Just a construction of bridge kukhala Topic Koma malawi ??come and see here in SA mighty projects konse konse koma you cant even see it On TV.......My malawi zikutipeza mochedwa
Koma why compare South Africa with Malawi. SA has the most gold deposits in the whole world, does Malawi have any!? SA has diamonds does MALAWI have any!? Bottom line, olo muli kumeneko, simungakhale Aku jonni?
Always great to see progress!🖤
Nice developments, tiyeni tisiye kunyoza.
takes us back home. thank you for this
Changing ❤
Video Camera with drone would have been great. Nice job
Thanks you my brother make more videos ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
You are welcome
Wamaso akuona 💪
Big up Mr brovo
Boma ndilomweli sitikusintha ayi ndizomwe tikufuna ife
Inu , yamikani zomwe wachita mzanu, za ku SA tisafanizire ndi kuno, zaka zonsezi ndani ku Malawi adapangapo izi?
Kodi inu kupit ku joni mesa mmathawa zovuta zakumalawi!! Tssaano pano wena wali uli konza dzikoli, ayipanso tere!?? Khwesi icho mulufuna!!
Here in Malawi, What We know is jealousy
😊😊😊😊 i love this dpp Lilongwe analibe nayo ntchito...shame on you
Just a construction of bridge kukhala Topic
Koma malawi ??come and see here in SA mighty projects konse konse koma you cant even see it On TV.......My malawi zikutipeza mochedwa
pepani ndithu. please dont skip the ADs,,
We don't see them on TV. We see them on TH-cam.
Koma why compare South Africa with Malawi. SA has the most gold deposits in the whole world, does Malawi have any!? SA has diamonds does MALAWI have any!? Bottom line, olo muli kumeneko, simungakhale Aku jonni?
@@DaroBilliand isn't even every where, sanayende uyo kkkkkkkkkk, ine ndayenda I know bwino, asatinamizepo apa, Malawi is progressing on it's level
my vote MCP 🗳 ❤❤❤❤
Progress
The government we wanted
Chonyasa ngat icho congratution
Cha pitala chanu chija chopotoka manja
China Aid❤❤❤
Japan
But he must go we don't need him😢😢😢😢😢😢
You must speak for yourself not we 😂
Tisanamizane. This is the ONLY ACTIVE GOVERNMENT I KNOW IN CONSTRUCTION
Musayike mu politics just comment to the person who's is posting the videos
Ndipo ndizoona 🎉
But kwathu kuno chitukuko chimabwera kudzera ku boma lomwe lilipolo,,ndipo bomalo limakhalapo kamba ka politics@@Eric-gb9ms
Boma la dpp amangoyankhula koma Mcp zikutheka,keep coming up with more development videos❤
Bodza