Dzina lanu ndi Yehova ochiza nthenda zanga,ositha nyengo,ochitira chifundo ndi yekhayo akayakhula Mau zimachitika mwa kufuna kwake osati mwakufuna Kwa munthui,amenei ndie yesu palibe ofanana nae....Ali ndi njira zambiri zogonjetsera Amen!!! Amen!!! Maso patsogolo
Dzina lanu ndi Yehova ochiza nthenda zanga,ositha nyengo,ochitira chifundo ndi yekhayo akayakhula Mau zimachitika mwa kufuna kwake osati mwakufuna Kwa munthui,amenei ndie yesu palibe ofanana nae....Ali ndi njira zambiri zogonjetsera
Amen!!! Amen!!! Maso patsogolo
Every time I am listening to your songs am blessed amama God bless you and your family
Mulungu azikudalitsani ❤
Ambuye andikhuze pa matenda anga mamawa omwewuno
The bass guitarist is prfect.
❤😅😅 love you mama
I like 🔥
🎉
Koma amayi mumandidalitsa