Mkhani zomwe zachitika lero pa 22 December 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 16

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Eyaa! Kalembela ayambilenso, smart mati idzipita za ucisilu mmalawi muno sitikufuna anabelo,nsambo ndi cikangawa adziwe kuti ife si ana amawo.

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Mmmmmmm kulibwino kungoyambilanso kalambelayo chifukawa uyu walowa chiphwilikiti asatipusise awa agaluwa

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Ndawachinyama opusa ekha amene angazavoteleso chakwera

  • @KelvinMungomo
    @KelvinMungomo ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂 chisiru iwe usanenechocho achoka ameneyo

  • @VenançioZocueza
    @VenançioZocueza 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kuvotera chakwera mchimodzimodzi kuvotera,njala dzikwanje, komanso tsankho.

  • @KhirChisale
    @KhirChisale 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthuwatu anangozolowela zoononga nanga mpaka ndalama zaboma koma zizingotha ndi zimenezi zoona

  • @IshmaelSaidi-v6z
    @IshmaelSaidi-v6z 2 นาทีที่ผ่านมา

    Malawi wa3ka ponyasa ndi uchimo

  • @Abdul-xk8dq
    @Abdul-xk8dq ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma inu mukunyadila chiyani mumakanika kugula sopo zithu zadula kwambili ndiye mkumati chakwela Machini amalawi mwatani kumachemelela zopusa

  • @Alfred-lb4jw
    @Alfred-lb4jw 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera ñdi galu zed achoke galu ameneo watikwana zed .

  • @FosterKasola
    @FosterKasola 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mufela za eni ngat mukufuna ndalama achinyamata a ku mzuzu

  • @VenançioZocueza
    @VenançioZocueza 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achakwera tsitsani katundu osiyana Siyana kuti mukhale Dolo.osati ukape wanu wonunkha ngati chiphwisi.

    • @Extratremendouszeus
      @Extratremendouszeus 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Sangakumveni man..liiran kuusi bas

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Musanamepo. apa mumabwaza anthu ofikafika pamalopo

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nosense news. About cjikangawa

  • @Alfred-lb4jw
    @Alfred-lb4jw 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera ñdi galu zed achoke galu ameneo watikwana zed .

  • @Alfred-lb4jw
    @Alfred-lb4jw 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera ñdi galu zed achoke galu ameneo watikwana zed .