2024 Sliver strikers 1 - 0 Fomo fc ⚽🔥
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 16 ต.ค. 2024
- Sliver strikers yomwe ikutsogolera tnm super league ndimapoints 36 ikupitilira kuthambisa ma team pomwe zulo yagonjesa team ya fomo fc 1 kwa duu , kuwina kwazulo kwapangisa kuti ifike mapoints 36.
Onelani masewelowa mene analili.