ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Watching from South Africa Cape town but from Mzuzu you guy's you are the best regards for the Malawian keep it up
Waching from AS apington gayz tamayipaseni moto mwina mkusiya zonyamula ma frasiki popita kuzipatala zathu chilichose tizikachipeza konko❤😊
Watching from Lebanon please mikuluwiko muchepese point of corrections kuba kwambili and kulembana ntchito pachibale
Michael usi sangapereke K20,000,000 😂 akuziwa kt sangawine.
watching from Tokai Cape Town. Akanakhala wina wanzeru akanangotura pansi udindo. cos ananena kaye. Kodi zinthu ankanena kut akazalephera azapanga resign ndi ziti??foolish leadership
Mlandu wa amayi agamulidwa 53 years ndi mmene nkhani yawo idayendera pa imfa ya amuna awo sukusiyana ndi mmene zinayendera pa infa ya chilima ndi ena 8 kotero ngati mtero achakwera ndi boma lawo adapha chilima ndi ena onse mlandu uli 50-50 .
Bwana steve palibe zobwela limozi ayi. Achoke bomamo DPP ilowe
Onse amene analumbira koma kusemphana ndi chilungamo Obviously samaopa mulungu
Akupangila mademo ifetu amalawi tikuvutika kwambili dzithu dzikungo kwela every day ayi chakwela walephela akukanililanji walephela kale akufuna tipitilidze kuvutika ayi dzikolitu ndilatose Kapumeni man
Kkkkkk kkkk chikangawa chakwera koma zooona wayonda malawi ukona koma
Chakwelaso 100 years yakupha chilima 2026 adzanyamanyi Kumaula koko nayeso ndiwakupha monyatsa kwambili
Watching Mibawa TV, from Balaka
Kuvomeleza kukuwavuta chosecho akudziwandithu kuti alephera
Steve usanene kut azipani zosusa amabwe pamoz ndi boma athandizane nkhani yamafuta. Iwowa a MCP anachosa DPP m'boma kusonyeza kut amalephera kubwelesa mafuta mdziko koma iwowo ndi amene angathe lero aba ndalama kumafutako ndiye mukufuna a DPP olephela aja abwele akonze zimenezi?? Mbuzi iz zalephela kulamulira dziko atule pansi udindo
Munthu uyu Mulungu azimuteteza kwambir Namiwa
Iyi yekha ndaseka kkkkkkk
Koma anyamata inu mmasangalasa boma lilibedi solution
Akutapa pa mulandu oti akukuganizira kuti umaganizira upo ofuna kuliseka boma.
Fuel it's pangolin now in malawi with poor governing of government of malawi mbuzi chakwera
Nde kusadakatu kut khalani 5-5 ndekiti anthuwa ndi buzi zeni zeni
Timakukondani mumatiimilila
Pano zithu ziknukha ngati kutoilet
😂😂😂
Watching from South Africa Cape town but from Mzuzu you guy's you are the best regards for the Malawian keep it up
Waching from AS apington gayz tamayipaseni moto mwina mkusiya zonyamula ma frasiki popita kuzipatala zathu chilichose tizikachipeza konko❤😊
Watching from Lebanon please mikuluwiko muchepese point of corrections kuba kwambili and kulembana ntchito pachibale
Michael usi sangapereke K20,000,000 😂 akuziwa kt sangawine.
watching from Tokai Cape Town. Akanakhala wina wanzeru akanangotura pansi udindo. cos ananena kaye. Kodi zinthu ankanena kut akazalephera azapanga resign ndi ziti??
foolish leadership
Mlandu wa amayi agamulidwa 53 years ndi mmene nkhani yawo idayendera pa imfa ya amuna awo sukusiyana ndi mmene zinayendera pa infa ya chilima ndi ena 8 kotero ngati mtero achakwera ndi boma lawo adapha chilima ndi ena onse mlandu uli 50-50 .
Bwana steve palibe zobwela limozi ayi.
Achoke bomamo DPP ilowe