ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
AaaaahMy babe girlShe’s so lovingShe’s so patientShe’s my heavenly sentCHORUSMbuye dalitsani okondedwa wangaMumpatse moyo wautali ndi wathanziPoti ndiye apangitsaMoyo wanga kukomaNdichotsereni mtima wachimasomasoAsamazunzike ndi kundidandaulaPoti ndiye apangitsaMoyo wanga kuwalaNdiye apangitsaMoyo wanga kukomaNdiye apangitsaMoyo wanga kuwalaVERSE 1Kalekale okongola ndinkangowaonera pataliKumangodzidelera kuti ine sangandiloreMalingana ndi nyengo zimene ndinali kudutsamoSindinkadziwa Chauta adandisungira wanga mmodziLero lino siuyu ali nane pambalipaAmakhala nane m’nyengo zanga zonseAmalira pomwe ine ndikuliraAmasangalara pomwe ine ndiri pachimwemweOnena nenani koma izi zokha sim’sokonezaPopeza ndi banja lochoka kwa ChautaMukatiyang’anitsitsa timayenerana timakhalanaSizochoka kwa munthu adapereka yekha ChautaNamalenga, Namalenga, ndikadakonda inu mukadakhala m’busa wathuMudzzitiyang’anira tikhale banja lachitsanzoAkamaona ife anthu azisiliraCHORUSVERSE 2Ndi zomvetsa chisoni mabanja ena leroAngokhalira limodzi koma banja linathaBambo amapanga zawo, amayinso zawoKumatukwanizana pamaso pa anaNthawi zina kumenyana zopanda ulemuPalibe amafuna kulolera mzakeKoma zikakumana njobvu umavutika ndi udzuPamapeto pa zonse ozunzika ndi anawaEna amayambana akapeza chumaNthawi yomwe adali amphawi ankakondanaChina chirichonse ankachita limodziNgakhale kutchalitchi ankapita limodziLero Mulungu wadalitsa walakwanso wapalamulaLero chikondi chabambo, amayi sachionaAnanso chikondi chamakolo ndithudi sachionaAyambanso kupemphera kuti bola asaukensoAzikhalanso mwachikondi bwinobwino ngati kaleAaaahMy babe girlShe’s so lovingShe’s so patientShe’s my heavenly sentCHORUS
I'm impressed Bro. your songs usually touches things that are happening in life especially Chinamuluma, I like your songs big time. So happy I can access them online. please kip it up.
Odzuzika ndi achinadi Junior Skeffa ndizoona, wadalitsa Mlungu walakwadi, amen bro
This guy is really talented..its very easy to tell,its true koma mabanja ena yali questionable. Shame on you.big up Skeefa !
Wow i can't even to stop watching this video Congrats Mr Chimoto
Zambia loves you
The message in this song is great,Ilike it to hell.Keep it up bro ,Never put the sky as your limit.God bless
Beautiful piece of Music. It make me miss my stay in Malawi. In Nairobi Kenya.
martin simiyu Tanzania. Muvi
I like u phwanga u mak every one proud bcoz of your songs sound something in our heart
Big up Skeffa ur very talented one
Wow I love it
Be blessed Skeffa.
i like it and he knows how to sing!
I like it coz it affects everyone who pass those stage they knw how tough it is
Nice one skeffa
A chimwe. Yandigwira. Mtima kumtukwanizana pamaso pa ana
I like this aong
Thandi nice
i ilke this song
I like it ,kip it up skeffa
big man
My favourite musician in Malawi you Rock, I love the way you sing.
Kkkkkkkkk
Big up Skeffa ur very very talented one
Aaaaah
My babe girl
She’s so loving
She’s so patient
She’s my heavenly sent
CHORUS
Mbuye dalitsani okondedwa wanga
Mumpatse moyo wautali ndi wathanzi
Poti ndiye apangitsa
Moyo wanga kukoma
Ndichotsereni mtima wachimasomaso
Asamazunzike ndi kundidandaula
Poti ndiye apangitsa
Moyo wanga kuwala
Ndiye apangitsa
Moyo wanga kukoma
Ndiye apangitsa
Moyo wanga kuwala
VERSE 1
Kalekale okongola ndinkangowaonera patali
Kumangodzidelera kuti ine sangandilore
Malingana ndi nyengo zimene ndinali kudutsamo
Sindinkadziwa Chauta adandisungira wanga mmodzi
Lero lino siuyu ali nane pambalipa
Amakhala nane m’nyengo zanga zonse
Amalira pomwe ine ndikulira
Amasangalara pomwe ine ndiri pachimwemwe
Onena nenani koma izi zokha sim’sokoneza
Popeza ndi banja lochoka kwa Chauta
Mukatiyang’anitsitsa timayenerana timakhalana
Sizochoka kwa munthu adapereka yekha Chauta
Namalenga, Namalenga, ndikadakonda inu mukadakhala m’busa wathu
Mudzzitiyang’anira tikhale banja lachitsanzo
Akamaona ife anthu azisilira
CHORUS
VERSE 2
Ndi zomvetsa chisoni mabanja ena lero
Angokhalira limodzi koma banja linatha
Bambo amapanga zawo, amayinso zawo
Kumatukwanizana pamaso pa ana
Nthawi zina kumenyana zopanda ulemu
Palibe amafuna kulolera mzake
Koma zikakumana njobvu umavutika ndi udzu
Pamapeto pa zonse ozunzika ndi anawa
Ena amayambana akapeza chuma
Nthawi yomwe adali amphawi ankakondana
China chirichonse ankachita limodzi
Ngakhale kutchalitchi ankapita limodzi
Lero Mulungu wadalitsa walakwanso wapalamula
Lero chikondi chabambo, amayi sachiona
Ananso chikondi chamakolo ndithudi sachiona
Ayambanso kupemphera kuti bola asaukenso
Azikhalanso mwachikondi bwinobwino ngati kale
Aaaah