ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Je suis congolais République démocratique du Congo j'adore cette chansons
amen kuyimba kwa bwino muli uthenga wamphamvu ambuye azikudalidzani pitilizani
Ayi atsikana mukuimba bwino makamaka oyambitsayo alindimau abwino keep it up
Odala amene akudziwa Kut tili mmasiku ongowonjezela. Amen
Mlungu atamandike chifukwa Choti pulumusa mu uchimo amen 👏
Mulungu adzakupeza ukuchita chiyani nzanga tisakopeke ndizadzikolapasi zilimbemoyo mulungu atisamalile amen
Je suis de la c'est musique, elle chanteBien RDC j'adore
Nyimbo iyi ikundisuntha kwambiri ,munaimba bwino opanda zozionjezera muli mu natural mavalidwe abwino
Amen mwaulemu anu pitilizani kutilimbikitsa
Nyimbo iyi ikundisuntha kwabasi!!! Big up to Mpachika LMC🥰
Amen, nice song end mavalidwe ali bwino zedi ,,, tili mu nthawi yoonjezera tikueneradi kuchitapo kanthu ,, amen
Good vocals and meaningfull songs. Keep it up anyamata. Koma asakunyengeni satana, dziwani kuti ndinu nyali yoyikidwa pamwamba kuunikira onse
Zoonadi asanyengereredwe
Am blessed amen
Amen and Amen powerful massage ❤❤❤
Amen tilidi munthawi yowonjezera..
alemekeze ambuye
Jesus need us to found in church all the time.
Really powerful song Amen n Amen
Mulungu adzikudalitsani apitilize kupeleka lunso pa inu nonse :^) Ed Moçambique
Powerful massage 🙌🙌🙌🙌
Great message ❤❤❤
Aman ndikuva kukoma
Yes wabale wanga
Choir imeneyi imandisisimutsa hvy
Amen nyimbo yachilimbikiso
Amen Amen
Ndipo ndizoona masiku oonjezera ofunika kukozeka
Mulungu adzingolemekezeka mudayimba bwino kwambili komanso kuvina kwabwino
This is more than great
Powerful message
Nyimbo iyi imandililitsa ndikaganiza zomwe zikuchitika zdiko lapsi
nice one
Beautiful song
Amen
Kuyipasa moto
Pano tili pathawi yoonjela emen
Mulungu adzikudalitsani mwatidalitsa kwambiri
God Bless u
Amen 🙏🙏🙏
❤❤❤amen
Where is our mumtendere main vocalist pliz?...nice one
Kayadi alikuti mwina anafooka
@@innocentbvutani6238 alipo munyimbo inanso ndamuona
@@innocentbvutani6238 ❤
Even me I miss that Muntendere Wamuyaya vocalist, that was really great vocal❤❤❤❤❤ but it's really nice too
@@Mpungwe123 Title yanyimbo imeneyi ukuti chani ndiisake?
Amém ❤❤❤
Mpachika
Nice
Amém
They are coming to launch these songs here in Lilongwe from Blantyre end of this month of April.
Are these guys from BT?
@@PaulChide-ds9hqshare program for launch and other details
@@davidyafeti3391 yah from Bt
Amen ❤
Amen 🙏
Je suis congolais République démocratique du Congo j'adore cette chansons
amen kuyimba kwa bwino muli uthenga wamphamvu ambuye azikudalidzani pitilizani
Ayi atsikana mukuimba bwino makamaka oyambitsayo alindimau abwino keep it up
Odala amene akudziwa Kut tili mmasiku ongowonjezela. Amen
Mlungu atamandike chifukwa Choti pulumusa mu uchimo amen 👏
Mulungu adzakupeza ukuchita chiyani nzanga tisakopeke ndizadzikolapasi zilimbemoyo mulungu atisamalile amen
Je suis de la c'est musique, elle chante
Bien
RDC j'adore
Nyimbo iyi ikundisuntha kwambiri ,munaimba bwino opanda zozionjezera muli mu natural mavalidwe abwino
Amen mwaulemu anu pitilizani kutilimbikitsa
Nyimbo iyi ikundisuntha kwabasi!!! Big up to Mpachika LMC
🥰