ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
I like these guys kkkkkkkk pitilizani
Anyamata akuimirira Malawi awa, olimibikila ndi luso . A Malawi akuthekera tiwakankhe. Katungwe nkukankhana tisaiwale.
Nice
But am not get other episode yathera episode 19
good story scripting i like this
I like toñde wadula
Big up from Houston. That's my village born and raised. Brings good memories
I like tonde wadula comedy
Very nice
Anthuwa luso alinalo timamva nawo kukoma komano ndi zomvesa chisoni kuti alibe sponsor,tipemphele kumwamba kuwapase sponsorship yabwino,tonde umatha ndi nzako gaga keep it up mr thembwelembwe😂😂😂mr kalanka zikutheka watching from durban
Wow anthu awa ali ndi luso ofunika a Malawi tiwapange support
NICE ONE
Ok lero ndaziwa ndithu❤❤❤
Tonde wadula ndi mbambande. Kma camera sinalibwino ayi apapa pojambura
Tonde ❤ keep up the good work 🎉
Atone osadanda mumakwana inuyo zanu zikhala pa bho
Tonde umaitha keep on
Guyz mumatha
Zoonadi zinafunika kutengapo mbali Amalawi tatengani mbali chonde
Kwambiri,tiathandize awa,Nkhalongo multimedia
Mumatha
Gaga kma mabodza iwe😂😂
Kkkk atonde mwachande mwasiya kt😂😂😂😂😂😂
Amandisangalasa kwambiri anyamatawa
Komano a Chibiliti mpaseni kaye ka 2pin Gagoyo kkkkkk
Tonde umatha ase
Chibiriti kutafuna chimanga kkkkk
Zoonaditu luso athu ari nalo koma amasowa kuti lituluka bwanj,timakunyadirani
Tonde kawawa