```Zomwe lipoti lakanikabe kuyankha ndi izi 1. ...anamuletsa chimwendo banda kusakwera ndege !!! (......./) sakumutchula 2..... . anazimitsa phone ya modzi mwa okwera ndege ndani ???(........) Ndege yokwa 10:16 am phone inazimisidwa pa 10:26 malingana ndi a airtel 3....... Chifukwa chani boma limayamba kutsaka ndege mochedwa (.........) Ndege yogwa pa 10:16am kuyamba kutsaka pa 17:00 pm 4..... Anamukakamiza chilima kukwera ndege ndi ndani poti aku office ya chilima ati iyeyo amafuna ayende pa galimoto ??? (..........) 5........kodi ndege inali ndi black box or ai ( apapa ndiye sanakambe or kamodzi 🕵😂) mukubitsa chani ???? 6.......ndege yoti inali ndi mafuta a 4hrs itagwa bwanji sinayake ndi pa modzi pomwe ndege yoti yachoka mwamba ???? (............) 7.........akuti a chakwera sanaziwe kuti chilima wabwera kuchoka Ku koleya kufikira kunva kuti ndege yake ya Malawi momuno yasowa ???(......koma zoona izi 😂) 8...... Kodi anawaudza a chakwera kuti ndege yafika Ku mzuzu ndi ndani ??? ( ....... Tsongoleri wa dziko ananamidza dziko apap ) Ndimwere kaye madzi 🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵 Tawatchulani anthuwo dziko liwaziwe mukubisiranji?? Dziko likufuna limuziwe yemwe anamuuza chimwendo banda kuti asakwere ndege komanso yemwe anazimitsa phone si choncho Kodi amalawi anzanga
Inu ndemukufunika kukapanga kafukufukuwu tikasintha Somali 2025 chifukwa apa ndiye tapakidwa mabi. A doctor Dzamalala sakubwera kudzafotokoza zomwe anapeza chifukwa choti anthuwo anaphedwa ndipo sakufuna kuperekela umboni wabodza cz akuopa kuphedwa nawonso choncho asankha kukhala chete 😢 ndipo nkanakhala ine Mulungu nkanangodzutsako mmodzi mwaachifwambawa MCP member to expose all who have hand in this terrible death's. Even Ralph Kasambala was murdered and Sidic Mia 😢 God is watching us 🙌🙌💔💔😭😭
ayankha mulandu amenewa pompano...tadekha
```Zomwe lipoti lakanikabe kuyankha ndi izi
1. ...anamuletsa chimwendo banda kusakwera ndege !!! (......./) sakumutchula
2..... . anazimitsa phone ya modzi mwa okwera ndege ndani ???(........)
Ndege yokwa 10:16 am phone inazimisidwa pa 10:26 malingana ndi a airtel
3....... Chifukwa chani boma limayamba kutsaka ndege mochedwa (.........) Ndege yogwa pa 10:16am kuyamba kutsaka pa 17:00 pm
4..... Anamukakamiza chilima kukwera ndege ndi ndani poti aku office ya chilima ati iyeyo amafuna ayende pa galimoto ??? (..........)
5........kodi ndege inali ndi black box or ai ( apapa ndiye sanakambe or kamodzi 🕵😂) mukubitsa chani ????
6.......ndege yoti inali ndi mafuta a 4hrs itagwa bwanji sinayake ndi pa modzi pomwe ndege yoti yachoka mwamba ???? (............)
7.........akuti a chakwera sanaziwe kuti chilima wabwera kuchoka Ku koleya kufikira kunva kuti ndege yake ya Malawi momuno yasowa ???(......koma zoona izi 😂)
8...... Kodi anawaudza a chakwera kuti ndege yafika Ku mzuzu ndi ndani ??? ( ....... Tsongoleri wa dziko ananamidza dziko apap )
Ndimwere kaye madzi 🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵🕵
Tawatchulani anthuwo dziko liwaziwe mukubisiranji?? Dziko likufuna limuziwe yemwe anamuuza chimwendo banda kuti asakwere ndege komanso yemwe anazimitsa phone si choncho Kodi amalawi anzanga
Ndichoncho ndithu osati zamkutu zawozi
Inu ndemukufunika kukapanga kafukufukuwu tikasintha Somali 2025 chifukwa apa ndiye tapakidwa mabi. A doctor Dzamalala sakubwera kudzafotokoza zomwe anapeza chifukwa choti anthuwo anaphedwa ndipo sakufuna kuperekela umboni wabodza cz akuopa kuphedwa nawonso choncho asankha kukhala chete 😢 ndipo nkanakhala ine Mulungu nkanangodzutsako mmodzi mwaachifwambawa MCP member to expose all who have hand in this terrible death's. Even Ralph Kasambala was murdered and Sidic Mia 😢 God is watching us 🙌🙌💔💔😭😭
Wonders will never end
Ndani anayamba kufika pamalopomwe ngoziyo idachitikila? Tikaziwa anthuwo atiwuza komwe ndalama zidapita chifukwa ndege siingabe ndalama plz adalakwanji chilima moyo uno ukupweteka kwambiri akuzikolakola abomawa
Mafon aja anakafufutilanji ma whatsap ma dial calls ma text anawafutilanji asilikali aku Rwanda ankazani