LERO PA MWAMBO OLUMBILISA OFUFUZA ZA NDEGE AJA - ACHAKWERA AWACHENJEZA KUTI ASAMVELE ANDALE AMISECHE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 71

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +7

    Palibe nduziona apa kadyeni ndalamazo poti zabooka, tidza panga tokha chaka chamawa kafukufuku zopusazi ayi💔💔💔

  • @WandaMinjale
    @WandaMinjale ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Apa a Tonny Nyirenda asamalitse kwambiri atha kuononga mbiri yawo ya utumiki ngati chilungamo sichioneka . Kudzakhala kutha kwao

  • @CadTafa2
    @CadTafa2 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Muyambire pa kasambar

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Palibe chingachitike apa ugalu wokha wokha chilungamo tizachipeza 2025 basi anyani awa akachoka

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      You don't know what u need guys khalani choncho.... Believe what you believe after all aliyese azafa... Even this commission of inquiry is useless..... Osauka achialubino amaphedwa aja where is there own commission of inquiry.... 😢😢

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

      ​@@wisdom20mkango49😂😂😂😂 mufuse mbuyako kt sanaike commission of inquiry ya albino chifukwa chani?? Akudziwa kt akukhudzidwa ndi njira yokhao yopha albino yomwe MCP inagwiritsa ntchito pofuna kuipitsa DPP kt avoteredwe, mma court munali milandu yambirimbiri yokhudza albino chiloweren m'boma simunapangep kanthu achina pedegu inu

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndipo zokhumudwitsa zokha-zokha izi sizingathandize kudziwa choonadi.

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Simukulumbira nonkha pamenepo??tikukuonani

  • @khasimMusa-d3w
    @khasimMusa-d3w ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyerenda Nd wa MCP chkangawa apezeka bwanji mukafukufuku ameney

  • @MadaMatiti-u9g
    @MadaMatiti-u9g 3 นาทีที่ผ่านมา

    Zonsezitu akufuna kutiphimba ife maso palibe chadzeru apa......

  • @StarchJonas
    @StarchJonas ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    sound sili bwino, zotsatiranso sizikhala bwino

  • @chimwemwechiundira6002
    @chimwemwechiundira6002 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Why the double annoying noise for?

    • @JosephIsaac-s1c
      @JosephIsaac-s1c 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      In order to confuse audiences 😢 but it's very sad

    • @JamesBrown-gx8my
      @JamesBrown-gx8my 20 นาทีที่ผ่านมา

      Mbuli zokhazokha they don't even know how sort out shit....shame

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 17 นาทีที่ผ่านมา

    Kodi ndege yopanda zonse zomwe zimanenedwa zija iweyo Chakwera ungakwere???? We are not stupid.....

  • @JibraanSharief-ol1yn
    @JibraanSharief-ol1yn ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akumana amfi wokhawokha

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy 22 นาทีที่ผ่านมา

    Inu achakwera mutsatiputsise ife amalawi ,,, olo mwana pano akudziwa kuti ndiiwe unapha chilima ,shupt man

  • @ChimzyWesley
    @ChimzyWesley ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kwamtere wasankha akuchipani ukuti anthu ankhulupirire zimenezi

  • @CrispineBetha
    @CrispineBetha 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chilungamo ife tinadziwa kale kuti chilima munachita kupha abakha inu a mcp...pano muli busy kumuzuzu Mai kaliati agalu inu.

  • @HenryChapweteka
    @HenryChapweteka 33 นาทีที่ผ่านมา

    Where is black box man?

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ziyambire pa kasambala..

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Namiwa upite kwa yasi gama mutumiki wa Mulungu ndi amene akakulumbirise mowona ukapanda apo namiwa upemphere molimba ugwa mumayesero i promise you my friend

  • @MineMoyo
    @MineMoyo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma ma baibulo omwe mukuwagwirawo mulungu akuona 😢😢😢 ngati mwatengelapo business mukusemphana ndi njira ya choona kwa mulungu

  • @wisdom20mkango49
    @wisdom20mkango49 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    If I was chakwera I couldn't point this commission of inquiry...... Where is the inquiry of Chasowa.... Albino anaphedwa aja... And 21 people who were killed ku mzuzu... Who was arrested.... Poti awa anali olemera ndiye basi busy kulubwa fwetseke

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxidwa pa ifa ya chilima

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Iyiyi siyitha bwino chiripo chimene asungira achakwera

  • @AmanaKaisi-p3e
    @AmanaKaisi-p3e 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    M'bale wanga Alide Qur an wagwirayo polumbira ukapange chilungamo,momwe chisilamu chimanenela

  • @Zebron-kg2qz
    @Zebron-kg2qz 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    TULUTSANI BLACKBOX CHOYAMBA OSATI ZOPUSA ZIMENE MKUKAMBA YAPO ZILIBE NTCHITO

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 21 นาทีที่ผ่านมา

      Yes ,, ayituluse chakwera otsati azitiuza zamanyi ife amalawi,,mfiti chakwera

  • @YNW2KSummer
    @YNW2KSummer 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chisulu uyu' akuziwa kale zamkatimo
    Angodyapo ndrama Za bomo kuphimba mmaso a Malawi basi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Yasini gama ndiyekhayo angakulumbilise mowona iwe namiwa ma judge ambiri saziwa Mulungu wamoyo ndi akatangale sangalumbilise munthu kukhala wachilungamo namiwa ndikubwerezaso kuti usanayambe ntchito yo pita kwa mutumiki wa Mulungu yasini gama ukapanda apo sukabwera ndi ma result oona pa nkhani ya ndege because azako wose ulinawo mu inquiry ndi mibulu yolusa komaso achiphamaso asankhidwa kupusisa amalawi from nkhata bay my home sweet

  • @Giftjames-k4r
    @Giftjames-k4r 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ali Galu uyo😢😢

  • @TimothyNkhutembaChirwa
    @TimothyNkhutembaChirwa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela angalumbisile chifukwa nayeso Ali mugulu

  • @akimchigaga3441
    @akimchigaga3441 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mulungu musamamutenge ngati nchimwene wanu, kulumbira mukulumbirako chonsecho chilungamo mwachipotoza kale, muzayankha pamaso pa mlengi, pamene zobisika zonse zizabwera pa mbalambanda,

  • @MikeBatson-d6k
    @MikeBatson-d6k 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bwanji osafufuza za ngozi ya ndege zaziiiii

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Galu uyu wawapatsa kale chitseka pakamwa onsewa ndiye adzitipusitsa pamaso

  • @licysaidi
    @licysaidi 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ma sound waves bwanjiso nanaaa🤦🤦🤦🤦🤦

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    ngati sound yake ikhale imeneyi ,tisayembekezele chabwino 😂😂

    • @EmmanuelkpPraise
      @EmmanuelkpPraise 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kkkkkk zovutadi

  • @austinvincent1264
    @austinvincent1264 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sound sikunvekatu bwino

  • @Khadija-q9r
    @Khadija-q9r 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    aaaaaaaaa. Zithu zija kunooo basi zalowa chipolonje

  • @IdahKadewere
    @IdahKadewere ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pali abambo ena ake pano a MCP akutukwana osakhala masewera amenewa aligulu lolembedwa ganyu ndi achina wadowado chakwera kut azipha anthu 2025 izafika nonse wakumaula boma ili akutenga ena inu muiwale muzipakuliratu

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ngakhale chakwela analonjeza kuti , zikazatha zaka ziwili asanakwanilitse zomwe walonjeza , azatula pansi udindo .
    Tingakhulupilile bwanji comission of inquiry yosankhidwa ndi chakwela him self .
    Comission of inquiry yamtunduwanji yopanda akubanja kwa chilima komanso UTM members ??

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MCP ikakutchingilani iphanipo awili kapena mmodzi anthu azitenga phunziro, muziyenda mdimipeni or ma screw drivers, this generation a MCP asatsekele njila nzake noooo

  • @DoreenLivata
    @DoreenLivata 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Muyambile pa kasambala kma kuvuta kumalawi kkkkkk

  • @MadandoChannel
    @MadandoChannel 7 นาทีที่ผ่านมา +1

    Pastor fake😢

  • @MissoutNiceday
    @MissoutNiceday 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi engineer sakukhoza bwanji zimenezi?kumalawi ndikomvesachisoni kwambili.

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tukwapikanatu apa ni ngawa ayitandeje wawojo plz wasalile Soni anyamata wawo kuti mbolembole akasokonesya

  • @BlessingsUndih
    @BlessingsUndih 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akachoka m'boma kafukufuku azakhazikisidwaso mpaka chilugamo chizaoneke

  • @WandaMinjale
    @WandaMinjale ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Izi ndindale a Tonny Nyirenda a vomera za chabè panakakhala kuti kafukufuku yu wa chitika mwezi wa June tidakati chilungamo chilipo koma pano patatha 4 month . Mavuto alipo samalani.

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi athu mukufuna chani mumafuna mukadapita inuyo aiiiii ifeyo tidikile zotsatilazo aaaaaaaaa ngat mukudziwa igopitani mukafufuze inuyo bwa

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zitiku vabwino bwino tapangani bwino zaundiwo yachamba😂

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Alani witika

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kd kilumbila kalumbila kwandani kd wina aliyetse kuno kumalawi akudziwa zoti chilima adapha ndi anthu achipani cha mcp chifukwa chagwizano omwe adagwirizana pakati pawo chilima ngati kilibe lero padziko lapansi chifukwa cha mcp ndamene adapha chilima basi

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Muchedwa nazo izi zoti ndipange kafukufuku wapadela mcp idapha chilima nkhani yata why ndikutero adamupha chilima posafuna zomwe adagwirizana after 5 year alamilile wina then 5 years inayo azalamulile chilima wakoma mpando adapanga uphandu ofuna kumisowenza chilima inde zidatheka adamupha ndeno lero kumati akalimbile akalumbila kwandani guys amalawi kd chulungamo mukudziwa km kukanikha kuyangula bwinji

  • @AndrewMdala
    @AndrewMdala ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chimene amachedwela mosemuja ndi chiyani

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 18 นาทีที่ผ่านมา

      Eti how many days ,bola ife amalawi tikuziwa kuti anachita kuphedwa

  • @Edisonsquare-d7e
    @Edisonsquare-d7e 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zawungalu bc

  • @JibraanSharief-ol1yn
    @JibraanSharief-ol1yn ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😢😢😢aneneli satanic poster a fake

  • @ELLENZAPS
    @ELLENZAPS 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kungotaya nthaw ixi okupha ndiyemweyo tseki

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 17 นาทีที่ผ่านมา

      Muziti kuwononga nazo ndalama chilungamo akuchiziwa

  • @PamexMasanjala
    @PamexMasanjala 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    mosemuj mumafuna kut mubise kaye maumbon kenako

  • @AndrewMdala
    @AndrewMdala ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tizafufuza tokha chaka chamawa panya panu

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 14 นาทีที่ผ่านมา

      Chilungamo next year chiziwika angofuna powonongera ndalama 😅

  • @KingsleyTchuka
    @KingsleyTchuka 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkkk

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Panyapako pa nyini pa manu anthu inu mwava president walakwa chani mesa mumafuna zimenezo ndiye apa mukuti chani patumbo pamanu

  • @STEVENMPONDA-o6r
    @STEVENMPONDA-o6r ชั่วโมงที่ผ่านมา

    𝚉𝚊𝚣𝚒𝚒. 𝙿𝚊𝚕𝚒𝚋𝚎𝚎 𝚌𝚑𝚞𝚖𝚟𝚎𝚔𝚊𝚊 𝚊𝚙𝚊𝚊

  • @JackInsest
    @JackInsest ชั่วโมงที่ผ่านมา

    How dare are you Chakwera , u don't have any shy , u are the one who made a plan , this commission of Enquiry will do it next year , to another Government , not your Government , we loose Hope on you and your entire Cabbinet , don't lie Malawian , we are fade up with your Government , be ready to go in prison next year with your Cabbinet and your family , will see next year , be there galu iwe