BEN LONGWE AKUYING'ALURABE NKHANI YOMANGA ANTHU BOMA ILI LIKUNYANYA KOMA PALIBE KUOPA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 25 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 13

  • @ChrissyBenito
    @ChrissyBenito 2 วันที่ผ่านมา

    Ulamulilo uwu, ndiwakhanza tikuti, athu akuzuzika, tikagule sopa mavuto athu akuvuka dziko lokhala lathu

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 2 วันที่ผ่านมา

    Longwe gwila ntchito umakwana amalawi akunvetsa kuti umafuna kulowa mudziko lako mwantendele koma chilungamo umachidziwa thanks brother longwe masukani

  • @TimeMbona
    @TimeMbona 2 วันที่ผ่านมา

    Following

  • @GladysBonongwe-p6b
    @GladysBonongwe-p6b 2 วันที่ผ่านมา

    Mau amphavu

  • @DadTshepo
    @DadTshepo 2 วันที่ผ่านมา

    Anibe Ngwelo Chawapana Chitseko Pano akudziwa MCP yapita now akuituluka mmaso muli gwaaa😢😮😢😮😊

  • @spargomw
    @spargomw 2 วันที่ผ่านมา

    Apa Ben Longwe wabwera ngat coming😂😂😂😂😂. Waona kut kuja madzi achita katondo.

  • @Harrychokanda
    @Harrychokanda วันที่ผ่านมา

    Ndalama za chikangawa zinatha eti mwayambanso kulankhula 😂😂😂

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 2 วันที่ผ่านมา

    Mkuku amayakhu zovekatu ❤. Kutenga kusanje kukakusiya kulilongwe mcp

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 2 วันที่ผ่านมา

    Osanama.this.ben longwe ndi gass man mcp mulipo ndi ameneo telelanya abambo

  • @TennysonMulimbula-q5j
    @TennysonMulimbula-q5j 2 วันที่ผ่านมา

    Malawi Crocodile Party must be shown the exit gate

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 วันที่ผ่านมา

    Iwe Mesa anakugulq a mcp iwe

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 2 วันที่ผ่านมา

    Longwe buledi kuchoka pa 1600 mpakana 2500 limenelo dziko wina uja ndiye wafika pa 3500 buledi malawi ameneyo hhhh

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 2 วันที่ผ่านมา

      This is shupit amumba apite kukaunjika people akulira plzzz mukuwatani amabelo ine ndi world nate