ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Keep it up mr Dc
Aaaaaaaaa koma kalindo ndi munthu wankulu kwambili ndipo amayankhula saopa kanthu
Kkkkk koma Born aaaa ndi president wanthudi ,l salute you sir
Ndimadikira Dc kuti lero atichani apa nditha kukagona 😂😂😂 Boni kalindooooooooo!!!
Kkkkl mpaka police 200 koma bon kalindo ndimunthu okwiya kwambiri 😂😂😂😂😂
Bon kkkkkkkkk akuti aputa milandu yambiri iwe ndi 1 basi kkkkkk
Eeeee ai ndagonja nanu big up a 🙋DC
Mr kalindo ife tidalira inu basi❤❤❤
Wakumuzi kwenikwenni za pa social media -zi saziziwa kuti inu muma -aimilira
😂😂😂😂😂😂😂😂😂Nyau kumva pain 😂😂😂
Kod Aku Germany aja bas angotithera ndalama mosemuja lipot osabwerensa aaaa ndiye angopita kwawo wapas amenewo iyaaa
It's the Dc keep it
Kodi kwanu sanakuvoteren bwanji😢😢
Ichichi sichamasewera Adaaa😂😂
🤝🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🤝🤝🤝🤝
DC 🥰
Bon kalindooooooo
Za Imfa Ya Chilima Tisaopsezane, Ngati Simunamuphe Tiuzeni Kuti Chinachitika Ndichani? Ku MCP musabise zinthu zoti munapanga nokha, Chakwela Ukhale ndimanyazi Ubusa wake Uti Unkapanga iwe Okupha Nzako Chifukwa Chautsogoleli?
Wanthu wanthu DC 💪
DC ❤
Ndodo ija ituluke DC tatopa ndi chakwera ife kkkkkkkkkkk the DC ❤❤❤❤
Kkkkk chikumvesa kukoma a Malawi ambili
KkkkkkkkMwana ovuta kulera Hehehehe
Amafuna kukuipisirani Mr DC koma akunama 💪
Bon Kalindo the DC (The most dangerous child)❤❤❤❤❤❤
Mwana woipa kwambiri😂😂😂
🤣🤣🤣🤣 mpaka a police 200 kkkkk
The DC salute
The DC, ndipo anthu tizamulilira kwambri mkului nd ntchto yakei akazasamira mkono
The braval child of Malawi, Speak out without fear and favor! Bon kalindo, The DC...
😂😂😂😂😂the DC machine
Winiko the DC pachilungamo sumawopa iweyo umatha
❤❤❤❤❤ more fire 🔥
boni kalindo malawi 😂😂😂😂
Bon Kalindo
Mr Dc mumakwana inuyo tilinanu ife amalawi
The DC
zopanda ntchito zomwe ukulu inu mumalankhula
Chizagwira zipolopolo😅😅 iwe ndi machine, wait to destroy them with you
Umakwana DC
The DC🔥
It's plezident of poor people
The DC!
Uyu yekha timuteteza I swear
The DC 😂😂😂
Kulankhula wina aliyese atha kulankhula koma kuchita zakupsa...Bwana Bon kalindo akumalankhula koma ndi action yanji yomwe ikuchitika? We need kulankhula ndikuchita namaona progress..Mukatiuza zomwe mwapezazo kenako muzinenanso kuti tipanga izi pothana ndizimenezi...tisamangokhalira kumva mwana oopsa mmalankhulidwe, action nothing
Inu mene mwayankhulamu mwapanga action yanji? Kkkkkkkkkk
Kkkk mbuli ife timakonda DC
@@myheartforkids2876 Amene amawatsata omenyera ufulawa atha kudziwa kuti nthawi ya Bingu kunali Mavuto Bamusi ndipo amati akanena amapanga action ndipo Mpaka Bingu anasintha machitidwe azinthu zina, nthawi ya Peter kunali Timothy Mtambo, za amenewu mukudziwa zomwe amachita, Koma Bwana Bon mmmm tiyeni tizingomva Mwana oopsa komanso kung'alura kenako tiseke osaona chisintha...I always appreciate for actions not talking that's why tonse Government tikudana nalo coz nawoso kulankhula amatha koma kukwanilitsa kukuwavuta
DC mewafika
The DC umakwana
Chipangoline😂😂
Zamanyi basi kape ndiweyo akanadakhala Ofuna kupha akanampha iweyo umatisokoneka mutu amakutuma ndindani? Umango uwanamizila anthu wosawuka ndidziko lanji lomwe kungapezeke wolemera wose?
Iwe akupasa zingati koma inu ndi onvesachifundo kupusa uchisru
Nyau imeneyi itayeni
Matako ako nyau iwe
Kape uyu
Even ur voice doesn't sound like a leader
😂😂😂😂😂
😂😂
Ati amangidwe ndamako
😂😂😂😂😂Amangidwadi ndi amake a Chakwera 😂😂
😂😂😂
Kkkk
Keep it up mr Dc
Aaaaaaaaa koma kalindo ndi munthu wankulu kwambili ndipo amayankhula saopa kanthu
Kkkkk koma Born aaaa ndi president wanthudi ,l salute you sir
Ndimadikira Dc kuti lero atichani apa nditha kukagona 😂😂😂 Boni kalindooooooooo!!!
Kkkkl mpaka police 200 koma bon kalindo ndimunthu okwiya kwambiri 😂😂😂😂😂
Bon kkkkkkkkk akuti aputa milandu yambiri iwe ndi 1 basi kkkkkk
Eeeee ai ndagonja nanu big up a 🙋DC
Mr kalindo ife tidalira inu basi❤❤❤
Wakumuzi kwenikwenni za pa social media -zi saziziwa kuti inu muma -aimilira
😂😂😂😂😂😂😂😂😂Nyau kumva pain 😂😂😂
Kod Aku Germany aja bas angotithera ndalama mosemuja lipot osabwerensa aaaa ndiye angopita kwawo wapas amenewo iyaaa
It's the Dc keep it
Kodi kwanu sanakuvoteren bwanji😢😢
Ichichi sichamasewera Adaaa😂😂
🤝🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🤝🤝🤝🤝
DC 🥰
Bon kalindooooooo
Za Imfa Ya Chilima Tisaopsezane, Ngati Simunamuphe Tiuzeni Kuti Chinachitika Ndichani?
Ku MCP musabise zinthu zoti munapanga nokha, Chakwela Ukhale ndimanyazi Ubusa wake Uti Unkapanga iwe Okupha Nzako Chifukwa Chautsogoleli?
Wanthu wanthu DC 💪
DC ❤
Ndodo ija ituluke DC tatopa ndi chakwera ife kkkkkkkkkkk the DC ❤❤❤❤
Kkkkk chikumvesa kukoma a Malawi ambili
Kkkkkkkk
Mwana ovuta kulera
Hehehehe