I respect you Eng Newton Kambala, we need people like you to lead our nation, and also please make policies for our country to make private sector or business more profitable than politics then our country economy will improve. I agree with you we need more engineers in positions for our country to develop.
Where have u been Leah? We missed your interviews, ur so brilliant in asking questions, Kqmbala is very cleaver amafunika iwe Leah. I regret kuti kwachitika ma interviews mmbuyomu koma aaaaaa ofusa wake manyaka eni eni
Osatchula bwanji, zoganiza bwino zake ziti. Simunaonelepo video akunena kuti azaimira pa yekha ku Chilimba?... Musamukakamize, Usi had his intentions, ichi chakoma ichi chakoma...
Eeee koma uyu ndikatundu l think Kambala ndimunthu ofunika kwambr ku UTM big up bwana and you Leah kufunsa kwabwino bring it on mukumatimvetsa kukoma hvy ndi mzako wa ku times Cathy
Some questions from Lea Malekezo are very stupid, no need to be answered, for example kodi utm inayamba bwanji? This questions can not change anything, I like your confidence my Newton Kambala, even I personal I do feel not only feel but I am confident enough that it was not a normal accident that claim chilima's life
Nafenso abwino Lea Koma chonde muwauze ma camera man azikhala serious kumayenda kutsogoloko Mmmm Ai mwina muzipasa mpata kumapeto kwa programme Kuti naonso aonekepo pa programme chifukwa akumasokoneza palibe desplin
ZA IMFA YA CHILIMA ZIDZATIVUTA KUVETSETSA , KOMA TIMALIMBA MTIMA CHIFUKWA CHA MAU A MULUNGU , MAU A MULUNGU AMANENA KUTI MUNTHU ALIYENSE MULUNGU ADAMULEMBERA MALILE OKHALA PANO PA DZIKO LAPANSI, TIYENI CHINA CHAKE CHODZIDZIMUTSA CHIKACHITIKA CHIKHALE PHUZIRO KWA MIYOYO YATHU KULAPA NDI KUTEMBENUKA MTIMA , KULUMIKIZANA NDI MULUNGU. MULUNGU
Ine mpaka pano 3 years now no connection ku Escom ndalama kungotenga kukhala pansi angot ma meter kulibe ma meter akabwela ma wire kulibe and yet wina wangobwela kumene kumanga nyumba magetsi ali ngweeee very sad
Mr Newton Kambala you have transformed my mind...... Its high time we as a nation we need to start being business oriented we have countries liks Tanzania, Zambia and Rwanda they transformed there countries.
This gentleman is very humble, shrewd and wise. If he win in convention I'll truly vote for him
An eye opener to hear the other side of the story. Thank you for being open and direct to your answers
matured,confident,precise,coincise,composed. I am impressed
Totally impressed as well
Kulakhula kwa kambala ndikomwe kumafunika kut amalawi adzikuva ndithu mulungu akusunga wathu wakut angatha kupanga support nyengo zamalawi ❤❤❤❤❤❤ ndakudziwani lelo akambala god bless you sir
All UTM candidates are brilliant than any part in Malawi who ever wins will shine the part again
I respect you Eng Newton Kambala, we need people like you to lead our nation, and also please make policies for our country to make private sector or business more profitable than politics then our country economy will improve. I agree with you we need more engineers in positions for our country to develop.
Amazing, wonderful, fantastic interview, Leah, you are the best 😢
This man is so honest in his speech..bravo
Mumawadziwa anthu a ndale inu?? Aaa muu
Even kumene amakhala anthu amawayamikira ndi munthu wabwino kwambiri odzichepetsanso
Kambala namudziwa lelo ndi katundu
"Engineers don't talk, they do things" I quote
Koma muwauze ma colleagues anu kumeneko asamayende yende mkati mwa program, that's very unprofessional.
Kambala my vote,,,,a
ESCOM ine 8 years magetsi chilipilireni koma sakulowa eish
Where have u been Leah? We missed your interviews, ur so brilliant in asking questions, Kqmbala is very cleaver amafunika iwe Leah. I regret kuti kwachitika ma interviews mmbuyomu koma aaaaaa ofusa wake manyaka eni eni
Panja Ali ndi baby,, aanali kokozekera baby
I have known today that this gentleman is is genius
Exactly
Maturity ,humble nd well spoken man......Mr you derseve to be Utm president
Welcome back Leah we miss u
U can say it again ❤
Kabambe is the only hope ku utm mukapanga mistake kusankhawina mwatherapat
*SKC 😢😢azayankha afune asafuna ine mupaka pano chilima ndikuwon ngati anapita zikolina kut zambweraso koma kuliziii
Usi ndi katundu onganiza bho ndipo siku lina muzamukumbukila
Ndipo zoonadi
Osatchula bwanji, zoganiza bwino zake ziti. Simunaonelepo video akunena kuti azaimira pa yekha ku Chilimba?... Musamukakamize, Usi had his intentions, ichi chakoma ichi chakoma...
Kambala is the right person to be a reader took true and wise .no fear .viva kambala viva 🇲🇼
Apapa ndikuona kuti Dr usi zomwe akudandaula nzowonadi akuzunzidwa, akambalawa sali owongoka ndipo akufuna atatengadi chipanichawo cha utp.
Ndinvele nawo ine.. i will drop my comment at the end
Usi is innocent at utm.vuto ndiloti he is working with utm's best enemy
This guy is genius and well connected
Viva UTM
Eeee koma uyu ndikatundu l think Kambala ndimunthu ofunika kwambr ku UTM big up bwana and you Leah kufunsa kwabwino bring it on mukumatimvetsa kukoma hvy ndi mzako wa ku times Cathy
Engineer Kambala,confident,matured and truthful and precise
Dolo..I like his composure..From this interview ma guy ena aja ali kutali ndi kambala
Rest well my president @SKC. I'll live to remember & respect you 😭
Kunena chilungamo bwanawa akuenela kukhala president wa dziko lino ali bhoo kwambiliiiiiii!!
Mhu koma!! Munthu ndithu lero akanene kut "nditha kukonza dziko!!" Koma mumapitadi ku Church n mumawerenga baibulo inu?? Yeremiya 10 : 23 mutawerenga zomwe amanena komaso Masalimo 146 : 3 komaso Masalimo-wo tawerengani chapter chonse Salimo 146 : 1-10 mwina mukawerenga ma chapter amenewa mitu yanu itsekuka n muzindikira kut ayenerera kulamulira komaso anthufe tikuyenera kulamuliridwa ndi Yehova basi❤
Munthuyu muli nzeru kwambiri, komaso alibe mantha. Malawian needs people like him.
Ambience yanutu ndiye siili bwino a Zodiak
To my side this guy deserves to be president adviser
She is back!!! We missed you Leah❤
Good interview, very informative 👍
Next time work on the background noise
Kuli moto pa Sunday. Moto kuti buuu!
Waz he really absent.? Willingly or unwillingly. A soft coup happening there.
engineer kambala is the right çandidate for utm no matter what
Welcome aunt Lea how is ababy❤
koma ku UTM Kuli mambomba🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤❤❤koma za amayi mere chilima mwakambazi ndizoona akhoza kukhala sogoleli wabwino chifukwa ndimakhulupilila kuti akuziwa zambili za amuna awo komaso ankakondani ukamakondana kwambili ndi nkhazi wawo akuenela kuziwa zambili
Newton Kambala my vote UTM convention
This man is genius ❤❤🎉🎉
Some questions from Lea Malekezo are very stupid, no need to be answered, for example kodi utm inayamba bwanji? This questions can not change anything,
I like your confidence my Newton Kambala, even I personal I do feel not only feel but I am confident enough that it was not a normal accident that claim chilima's life
Welcome back Leah Malekano. We missed you
Watch and listen with a Sober mind...
Interview of the year.......
Ineso ndalandilapo nsalu za utp he is a smart guy
Humble as well
I ❤ this!
What was all that background noise about Leya
UTM has pillars, if they all stay put after convention, the future is bright.
I love his honesty
All utm candidates are brilliant
Welcome back Leah Malekano
44:43 He is the right candidate of UTM
Mukamuona mchewa ku Southern Region or Northern Region Iphani
Nafenso abwino Lea Koma chonde muwauze ma camera man azikhala serious kumayenda kutsogoloko Mmmm Ai mwina muzipasa mpata kumapeto kwa programme Kuti naonso aonekepo pa programme chifukwa akumasokoneza palibe desplin
Mzeru zilimo koma mmafatsa kwambiri nde anthu samakudziwani Bola muiphule ku convention then mulankhule kumtundu wamalawi
Nonse ma aspirants nde nd a mzeru and ngt pangakhale ma alliance UTM ikuyenela kuzasogola
ZA IMFA YA CHILIMA ZIDZATIVUTA KUVETSETSA , KOMA TIMALIMBA MTIMA CHIFUKWA CHA MAU A MULUNGU , MAU A MULUNGU AMANENA KUTI MUNTHU ALIYENSE MULUNGU ADAMULEMBERA MALILE OKHALA PANO PA DZIKO LAPANSI, TIYENI CHINA CHAKE CHODZIDZIMUTSA CHIKACHITIKA CHIKHALE PHUZIRO KWA MIYOYO YATHU KULAPA NDI KUTEMBENUKA MTIMA , KULUMIKIZANA NDI MULUNGU. MULUNGU
Omwe tidzavotele Kambala lets gather here tiwelengane kuchitila kuti tikawina ma udindo asazavute kugawana🤣
Hahahaha
Hahahaha
Kambala is a great man
Akawina, @kabambe mukasuma ku court? @kambala
Kambala my vote
Ma twins ali bwanji ❤❤❤ welcome back Leah
President ndiemweyi❤
Km ku UTM muli ma good leaders i can't lie
Ine mpaka pano 3 years now no connection ku Escom ndalama kungotenga kukhala pansi angot ma meter kulibe ma meter akabwela ma wire kulibe and yet wina wangobwela kumene kumanga nyumba magetsi ali ngweeee very sad
SKC continue resting in peace!!!
Kambala yi sindimamuziwa bwino bwino
DPP muzimva mulungu akuwululilani zomwe zinkachitika anthu ankasokoneza aja
Guys ineyo za chilima sindimadandaula ndiamene akupangitsa kuti mpaka lelo tizivutika ndiamene anatipangita kuti tiwone mavuto
Leah unasowatu nice to see u again
Honest imfa ya SKC imatizuza koma... Si zabwino zimene zija koma
This man has full righteousness
Welcome back Leah, ❤❤
Akuti ndimakuwonela patali. 😂😂😂
Ma deligates a UTM ofunika kuchenjera ndi azipani chifukwatu azipani zina zimachita bribe madeligetsi kuti akasankhe weak candidate for their own advantage. External forces ndiyoopsa. UTM sankhani munthu wothekera kuti chipani chipite patsogolo mukangovotera kuti ayeni chipani ngakhale ali ofooka mundale DPP ndi MCP izakuvyivyinizani mwinanso position 3 yomwe oasipeza
U sound good..... wishing u the very best
1:11:30
My vote to kambala
I really love you Sir
This one is not a candidate to be the president. No to the so-called Eng Newton.
Malawi needs Economists not Engineers. Period!!!!!
Magufuli was a medical doctors you fool!!!!
Book economists? We need proven economists
Mwaonjezasotu kmeneko mungoti pakalapakala nthawi ya ntchito,tizinvela phokoso lanulo
Leah where were you, we missed you
Kabambe ndi a mtumbuka dzivereni nokha Kuti ndinu osafunikila komaso ndinu achinyengo Kumasi wanenesa kambala Kuti ndinu a tsizina mtole Moti dziwani Kuti mwalowa Mbali yoti anthu eniake a utm UTM sakukufonani
Zinaso zomwe akukamba awawa ndizabodza asamatipusitse ifeyo anthu wambafe, amafuna azioneka ngat anzeru akamayankhula pa camera, owanvera awawa ndiamene ali mbali zawo koma enafe ndie sitingakhulupirite zomwe akuyankhukazi never
Ndi munthu wa bho heavy even kudera komwe amakhala ndi munthu odzichepetsa kwambiri
Kkkkk, Asauze aliyese, nkuku uzani...
Palibe chinsinsi padzikoppa, Manganya ndi manganya
Komano akuluinuyo MCP munkaidziwa khalidwe lao chidapangitsa ndi chiyan kuti mupange Alliance ndi Mcp.
Mesa mudayamba mwaonako mu ulamuliri wao uja wakale
Lea is best 🎉
Tamva zambiri kuti pachipanda kuthesedwa mlandu chilima anali determined kutuluka mu alliance
Nkhani iyi ikula iyi sure ndipo mungoyenela muganidze bwino udindo umafunika kutsata nawo malamulo sikumukudzitenga bwino anthu inu
Akambala mmmmm inuyo musakakamire mpando wa u president,siyilan kàbambe or mtumbuka inuyo simukumaka
Dk... Ndi Kambala wii help malawi
Unfortunately Chilima is no more and aliyense atha kunena chilichonse chifukwa sangayankhe
Well spoken
Wabodza usamanamiza anthu iwe Newton Kambala (mbala)osànama chifukwa choti Chilima adamwalira sibwino àyi
Leah malekano ❤
Mavuto amene tilinawo kuno ku Malawi ndimabodza mzathu akamwalira aKambala ndi abodza Chilima sadanenepo zaudaniwu angofuna utsogoleri awawa alibe nzeru
Mr Newton Kambala you have transformed my mind...... Its high time we as a nation we need to start being business oriented we have countries liks Tanzania, Zambia and Rwanda they transformed there countries.
Ndiyekuti tinenekuti kambala ndiyo dolo osati SCK ndi mmene zikuvekelatu lelo