@@demiestudios378 inu ifetu ku shooter video musayese ngati sitimadziwa, ngini zi timazitsata mwinaso kuposa inuyo chabe kusadziwana, and vuto ma cinematographer aku Malawi kuno muli ndi vuto simufuna kulandira chidzudzulo that's why improvement imakuvutani kwambiri. Anzanu chidzudzulo amachilandira bwino as a way yokonzela zinthu zawo. Makani sakuthandizani.
Men these boys has shines
May Almighty protect you guys from the rust of pride mu kuimba bwino
Preaching the gospel through music. Blessings😊
Ana inu mmayimba nyimbo zosamba🥺🥺🥺🥰🥰🥰🔥🔥🔥🔥
Keep the fire burning boys👍🏼🔥💯
Pa ulendowu.. eish that part
Wow this is amazing guys
Powerful message
Madikira mfana wa bass yo😊❤
Congrats guys 🙏
Nice song 👍🏽
Eish guys🎉 nice❤💯💯
Mwapha🔥
😁hit ya Yahweh 🎉🎉
Very beautiful 👌💜
This is nice🎉❤
Za power a chisa oyipidwa😂👍🏼👍🏼🔥🥳💯
Amen!
Nice video brothers 🔥🔥
Amazing
😍😍
The basss😅🙄🔥🔥🔥🔥
Zamphanvu 🔥🔥🔥
Happy Sabbath
Nice one
Power!!!
Nice song
Blessed
Dzinalo koma lisithe you are no longer kids , mukukula and zomwe mukuimbazi eeeee sizaana
a mtamba aaaaaauuuuuzzzzzeeeee👌👌👌👌👌👌👌👌👌👌👌🤗🤗🤗👌👌👌👌👌👌👌👌👌👌👌👌
Amen
Mwa pha
Yonse mesa
Lit 🔥
Amen a mtamba
Anyamata pitirizani
GOAT
Za power 🎉🫡🫡
😊❤
Madoloo
Zamphamvu
Demie amajambula bho, koma ma lights ndiye akufunika apeze abho video sikuwala iyi.
Tikanakhala tikufuna kuti iwale tikanajambula masana nanu
Auze apopo ili mwala ka yuchita khala ngat ya Zambia mwaijambula bho🔥🔥
@@demiestudios378 inu ifetu ku shooter video musayese ngati sitimadziwa, ngini zi timazitsata mwinaso kuposa inuyo chabe kusadziwana, and vuto ma cinematographer aku Malawi kuno muli ndi vuto simufuna kulandira chidzudzulo that's why improvement imakuvutani kwambiri. Anzanu chidzudzulo amachilandira bwino as a way yokonzela zinthu zawo. Makani sakuthandizani.
@@demiestudios378 sizingatheke aliyense kumangoyamikila. Ndi bwino kukuuzani live kusiyana ndi kumakanenela kumbali, anthu akamakupopa ngini isali nyatwa ndekuti sakukukondani.