Zomwe Chakwera Wayankhula Ku Mangochi Lelo Pa 23 Dec 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 11

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nthawi yonse sunamangidwe bwanji, Mangochi ikamvera ndiye kugunata. Uyu kwake nkuyimba mwiyo basi.

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Olo mutukwane chani palibe tawonani unyinji wa anthu munya muwona sutembelela odalitsika mwava

  • @JohnLufeyo-y8t
    @JohnLufeyo-y8t 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mmmmm zamanyazi

  • @PeterNyondo-u5b
    @PeterNyondo-u5b 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kusamalila chuma cha a Malawi😂😂😂

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Malawi is a confused national 😢😢😢

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amakondatu nyanja anthu akumeneko yapita kuti nyanja?

  • @ZayineAlick
    @ZayineAlick 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ayawo akumangochi kupepela kwambili

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munthu uyu mtendere akunenawo ngwabodza. Bwanji anasowetsa Biyeni ndi ena 8.

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chithumwa chili pambali pake

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chimanga anagawa president ndi vice wake?Umbuli basi.

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkkk ziliko