Well said and I have watched it to the end plus I can even watch it again and again We need people like you to lead us Well done boss Even Brian was listening not just asking
Ineyo ndiri ndi mafunso angapo: 1. Kodi amane amasankha speaker wa nyumba ya malamulo ndi ndani? 2. Kodi ndizoyenerera kuti speaker akhaleso wandale komanso vice president wa Chipani. 3. Kodi Parliament ma standing order ake amakhulana kuti leader of the house ndi General Secretary wa MCP Ndukunena kuti 1. Vice president wa MCP ndi speaker ku parliament 2. Vice speaker wa parliament ndi MCP 3. Leader of the house ndi General Secretary ndi wa MCP Kuona kwanga ndiye kuli biasness kukomera MCP
Go to China, Every filling station is owned by government. We can do better by having facilities to learn how to refine crude oil in our universities. Who said Malawi cannot have mini refinery machine for crude oil for our small country, Malawi? We have Salima Sugar company run totally by Malawians. Same mentality and courage can be applied.
@mathewsnachuma8086 Kuti mukagure nao kumene amagurako? Africa has crude oil reserves in Nigeria, Sudan, Angola ect. Ngati sibodzaso koma nyanja yathu iliso ndi izi.
Kulembetsa ndi kuzavota is the only solution kwa amene akufuna MCP ipilire komanso kwa amene sakufuna chifukwa kumangoiyamikila boma la MCP koma osavota ndi zopoira chimodzimodzi kumangodandaula kuti boma siikuyenda bwino koma osavota nzopanda ntchito chifukwa mphamvu ili mu vote
Actually this guy always stand for Malawian, may God's continue to protect and bless the Man to lives a long life
Well said and I have watched it to the end plus I can even watch it again and again
We need people like you to lead us
Well done boss
Even Brian was listening not just asking
Suleman my pangolin 🔥🔥🔥💙💙
Ndimawanyadira kwambiri akulu amenewa because amatigwilira ntchito bwino ife amalawi ❤❤❤❤❤
Uyutu basi must be the president of malawi 🇲🇼
Allah adzikuonjezerani nzeru honorable
This man deserve to be President of Malawi he always fight for Malawians
Nduna za Chaka Cha Mawa ❤
We need people like this
Wait until they get into power🙌.I no longer trust politicians
Tikufuna atsogoleri odzindikira ngati su leman osati ungolimbikira kunena tiwina ngati vote akaponya wokha keep It up and continue kutiiimilira
Suleman our Pangolin in parliament ❤❤
Thanks Malangizo awulele awa
Improve on the audio quality otherwise we do love this program
Suleiman iweo ndikatu ,,,,brave chikangawa basi
Indeed mcp is a gangster party
nice said our MP
I watched it to the end🎉
Well said
Big osazasiya kunena chilungamo mu parliament 🎉
Ineyo ndiri ndi mafunso angapo:
1. Kodi amane amasankha speaker wa nyumba ya malamulo ndi ndani?
2. Kodi ndizoyenerera kuti speaker akhaleso wandale komanso vice president wa Chipani.
3. Kodi Parliament ma standing order ake amakhulana kuti leader of the house ndi General Secretary wa MCP
Ndukunena kuti
1. Vice president wa MCP ndi speaker ku parliament
2. Vice speaker wa parliament ndi MCP
3. Leader of the house ndi General Secretary ndi wa MCP
Kuona kwanga ndiye kuli biasness kukomera MCP
Zooonadi coz side inayo amakhala ndi phamvu ayi eesh
Parliamentarians amasankhidwa kudzera kuzipani so palibepo chachilendo..and speaker amasankhidwa mu parliament momwemu osankhanaso kukhala eniakewo
And palibe lamulo lomwe limaletsa izi
Have ever been in parliament?@@RichardPhiri-w8b
Powerful 🎉
May u live long honourable Suleiman,Allahumma amein
Soleman mumaima pachilungamo ndipo osafowoka osatopa mmene munanenela sindikusiyani a MCP ndilinanu nanu
Sameer Suleman anabwera kudzatumikira a Malawi mosanyengerera anthu achinyengo. Allah azikutsogolerani
Point 100 % I gree with you Mr
Sameer mulungu akhale nanu nthawi zonse
Suleman on fire
If we had ten such kind of brilliant ministers bwezi malawi atasintha osati achina kamajekete ndi chigawenga kunkuyu
Sulemani the Great. Ndinu mm'bale weniweni wa.anthu aku mudzi Keep it up Big man
it makes sense
Akatundu, leader of opposition incoming
Good guy who know how speck in Parliament not bon kalindo
I love ❤️ this guy ❤❤
I likes the guy so much even ma company Ake zadongosolo zija
Please fix your audio
Audio quality is trash too bad for a multinational broadcasting station
Mp wathu, wachitukuko,, amatithandiza ,,sakunama ,from nangumi vg
But the fact iz that those companies producing oil, are government owned. So diplomatically the President iz ryt. Remove politix on this matter.
Makina🎉
This is a useless Government....sizinawokeee
DPP my vote,
Praying for Smeer
Suleman machine
We put this on ourselves
MP ONSE ANAKATI AZIPANGA CHONCHIIIII!!!!!!
As a country we need to be shame this country has no president
Awawa ndi anthu omwe akufunika ku dziko lamalawi na ndi mmene zikuendela panopa
I can read truth here
Program iyiyi idzibwelezedwa npka chaka cha mawa indipatse malingaliro a boh
Our malema 💪💪
Njuju....
Basi ndikavota zikavute konko
Yes Malawi will remain the same don't kill our country
0:49
❤
Mmm ka pay nkamenekodi?
Wa m'boma saraly kufanana ndiwa garden ku south African
Ndalama ndi yo chepa kwambiri, near R5000 eish
Uyu amandiwaza zed
Mp wathu uyu
Mcp yafika pobowa mulungu atithandize ulamulilo uwuwu unyamuke ndipo usadzabweleso
Kooma ndiyeeeee!!!!
Koma abale dziko lathu likumvetsa chisoni... We lack serious people like Suleiman..
Sameer ndi ma tchini guys umakwana
Uyuyu ndi Boma akutiimilila
Go to China, Every filling station is owned by government. We can do better by having facilities to learn how to refine crude oil in our universities. Who said Malawi cannot have mini refinery machine for crude oil for our small country, Malawi? We have Salima Sugar company run totally by Malawians. Same mentality and courage can be applied.
Amagula kuti mafuta aku China wo
@mathewsnachuma8086 Kuti mukagure nao kumene amagurako? Africa has crude oil reserves in Nigeria, Sudan, Angola ect. Ngati sibodzaso koma nyanja yathu iliso ndi izi.
Kkkkk achakwera koama yaaaa
iwe! Salima sugar anagulitsa kwa amwenye muli kut kod brazi
@@plugentertainmentmw Times Exclusive’s Brian Banda engages Salima Sugar's CEO Wester Kossam as he explains his journey
Ntondo
Malawi anawonongeka
as I'm taking, galimoto yogawa akut ufa ma 5kg ikungoima ima kuno kumtandile akuti kugawa ufa koma kungopatsako anthu osakwana 10 yanyamukapo, funso mkumati kodi mcp inuvutisilanji aMalawi anthu akugona kale ndinjala , kumathawitsa ufa anthu akuuona ukupita mkumaithanangila galimoto , mukuxunxilanji anthu, Malawi alipanzuwa laleyu
That's why anthuwa katangale Samantha kumupewa because anthuwa amalandita ndalama zochepa zedi
Kuyakhura kwa nzeru
Asulemani inuyo mulungu akudaliseni ndithu kd muzichose ziwanthu za mcp iiii ayiiii
Malawi ali pamavuto akulu ndi mene Bwanawa akulakhulira apa😢
Brian wafika pongovera amwne nayeso ndi mmalawi akuyenera kuvetsera
Mumakwana bwana suleman
Leader 0f opposition kkkk
Or Brian chofusa mafuso chagwera mkati angoti kukamwa yasa😢
Brian kungoyamba ndi nkhani Yama bokosi😂
Mfundo izi mzofunika kumazimvera mobwerenza
Pakamwa wangolankhula basi
Pena ngati kusamuka kuno mkwabwino
ANtondo
Kulembetsa ndi kuzavota is the only solution kwa amene akufuna MCP ipilire komanso kwa amene sakufuna chifukwa kumangoiyamikila boma la MCP koma osavota ndi zopoira chimodzimodzi kumangodandaula kuti boma siikuyenda bwino koma osavota nzopanda ntchito chifukwa mphamvu ili mu vote
Joncb 1:13
Nkulu uyu ndi dolo
Kasongo
Am well andersteanding why he give u silly scandal to out in the parliament
Brian mafuso ako ase uzamenyanisa anthu kkkk
Iron man
Who told you kuti ndalama za toll gate zimapita ku Road traffic??😂😅
Mwakhalira makutu bwana?
Pakufunika nduna zonse ziphunzitsidwe ndi Suleman
Ndipo sakunama pa nkhomo pamunthu wandale ndipo anthu amazaza kufuna chithandizo
Uyu ndamene ankayenela kuyimira DPP
Tingopedza adzibambo awawa 5 ku parliament kukhodza kukhala bho
Eeee😂😂😂 uyu anali ku kenyayi😂😂 umakwana kma
Achina bwana mikaya koma amayankhulako ku patliamentiko😂😂
Kuli ziiiii
Brian akunama😂😂😂
Mulungu azikudalitsa ndichilungamo chanu adule mana
Za kuchipatalazo sizoona.Medical council momwe ikuvutilamu how can a person get involved in bribe
Kukhala wa MCP ndiuchigawenga ndamuona wina akuti kodi uyu amadalira chani azathera mmanja mwawathu meaning akulakaka atangomupha
Ndipo life duna yamawa imeneyo ndimakunyadira
Ichi mchanzeru kwambiri,how could one send you airticket for u to go and buy oil in his country? 😅😅😅
Boma la mafiya kkkk