Chabwino funding a mcp anamupatsa Martha chuzuma nde chizuma anatani anapanga chani mutayamba kumumanga inu achawezi a mcp , munthu mwamupatsa udindo othana ndikatangale chomumangilaso ndichani nde uziti funding funding fotseki😩😤 komanso usamazimve ukatswiri ndiwe muthu omvetsa chisoni bcz you know the facts but you wish to run away from justice
Kodi munthu aliyese Ali mbali ya chipani ndikuyipa, nenani kuyipa kwa munthu not the whole chipani, I don't hate DPP but I hate Peter muthalika I don't hate UTM but I hate kaliati njawala ndi kambala because of jealous and greedy
Nice podca
Deus umatha
Tikufuna kamangila being wakulu ku cb
Katangale sangathe pokhapokha Yesu abwele
Chawezi ulibe mfundo ndiwee kape mchifukwa anakuthamangisa ku times mmutu mwako mwazaza mamina forsake
Achawezi yankhani fuso,osati funding or special court
Ndipo angothawa thawa
Chawezi mbolo yako umatinyasa umakakamira nkhani ... Umaonetsera mbali kuti ndiwe wa mcp kape iwe
Chabwino funding a mcp anamupatsa Martha chuzuma nde chizuma anatani anapanga chani mutayamba kumumanga inu achawezi a mcp , munthu mwamupatsa udindo othana ndikatangale chomumangilaso ndichani nde uziti funding funding fotseki😩😤 komanso usamazimve ukatswiri ndiwe muthu omvetsa chisoni bcz you know the facts but you wish to run away from justice
Kodi munthu aliyese Ali mbali ya chipani ndikuyipa, nenani kuyipa kwa munthu not the whole chipani, I don't hate DPP but I hate Peter muthalika
I don't hate UTM but I hate kaliati njawala ndi kambala because of jealous and greedy
That guy is biased
Adha chawezi simukuyankha mafunso omwe mukufunsidwa ndipo mukundipsesa mtima kwambili fuso labwino bwino koma kudutsa uko , process yopanga replacement mai Martha chuzuma ikuchedwa why , nde uzikayankha kuti akusaka munthu olimba mtima wamva kut athu sangalembele mesa ena kusalembelako ndikamba kolembana tchito mwachinyengo ngati mmene mwapangila ku mec