Ine Sindingasiye U Akitivizimu - Bon Kalindo
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 25 มิ.ย. 2024
- On Nyasa VoiceBox, speaking for the first time since his arrest and release on bail, Bon Kalindo, Chairperson of Malawi First, says that no amount of arrests and intimidation will stop him from engaging in activism.
Ku Nyasa VoiceBox, polankhula koyamba kuchokera pamene adamangidwa ndikutulutsidwa pa belo, Bon Kalindo, wapampando wa Malawi First, wati palibe kumangidwa kapena kuopsezedwa komwe kungamulepheretse kuchita ziwonetsero.
#malawi
Kalindo atiimira ngati yesu❤❤
Mr kalindo he is the hero of malawi what kind of a person who does not give up even if the arrest him 1M times he is a person who care about other people's pls Malawian let support this person please because if it's was you and I we was gonna give up let think Malawian please
👏🏽👏🏽👏🏽👏🏽👏🏽zoona ndithu
Booooorn Kalindooooo
Kumasiyanisaso ndi misala
Koma English ya munthu uyu plz plz akuchititsa manyazi maiko akutiseka kwambiri simungathe kupeza njira zothetsera ai,ai tithandizeni boma tikuchititsidwa manyazi ndi munthu uyu wotembereredwa .
Hmmm dziko lino ndi la azungu??
Manyaz mukuchta ndinu kkkk mbuli yoyamba ndiwe
Umakwana born kalindo chilungamo chioneke palibe zoospyezana nthawi imeneyo inatha ndi kamuzu
Ndinu hero boss I give you a respect ❤
Bon kalindo ndi mwana oopswa kwambiri
I proud of you bon kalindo
There's God in this post,all I can say is Amen
Born kalindo umatha aise and osapanga matha iwe
😂 usamaseke ife timasowa tulo kkkkkkk welcome back DC
More fire
Tianazoni present wathu
Zonsezo nchabe koma nyimbo yooo 😂😂😂😂
Umakwana kalindo
a bwana pitilizani nyimbo yo Lazaro wa Bethany nice song 😂
❤Fire
Kalindo wooye
Tate wathu
Kodi akumachita kumulanda maphone?
Osaopa koma tiima pachulungamo
❤❤
Karido ❤❤❤❤
Osawasiya amenewa tiye nawo winiko
Umakwana kalindo......
Koma mwana ameneyo ngati alikodi akamupeza anthu amupha kaya.
DC mwana ooopsa kwambiri 😂😂
Mumakwana popanga Donate kuboma lamalawi Mr bon kalindo
Bon Kalindo ,The DC!!!!!!!
😘😘😘
💝❤❤❤ D C
Abwana donate more kwa anthuwa akuoneka kuti umphawi wavuta
😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂Kalindo eish
Katswiri
😂😂😂
😂😂😂😂😂
😂
😂😂😂