song Amen
I love this song actually its my daily song
Gosto das canções malawianas tem messagens muito forte ♥️
Amen prayer is only weapon we have to defeat our enemies
One underrated but very powerful
My favorite song
I really like the song
Kumva kukoma nyimbo ngati tafika kale ku mwamba .
Munyimbo zako James timatsitsimuka komanso kupeza chiyembekezo pa chozizwa
Amen 😢😢😢
king nyimbo yabwino
On point
Amen
Powerful song
Mwina yona walero ndiwe kufunika kusamala
Wow 😳
powerful
Mwina Yona walero ndiine dzuka nzimu wanga
Dzukani ambuye ndi nyengo zanga
Naiyi yokha imandiwaza
A Malawi dzukani tipemphere.
Mumatisimusa ambuye akudaliseni
mmmm koma munayimba bwinotu moti apa ndatsitsimuka
My favourite song
I love this song