Anthu anga akuonongeka chifukwa cha kusadziwa. Abale anga mwa Ambuye kukamva mawu muzikhala ngati ophunzira aku beleya omwe amati akalalikidwa ndi paulo amapita kukawerenganso malemba kuti zomwe amaphunzitsa zija ndi zoona? Read your bible then come back to me, bible mulibe mawu oti chauta pa ma verse omwe amawerengawo komanso si buku la malamulo koma chilamulo ndi zosiyana nde osamangothamangira kunena amen mukunamizidwa you have to be very careful bible is a word of God not a magazine.
Amen Fr Nthalika
Amen uku ndiye kuima pa choonad ambuye akhale nanu thaw zose
inuyo mulungudi anakusankhani kuti mutumukure osati ansembe enawa akulandila ndalama ndalama kunyumba yachifumu kubisa chilungamo mulungu akuze malire Anu father
Amen and Amen
Ichi chimandiwaza heavy
Fr Amen Amen
Amen🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Amen
Amen fr,wakumva amve ndithu
Ameen munthu wamulungu poima pa chilungamo
Munthu wamulungu ambuye azikudalitsani
Amen brother
Amen Amen Amen
Ameen
Kutumikira Ambuye muchoonadi nkokoma.Ambuye azikutetezani nthawi zonnse
Powerful
Kumeneko ndye.ku.bwera
Nanenso ndilinawo umboni mumati sisimusa bambo ntalika
Woitanidwa mchoonad Samasowq
🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏