ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
My favorite ❤️ song 💜
Very nic
Away from Zambia, dats dop 🔥💪
A woman of golden voice.
One of my favorites 🔥🇲🇼
Gud song
nice song fire
Love it 💕
Its a nice track
3 years later and here I am 🥹❤️
The visuals and the lyrics are so emotion invoking
Qqqqp
this is such a uniqur peice. i cannot understand the lyrics but of course, music is boundless ofany language.♥️♥️♥️♥️keep up the good work.
Where is chipililo mwanchenga?
Ritaa_Mubwere lyricsOh, Sispence, oh oh ohRitaa.. Hello?(Verse 1)Munachoka kuti mukukasaka ndalamaMpaka lero simunabwelerensoMunachoka kutisiya ndi amai athuKoma simunabwelere..Simumatumizanso chithandizo kunyumbaKoma zoti mukuchita bwino tikumvaSitimadziwa ngati mumatiganiziraSitimadziwa ngati mumatikumbukira(Chorus)Mubwere kunyumbaMubwelere kunyumbaMubwere kunyumbaMubwelere kunyumba..(Verse 2)Tinakula, otilera anali mai athuKuvutika pamodzi ndi amai athuKomanso mutangopita,achimwene anatisiyaAna anu akungolira,Chilichonse kuvutikiraPhone yokha mukanatiimbira (hello?)Kalata yokha mukanatilembera (you know)Sitimadziwa ngati mumatiganiziraSitimadziwa ngati mumatikumbukira(Chorus)Mubwere kunyumbaMubwelere kunyumbaMubwere kunyumbaMubwelere kunyumba(Bridge)Ohh, mubwelere kunyumbaOh, oh , oh ..Mubwelere kunyumba(Chorus)
My favorite ❤️ song 💜
Very nic
Away from Zambia, dats dop 🔥💪
A woman of golden voice.
One of my favorites 🔥🇲🇼
Gud song
nice song fire
Love it 💕
Its a nice track
3 years later and here I am 🥹❤️
The visuals and the lyrics are so emotion invoking
Qqqqp
Qqqqp
this is such a uniqur peice. i cannot understand the lyrics but of course, music is boundless ofany language.♥️♥️♥️♥️
keep up the good work.
Where is chipililo mwanchenga?
Ritaa_Mubwere lyrics
Oh, Sispence, oh oh oh
Ritaa.. Hello?
(Verse 1)
Munachoka kuti mukukasaka ndalama
Mpaka lero simunabwelerenso
Munachoka kutisiya ndi amai athu
Koma simunabwelere..
Simumatumizanso chithandizo kunyumba
Koma zoti mukuchita bwino tikumva
Sitimadziwa ngati mumatiganizira
Sitimadziwa ngati mumatikumbukira
(Chorus)
Mubwere kunyumba
Mubwelere kunyumba
Mubwere kunyumba
Mubwelere kunyumba..
(Verse 2)
Tinakula, otilera anali mai athu
Kuvutika pamodzi ndi amai athu
Komanso mutangopita,
achimwene anatisiya
Ana anu akungolira,
Chilichonse kuvutikira
Phone yokha mukanatiimbira (hello?)
Kalata yokha mukanatilembera (you know)
Sitimadziwa ngati mumatiganizira
Sitimadziwa ngati mumatikumbukira
(Chorus)
Mubwere kunyumba
Mubwelere kunyumba
Mubwere kunyumba
Mubwelere kunyumba
(Bridge)
Ohh, mubwelere kunyumba
Oh, oh , oh ..
Mubwelere kunyumba
(Chorus)