ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Komatu simene ndimayembekezera2, adha awa ndi dolo kwambili ndipo sanatchule munthu aliyense aziweluze yekha Beautiful song🔥🔥🔥🔥
Omwe tabalalika let's gather here😅
.. nyali yawo dziwa siingawale ngakhale azime yako..!. koma @mlaka
Nyimboyi koma sikubheba honestly...Aaaaaaa
Bola yemweu basi ❤❤
Macadet onse sakunvetsa ...tikut nabola chakwera emweyu....💯💯💯💯💯
Sound yabwino inja mwalowesa ndale Adan okuda milomo or achakwelawo kukuziwa sakuziwa
Massage ikutibalalisa mwina vuto ndine aaaaa ndazisiya
Yochemerera Chakwera eeee Zilikotu Ziliko
Bola manganya emweyu osati kabambe, tikudziwa mwalowa mpingo chifukwa cha kadona ka koma nanga kakadzakukani muzidzapepherabe muno??😂😂😂😂❤❤
@@enerstkadyamikondo4790 iwe nde waitolera!ine chidzungulire🤣🤣
Munthu wamkulu kuposa nyumba ulemu wanu big mlaka
Composition 💯%
On repeat mbali yakuno koma tanthauzo lake sindikulipezabe 🤣🤣🤣🤣 zikundimvekera ngat wabaya mbali zonse🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ndalira undimenyeranji ndalakwa chiyani bwanji sunanene pomwe ndakufinyapo. Dzikodi limakomera zimbalangondo
Mwina akuti nabola Kabambe yemweyu
Always on point🔥🔥💯💯💯
The legend never disappoints, inuyo simunapalepo, Zambia approves
eeish simmene anthu ambiri tinkayembekedzera potengera manong'onong'o... koma Ankolo inuyo ndi dolo 🔥
Nice 1 Mr Mlaka 🥳
Simply superb
Iyi akangoivela bushiri usanja uwolokaso🔥🔥🔥🔥
Vinyo adakalipo koma vuto ndi uko wapitako
Munthu wa mulungu nkhaniyi sinathebe et
Best one
Mlaka never disappoints wat master peace 🔥🔥 much love from Zambia 🇿🇲
Dan luuu tasangalala kuti mwalowa mcp koma mlaka akuti akudziwa kuti mukuzembela mkaziyu koma akapanda kukupasan udindo muyendabe mlaka ❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndinu dolo kwambiri.. parabéns respeito
Michael Usi nyimboyi ndiyake ndithu
Mbambande
Katswiri katatu 🔥🔥mlaka ndi mlaka basi
Beautiful song❤
Mlaka ndi Mlaka basi, nduchita kulephera kuti ndimve kuti akupereka Uthenga wanji
Ndihit 🔥
Kuimvela mdi mtima wauzimu muli uthenga wamphamvu koma muntima mwakuda uzingogwa chifufu ngati akunena iwe
Kuswakuswa
Vinyo watha
My musician love you bro
Best ever.... 🇲🇼🇲🇼🇲🇼💪🎤🎙️
Best ever, Mlaka ndi Mlaka
boladi yemweyu
Aliyense aziweluza Yekha Mlaka sanatchule munthu kk
Dolo ka handede
Kaya akuti chani nyimboyi?
🔥🔥🔥🔥🔥
Angoni nditanthauzileni
Phawafu
Best composition
Kuswakuswa❤
Best
Chakwela si ndalama sangakomdedwe ndaliyense
Katswiri kwambiri
Watching from Nyimba Zambia
Nice song
Vinyo anatha mlaka
That's the Mlaka we know,kuswakuswa real sound indeed
What a nice masterpiece 🛑
The best song
nice tune
The legend never die....fada iyi mwapha zantchito zenizeni....
Best song. We call this maturity in composition at it's best
Kukuluwika ndiye mumatha
🔥🔥
fazalawa awawa nyimbo zao zimafunika ka Dictionary pambali
Waiting
Chikangawa 😢
Legend
Gud song
Eeeh, koma amkolo mumaimba
Wa chilungamo samakondadwa kwambiri ndi anthu chifukwa anthu tinasankha mdima tidadana Nako kuwala
Nyimbo imeneyi nde mwathyakula brilliant one
can't wait
Bro umatha kuyimba
True definition of mkuluwiko
koma ndiye mmmh
Guys I replayed this song but still I'm confused, there is anyone can explain for me please
A Mlaka paka tipange chidzungulire zomwezi? 🤔
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mwaimba boh koma uthengawo nde olakwika
Mlaka ndi mlaka bas 😂 kungodutsamo chete
Mwati bwanji?? I'm not getting the storry
Eeeeeee amene wamba nyimboyi zomwe ikukamba ulemu wake... mbali zakuno beat yo ndye ikuvinika.
Perfect
I need to listen in different angles to understand the lyrics... Inuyo ndiwakulu biggy
Keanu anthu anthu akufa ndi njala galu
Pantumbo panu ndinthu
legend
Nice
Ana a 2000 sangaikonde nyimboyi 😂
Too much mikuluwiko palibe tikunvapo ati Chan 😂😂
I'm 100% confused 🤔
Apotu
iyiyi ndi nyimbo ya aliyense...ilibe chipani....that's MATURITY...
Chilungamo pamaso mumtima zigawenga Malawi siwopusa sangapange dzina kawiri
Mlaka ndi mlaka basi
The are messages in the song this guy can confuse audience as it is
Tonse timayembekezela kut nd political song bwelani kuno
Koma mcp mukugula oimbatu
Simene kuliri.Boma ndilomweli 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Mlaka ndi mlaka
ndi chorus yokha yo yomwe ikundipomboneza koma nyimboyi ndi mwala....and ili neutral apapa za dyedwa mwaulele
NoNoooooooo
Good artist, good music, well composed but going to the wrong Person
still loading
1960 🤣😂
Timayembekeza kutukwana koma apa tikuchita kusowa poyambira.watikuluwila mlaka.bas angojgala emweyo nanga titani🤣🤣🤣
Komatu simene ndimayembekezera2, adha awa ndi dolo kwambili ndipo sanatchule munthu aliyense aziweluze yekha
Beautiful song🔥🔥🔥🔥
Omwe tabalalika let's gather here😅
.. nyali yawo dziwa siingawale ngakhale azime yako..!
. koma @mlaka
Nyimboyi koma sikubheba honestly...
Aaaaaaa
Bola yemweu basi ❤❤
Macadet onse sakunvetsa ...tikut nabola chakwera emweyu....💯💯💯💯💯
Sound yabwino inja mwalowesa ndale Adan okuda milomo or achakwelawo kukuziwa sakuziwa
Massage ikutibalalisa mwina vuto ndine aaaaa ndazisiya
Yochemerera Chakwera eeee Zilikotu Ziliko
Bola manganya emweyu osati kabambe, tikudziwa mwalowa mpingo chifukwa cha kadona ka koma nanga kakadzakukani muzidzapepherabe muno??😂😂😂😂❤❤
@@enerstkadyamikondo4790 iwe nde waitolera!ine chidzungulire🤣🤣
Munthu wamkulu kuposa nyumba ulemu wanu big mlaka
Composition 💯%
On repeat mbali yakuno koma tanthauzo lake sindikulipezabe 🤣🤣🤣🤣 zikundimvekera ngat wabaya mbali zonse🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ndalira undimenyeranji ndalakwa chiyani bwanji sunanene pomwe ndakufinyapo. Dzikodi limakomera zimbalangondo
Mwina akuti nabola Kabambe yemweyu
Always on point🔥🔥💯💯💯
The legend never disappoints, inuyo simunapalepo, Zambia approves
eeish simmene anthu ambiri tinkayembekedzera potengera manong'onong'o... koma Ankolo inuyo ndi dolo 🔥
Nice 1 Mr Mlaka 🥳
Simply superb
Iyi akangoivela bushiri usanja uwolokaso🔥🔥🔥🔥
Vinyo adakalipo koma vuto ndi uko wapitako
Munthu wa mulungu nkhaniyi sinathebe et
Best one
Mlaka never disappoints wat master peace 🔥🔥 much love from Zambia 🇿🇲
Dan luuu tasangalala kuti mwalowa mcp koma mlaka akuti akudziwa kuti mukuzembela mkaziyu koma akapanda kukupasan udindo muyendabe mlaka ❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndinu dolo kwambiri.. parabéns respeito
Michael Usi nyimboyi ndiyake ndithu
Mbambande
Katswiri katatu 🔥🔥mlaka ndi mlaka basi
Beautiful song❤
Mlaka ndi Mlaka basi, nduchita kulephera kuti ndimve kuti akupereka Uthenga wanji
Ndihit 🔥
Kuimvela mdi mtima wauzimu muli uthenga wamphamvu koma muntima mwakuda uzingogwa chifufu ngati
akunena iwe
Kuswakuswa
Vinyo watha
My musician love you bro
Best ever.... 🇲🇼🇲🇼🇲🇼💪🎤🎙️
Best ever, Mlaka ndi Mlaka
boladi yemweyu
Aliyense aziweluza Yekha Mlaka sanatchule munthu kk
Dolo ka handede
Kaya akuti chani nyimboyi?
🔥🔥🔥🔥🔥
Angoni nditanthauzileni
Phawafu
Best composition
Kuswakuswa❤
Best
Chakwela si ndalama sangakomdedwe ndaliyense
Katswiri kwambiri
Watching from Nyimba Zambia
Nice song
Vinyo anatha mlaka
That's the Mlaka we know,kuswakuswa real sound indeed
What a nice masterpiece 🛑
The best song
nice tune
The legend never die....fada iyi mwapha zantchito zenizeni....
Best song. We call this maturity in composition at it's best
Kukuluwika ndiye mumatha
🔥🔥
fazalawa awawa nyimbo zao zimafunika ka Dictionary pambali
Waiting
Chikangawa 😢
Legend
Gud song
Eeeh, koma amkolo mumaimba
Wa chilungamo samakondadwa kwambiri ndi anthu chifukwa anthu tinasankha mdima tidadana Nako kuwala
Nyimbo imeneyi nde mwathyakula brilliant one
can't wait
Bro umatha kuyimba
True definition of mkuluwiko
koma ndiye mmmh
Guys I replayed this song but still I'm confused, there is anyone can explain for me please
A Mlaka paka tipange chidzungulire zomwezi? 🤔
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mwaimba boh koma uthengawo nde olakwika
Mlaka ndi mlaka bas 😂 kungodutsamo chete
Mwati bwanji?? I'm not getting the storry
Eeeeeee amene wamba nyimboyi zomwe ikukamba ulemu wake... mbali zakuno beat yo ndye ikuvinika.
Perfect
I need to listen in different angles to understand the lyrics... Inuyo ndiwakulu biggy
Keanu anthu anthu akufa ndi njala galu
Pantumbo panu ndinthu
legend
Nice
Ana a 2000 sangaikonde nyimboyi 😂
Too much mikuluwiko palibe tikunvapo ati Chan 😂😂
I'm 100% confused 🤔
Apotu
iyiyi ndi nyimbo ya aliyense...
ilibe chipani....
that's MATURITY...
Chilungamo pamaso mumtima zigawenga Malawi siwopusa sangapange dzina kawiri
Mlaka ndi mlaka basi
The are messages in the song this guy can confuse audience as it is
Tonse timayembekezela kut nd political song bwelani kuno
Koma mcp mukugula oimbatu
Simene kuliri.Boma ndilomweli 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Mlaka ndi mlaka
ndi chorus yokha yo yomwe ikundipomboneza koma nyimboyi ndi mwala....
and ili neutral apapa za dyedwa mwaulele