KODI NDICHIFUKWA CHANI AYAO AMBIRI NDIOSAPHUNZIRA?? chifukwa NDI izi🤙👇👇👇

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 28

  • @AhamaduJRAminie
    @AhamaduJRAminie 10 วันที่ผ่านมา

    Im proud to be Muslims and muyao❤😊

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 20 วันที่ผ่านมา +2

    Ayao kuchinda 😂

  • @mariawachesterweluzan
    @mariawachesterweluzan 17 วันที่ผ่านมา +2

    usamati sanaphuzire anaphuzira uhure kuranda amuna ayini,

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 6 วันที่ผ่านมา

    Koma pa dzinapo ndizoona mfana.

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 7 วันที่ผ่านมา

    ZAUSIRU IZI KUSAPHUNZIRA KWANUKO NDI KUFUNA OSANAMIZA WANTHU PALIBE MFUNDO APA USANYOZESE AYAO ANAPHUNZIRA

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 5 วันที่ผ่านมา

    Kusowa zokamba

    • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
      @CHIFUNDOCHINA-lp9lg  5 วันที่ผ่านมา

      @@RoseMkandawire-e2g naga ikunyalaya mgambe kupita

  • @IssahBwanali-i8w
    @IssahBwanali-i8w 17 วันที่ผ่านมา

    Munthu osazidikila ngati iwe ontchi mamuna amavaka nkono wa mazele iwe ukuvala wanja ngat ndiwe nkazi anthu osazindikila mavalidwe kom kukumba mbewa muyao munthu ozindikila ngakhalenso mavalidwe komanso kuchenjela kuyan'gana pansogolo

  • @WittinessNkhokwe-q7h
    @WittinessNkhokwe-q7h 20 วันที่ผ่านมา

    Ang'alule achiyao

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 22 วันที่ผ่านมา

    Komanso ku ciyawo mumalimbikisa ana kupita ku madalasi mmalo mupita ku sukulu nde inu bale mukunena zoona. Koma sopano iwe ukucokela kuti?

  • @brothergeomangulenje9456
    @brothergeomangulenje9456 18 วันที่ผ่านมา

    Nkhani yachikalekale imeneyo, ayao pano ndiophunzira

  • @IssahBwanali-i8w
    @IssahBwanali-i8w 17 วันที่ผ่านมา

    Mbuzi yamunthu kwambili iwe iweyo utamali maphuzilo ako onasakha kungwila ntchito yopusa ngt iyi pomwe ulipo olo nyumba ulibe pongona pokulozela uzafa uli ovutika iwe tabwela kuno uphuzile chikhalidwe osamangolongolola kumalawiko mukankhuta chisonso

  • @Kilop.y
    @Kilop.y 18 วันที่ผ่านมา

    Kalekale sukulu kuti Upite kalasi ina Pamatha chaka iwo anangofuna kusaphuzilako

  • @Amina-gg5gr
    @Amina-gg5gr 26 วันที่ผ่านมา +1

    Ngakhale asaphunzire umawadyetsa ndiwe

    • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
      @CHIFUNDOCHINA-lp9lg  26 วันที่ผ่านมา

      @@Amina-gg5gr ayaya apa ngawa kunyosyana,none jwachiyao

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc 24 วันที่ผ่านมา

    Umakwana________ aise Kodi iwe kwanu kuti? Ndamva watchula masukulu amene ndinaphuzira monga NAMWINI primary ndi Mpiri standard 8 kenako ndinapita ku MBENJERE secondary school, Ntaja, MACHINGA, paka ku CHANCO .
    Iwe ukuoneka wakwathu ndiuzeni.

    • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
      @CHIFUNDOCHINA-lp9lg  24 วันที่ผ่านมา

      Inenso konseko ndaphunzira

    • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
      @CHIFUNDOCHINA-lp9lg  24 วันที่ผ่านมา

      @@ThokoMsonkho-hy4uc mpiri,namwini,mbenjere NDIKOMWE ndinaphunzira,,,

    • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
      @CHIFUNDOCHINA-lp9lg  24 วันที่ผ่านมา

      @@ThokoMsonkho-hy4uc mpiri,namwini,mbenjere NDIKOMWE ndinaphunzira,,,

  • @PriscaMussah
    @PriscaMussah 13 วันที่ผ่านมา

    Khalani pansi basi

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 21 วันที่ผ่านมา

    Osaphunzira ndani. Ine muyawo wa ma degree atatu. Zachamba basi.

    • @thandimagombo1751
      @thandimagombo1751 20 วันที่ผ่านมา

      Ambiri ndiosaphunzira, mpaka pano ambiri saonetsa chidwi chophunzira

  • @MabushPaulo
    @MabushPaulo 26 วันที่ผ่านมา +1

    Ubwino wake mukudziwa Kuti ,Christu ndi chomwe chili choyambilira

  • @TinoCharamba-hr9el
    @TinoCharamba-hr9el 24 วันที่ผ่านมา

    Kod iwe zomwe ukunenazi unazitenga kut

  • @HassanTwaibu-c6h
    @HassanTwaibu-c6h 27 วันที่ผ่านมา

    aaaaaaa inu koma ndinu onamakwambili

    • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
      @CHIFUNDOCHINA-lp9lg  27 วันที่ผ่านมา

      @@HassanTwaibu-c6h bro apa sindikunyoza KOMA chilungamo,,antamusi unesoni jwachiyao

    • @HassanTwaibu-c6h
      @HassanTwaibu-c6h 26 วันที่ผ่านมา

      @CHIFUNDOCHINA-lp9lg aaa ngati ine ndati mukunyutsangati ndati mukunama eeetu