Rev. Alexander Kambiri preaching at Soche Anglican Church- Blantyre

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ก.พ. 2025
  • it was a revival meeting

ความคิดเห็น • 17

  • @CharityKachigamba
    @CharityKachigamba 6 หลายเดือนก่อน

    Ambuye akudalitseni pastor akusowa olalikira molamitsa kuti titembenuke mtima amen

  • @CatherineMdewa
    @CatherineMdewa 8 หลายเดือนก่อน

    Nthawi zonse ndimadalitsika ndikuphunzila zambiri kuchokela muuthenga wanu... Ambuye apitilize kukudalitsan ndikukuvumbulutsilani zochuluka kuti tiziyendabe ndi yesu nthawi zonse Amen

  • @JamesMajekete
    @JamesMajekete หลายเดือนก่อน

    Mmakwana abusa mulungu akudalitsen

  • @patriciamsopole8957
    @patriciamsopole8957 8 หลายเดือนก่อน

    Hallelujah

  • @phillipnavaya7398
    @phillipnavaya7398 ปีที่แล้ว

    So powerful

  • @quespeykatame2595
    @quespeykatame2595 ปีที่แล้ว

    Amen 🙏

  • @patriciamsopole8957
    @patriciamsopole8957 ปีที่แล้ว

    HALLELUJAH

  • @gracemwandumba7816
    @gracemwandumba7816 9 หลายเดือนก่อน

    Amen...

  • @molefiwakhiti8886
    @molefiwakhiti8886 2 ปีที่แล้ว

    Glory be to God..

  • @yusufelliotanalidodoloooma9685
    @yusufelliotanalidodoloooma9685 2 ปีที่แล้ว +2

    Komatu munthuyu akuyenda kwabasi. Everywhere around the world??? Ayiii mulungu amukonda munthu yu kwabasi. Ndine mslam koma mkuluyu ndimamusatira mkuluyu kwabasi. Amandisangalasa kwabasi. Mukayankhulidwe kake zanyengerera ayiiii. Chilungamo chiyende ngati madzi

    • @CatherineMdewa
      @CatherineMdewa 8 หลายเดือนก่อน

      Masiku otsiriza awa akatiuza motinyengerela tionongeka... Wakumva amve osavayo zake...

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 2 ปีที่แล้ว

    Amen amen

  • @christinambewe9354
    @christinambewe9354 2 ปีที่แล้ว

    Amen

  • @VictorSaka-xg7ho
    @VictorSaka-xg7ho 3 หลายเดือนก่อน

    Azibusa ena salalikila ma church ena akakhala wa c.c.a.p km uyuyu uyu ndi mtumiki wamulungudi sasankha owalalikila kut azilalikila achurch chake okha ai wandilimbikitsa kwambili

  • @tiyamikesamson7802
    @tiyamikesamson7802 ปีที่แล้ว

    Amen

  • @SalomesarahPofera
    @SalomesarahPofera ปีที่แล้ว

    Amen

  • @SalomesarahPofera
    @SalomesarahPofera 4 หลายเดือนก่อน

    Amen.