Wasn't expecting this movie to be this good.. ndulule kuti ndimaithawathawa coz tima movie tachuluka pampanje pano timakhala topanda mutu ..koma this one ase , take a credit for this movie,, nice storyline, excellent acting, .. I didn't like it, I LOVED IT! 🔥
ku Malawi tayamba kupanga zakupsya,my country pipo keep it up.....makolo mukasowa ndalama musamati mumgulise mwana ayi izi n nkhaza ngat alipobe makolo amene amapanga chikhalidwe ichichi mmh akanasintha....i must congratulate Dami astrong man fighting for what you love if out of 100 men 99 mkukhalangati dami bwezitu kuli mabanja abwino kunja kuno....komaso azimayi the fact that aman is the head sizikutanthauza kt mumpeleke mmanja mwa chilombo munthu opanda respect ngat ngati adobe pena kumakana,,as awoman we need to fight for our children at any cost even if t means loosing what u love most
Ladies and gentlemen this is absolutely beautiful and nice. I can expect this to be a malawian movie. I have been reactant to watch it but now I don't regret watching it
Mwa ma film omwe takhala kltikuonela ku malawa kuno.iyiyi ndi ndi school days komaso magwilagwila ndi mafilim omwe angatiike pa map ngat dziko.ndipo kwa ine ndikuiika pa 1 mwa maflm anzeru,otyakuka komaso ophunzitsa.i hope pokhala munthu omasulila ma film umaphunzila kachitidwe ka anzathu nkutibwdretseraso zabwino.Romeo and juliet wathu ndi KHASU.we all love you Akila.pangatalike mudzabooleza n mulungu adzikuladalitsani boss.
When rorah went to grave kukasiya khasi i got emmotional mmmm mpaka nayamba nawo kulila.. infact iyi yabwra kuzakhala it can be better if titamapeza mwayi wambiri opanga act ma acctors tikadalipo koma mwayi umasowa lets pray for Malawi kupeza mwai otukuka with acting. Really thanks to you Akila continue 🎉 grt job
Am still repeating since first day until now ❤❤❤iyiyi ndiye wayiswa, Each time I need to finish my day, ndiwonele kaye pang'ono Thanks to all guys, Crue yonse
Iyi nde movie nice work guys never thought that malawians can make movie like this one well done thou u need to polish some parts but so far complete awesome the definition of a best this is
Film iyi munali ndi concept yabwino ndipo ndiimodzi mwa ma film amene anayenera kutenga ma award mchaka chino koma maganizo anga ndikuona kuti mwaifulumira muli zinthu zingapo zomwe mukanakhala munazikoza zikanapangitsa kukhala yapamwamba. Ikanali immature mmaenera kudekha nawo ndikozekera bwino lomwe zinthu zomwe zikanakhala zofunika kutengera ndi scene yomwe mukupangayo. Ma actors alibho although some parts amaonetsa lack of seriousness koma mamuna wake ma Lolla ndi actor wabho
Ayiii zikomo kwambili ulemu ukhale kwama actors nonse ni ma actress kunena chilungamo khasu yabeba kwambili zed kumalawi kumakhala ma movie koma naiyiyi ili pa top kwambili congratulations guys 🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤koma mathedwe okhawo ine misozi yokha yokha 😢😢
Eeeee ndalira like tomnkalilira tikamaonera My Love ya Ramsey kale😢, apa pokha Amalawi we can clap for ourselves.. anyamata you have done a good job... Nice movie❤ ❤
Big up Akila,, despite being disabled but you always work hard to make both ends meet,,,,nice film,, everyone took his/her part seriously,,,zikhalidwe Zina mzoyenera kuzitaya coz dziko likusintha ili,,,,,I wish mwana wa Lora akanabwa mnyamata and named after his father,,,big up boys and girls,,ladies and gentlemen
Dickson Mandola my classmate at Lunzu Secondary school. I never thought you qre do talented like this. You started from the humble beginning koma with Akira booom🎉🎉 this is amazing. Tears came out ofmy eyes. Guys firm iyiyi mwakhiya. I wish you the bes6of luck guys.
This movie i must say is number one Akira you have done well with your team, i can't control the tears at the end....... once again keep it up so proud of you 💪💪💪❤❤
Movie koma iyi yophunzisa yosangalasa kwambir....never give up Mr Akila ndima organizer ose omwe atengapo mbali pa chinthu chimenech kutichitheke big. Koma ndimafuna part 1 sindinaonere please
Esshhh! Wandisiya opanda mawu aise eshhh Akira your the best ever palibe amene angapikisane nawe pankhani ya ma film kuno ku Malai 😢😢😢😢 kundisiya ndikulira aise 😂😂😂😂
Wasn't expecting this movie to be this good.. ndulule kuti ndimaithawathawa coz tima movie tachuluka pampanje pano timakhala topanda mutu ..koma this one ase , take a credit for this movie,, nice storyline, excellent acting, ..
I didn't like it, I LOVED IT! 🔥
One of the best movies of African Origin I have watched this year. Keep it up Akila. I love this. Koma Dami samayenera kufa abale 😢
ku Malawi tayamba kupanga zakupsya,my country pipo keep it up.....makolo mukasowa ndalama musamati mumgulise mwana ayi izi n nkhaza ngat alipobe makolo amene amapanga chikhalidwe ichichi mmh akanasintha....i must congratulate Dami astrong man fighting for what you love if out of 100 men 99 mkukhalangati dami bwezitu kuli mabanja abwino kunja kuno....komaso azimayi the fact that aman is the head sizikutanthauza kt mumpeleke mmanja mwa chilombo munthu opanda respect ngat ngati adobe pena kumakana,,as awoman we need to fight for our children at any cost even if t means loosing what u love most
Ladies and gentlemen this is absolutely beautiful and nice. I can expect this to be a malawian movie. I have been reactant to watch it but now I don't regret watching it
It’s a movie that deserves likes and support muli phuzilo larikulu kwa both achinyamata and makolo some decisions can lead to non reversing results
This is very brilliant,sindimayembekeza tuona luso limenel fire 🔥🔥🔥.am here waiting another move
What a great movie .....mpaka ndalira😭 ....keep it up
Akila unabwera kudzabebesa zinthu eish.zoonad mavuto anasitha miyoyo yamakolo ambiri mkukhala chiphinjo pa ana awo kamba ka zofuna zawo,TIKAMAONERA MA FILIMUWA TIZIPHUNZIRAPO KATHU❤❤❤Movie yokhunza iyi,kutsangalatsa komanso kuphunzitsa phwiiiiiiiii❤❤❤AKILA❤❤❤❤❤
Mwa ma film omwe takhala kltikuonela ku malawa kuno.iyiyi ndi ndi school days komaso magwilagwila ndi mafilim omwe angatiike pa map ngat dziko.ndipo kwa ine ndikuiika pa 1 mwa maflm anzeru,otyakuka komaso ophunzitsa.i hope pokhala munthu omasulila ma film umaphunzila kachitidwe ka anzathu nkutibwdretseraso zabwino.Romeo and juliet wathu ndi KHASU.we all love you Akila.pangatalike mudzabooleza n mulungu adzikuladalitsani boss.
this movie is well composed koma why Dami uja wafa eish pokhapo mtima wapweteka bwanji anyway keep the fire burning Akila 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Pamenepo mmmm not good. Because of khasu eeish
The only thing I lyk on this film is that Akila put alot of effort tikaona ndi ulumali wawo ❤❤big up my bro🎉
That's very nice Malawian let's work hard osati tizingoonela Nigerian movie let's promote zathu keep it up guys l enjoyed your movie
When rorah went to grave kukasiya khasi i got emmotional mmmm mpaka nayamba nawo kulila.. infact iyi yabwra kuzakhala it can be better if titamapeza mwayi wambiri opanga act ma acctors tikadalipo koma mwayi umasowa lets pray for Malawi kupeza mwai otukuka with acting. Really thanks to you Akila continue 🎉 grt job
Tonse amene tamaliza kuonera kuyambira part 1 mpaka 2 let's gather here lero pa 3 October
Dami samayenera kufa😢
Ndili part 2
Eya zoona zamayenera
Ine ndamalidza kumene kuonera part 2
Am still repeating since first day until now ❤❤❤iyiyi ndiye wayiswa,
Each time I need to finish my day, ndiwonele kaye pang'ono
Thanks to all guys,
Crue yonse
Number 1 movie in Malawi so far, komanso Dami samayenera kufa aaahhhh.... congratulations Akira entertainment!!!!!
Wow finally she's having damis preg anachitaso kukadzipereka pat❤
Ending yokhayo ndalephera kupanga control misonzi yanga😢 nice film akila
ending ya chabe
Ngakhale ine mmmm
Sory
Nanesoh mmmmh ndakanika kupilirah ndalira ndithuuu😭😭 Damiih
Ngati ine ndingolila 😢😢so emotional
Wow that's awesome...ndipo yandikhudza eti eishhh
Congratulations to A Killa ....landilani maluwa anu mukanali moyo man💐❤
I think a malawi tayamba kubwera ngat coming...congrats to akila n the crew ❤
Iyi nde movie nice work guys never thought that malawians can make movie like this one well done thou u need to polish some parts but so far complete awesome the definition of a best this is
Work done
No need to polish up its already polished
Serious Mani film iyi ayikwapula
Film iyi munali ndi concept yabwino ndipo ndiimodzi mwa ma film amene anayenera kutenga ma award mchaka chino koma maganizo anga ndikuona kuti mwaifulumira muli zinthu zingapo zomwe mukanakhala munazikoza zikanapangitsa kukhala yapamwamba.
Ikanali immature mmaenera kudekha nawo ndikozekera bwino lomwe zinthu zomwe zikanakhala zofunika kutengera ndi scene yomwe mukupangayo. Ma actors alibho although some parts amaonetsa lack of seriousness koma mamuna wake ma Lolla ndi actor wabho
This is what is needed in the industry.....it just needs good promo ....l love this
Tonse amene tikuonela pa 2 October 2024 tikumane pano 🥰movie ilibho heavy🥳
Ndaikonda
Ndipo suli wekha
Mpaka ndagwetsa msozi😢😢😢
Nice work by the way❤❤
tonse amene talira chifukwa cha dami atilipire😅😅 akila umatha💯
Ndipo atilipire zochuluka movie ili bho iyi❤
eeeiish 😭 ngat mpopi mmm yakhetseka misonzi
Mbambande
Ine pano
Ndipo. Ine nsomzi mpaka
Keep it up Akila,this is a good lesson.
Ma move achimalawi sindinagwetsepo mtsozi kma iyi yokha mbambande❤❤
Ndakumbukila ex wanga 😭😭😭 may his soul continue rest in peace
Inenso mpaka ndagwetsa misozi 😢
Ndipo inu
Ndipo straight abaleee same applies here mmmmmm
Though ndi movie but eshieeee💥💥 naneso ndalirah
Dame adali olimbikila mpake anthu 😢
Ayiii zikomo kwambili ulemu ukhale kwama actors nonse ni ma actress kunena chilungamo khasu yabeba kwambili zed kumalawi kumakhala ma movie koma naiyiyi ili pa top kwambili congratulations guys 🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤koma mathedwe okhawo ine misozi yokha yokha 😢😢
Yandikhuza film yanu bwana Akira... So sensitive, lessons and many more
100% movie... Keep it up Akira. Ndagwetsa mnsozi.
Xul mphatso kufa, khasu dami naye wafa.
Zosakhala bwino.
Bolabe dami wapita atasiya mimba koma sa mphatso machira opoila kwambir. ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️ nice film eeeee part 2 mmm
kulibe movie Ku Malawi kuno yaliza anthu ngat iyi.......
nice movie akikaa
you number 1
Kod tilipo gulu eti😂. Movie aika iyi
Watching from central Zambia this is a good movie and so educative
Kunena zoona film mwamenya iyi❤ keep it up
Your fan from nigeria i really like it ngakhare sindikuva chiyakhuro chanuchi all the way from 🇳🇬 🇳🇬 big up
Kkkk ndiye wachilemba bwanj
Aaaaaaa 😂
Kkkkkkk umakwana
❤❤❤😂😂😂 Ndizomwe ndikudwabwazi ine
😅😅😅ndie mwalemba bwanji chichewa
🇲🇼This is a must-watch!
Akila ndimayesa luso lawo ndi kumasulira mafilimu kokha koma ayi ndithu movie ili bwno kwambiri zedi 😊😢
❤❤❤❤❤ setting and Location matches with the idea behind the story....
Number 1 zikuchita kukhala ngati live Akumudzi mwaphaa imeneyi Ambili alira nayo
one of best movie in malawi. Akilla apapa mwaigwira ntchito everything its perfect big up!!!!
Walira ngati ine ndani mkazi uja atafika kwawo kusiya katundu kupita kukafufuza Damie eish come gather here fam movie ili super
Eeeee ndalira like tomnkalilira tikamaonera My Love ya Ramsey kale😢, apa pokha Amalawi we can clap for ourselves.. anyamata you have done a good job... Nice movie❤ ❤
Ine mpaka kulira ..nice movie
Got emotional while watching this movie😢😢Dam kungogwira ya kalavulagaga ,,ai bwino koma,mpaka ndalira🥹🥹🥹😭
Adobe wakuba khasu 8pn koma mpaka akuti yafika 500pn 😮😮😮😮
Balance ya 250 ndikuzatengela nkazi wa Million mbanva yolusa kkkk
🤣🤣 Nchakubadi
@@mussahdickson3538 🤣🤣🤣🤣
This movie teaches Us something, Akila Ntchito mwayigwira and Ku Malawi kufunika ma filimu Abwino Ngati awa... Much love from USA.
Damison best actor in this movie anaikirapo mtima,big up akira with your entire team move iyi mwaswaaa shuwa... congratulations guys🎉
Ndip ndaphunzila chinachake mu filim iyi eeeesh zabwino kumayamikila gys
well done guys to all of them .watching from Cape town
Man damison aja eee anaikirapo mtima size kukana
🔥🔥 ndye muli chidakwa chong'alula ma fact
Wow that's anice movie from the warm heart of Africa
Akila ena ajanso mudzingoponya pa TH-cam pa
Movie yokoma heavy koma dami watililitsa heavy mumakwana guys we learn alot of things through this film big up❤
This movie is something else... mpaka ndalira ine....big up mr Akila❤
Nice one guys and thumbs up to you.. waiting for part three..I enjoyed the movie all the way from 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Nice film kuposa xool day
Kumapeto kwake zoveza chison eish, !!! DAN wapita Nice movie,,,....Congratulations you guyz
This movie is giving me impressive makolo adyela komanu akila umaitha keep it up good job
Big up Akila,, despite being disabled but you always work hard to make both ends meet,,,,nice film,, everyone took his/her part seriously,,,zikhalidwe Zina mzoyenera kuzitaya coz dziko likusintha ili,,,,,I wish mwana wa Lora akanabwa mnyamata and named after his father,,,big up boys and girls,,ladies and gentlemen
Dickson Mandola my classmate at Lunzu Secondary school. I never thought you qre do talented like this. You started from the humble beginning koma with Akira booom🎉🎉 this is amazing.
Tears came out ofmy eyes. Guys firm iyiyi mwakhiya.
I wish you the bes6of luck guys.
This story touched me a lot. Congratulations Malawi, here is Mozambique 🇲🇿
Eeee the greatest movie, aaaa ma ulemu anthu munafasa, ma phudzilo nde ndiosayamba ndithu, congratulations to them pa ntchito yabwino mwagwira. 🎉🎉🎉🎉🎉
This movie i must say is number one Akira you have done well with your team, i can't control the tears at the end....... once again keep it up so proud of you 💪💪💪❤❤
I was not expect that this movie can be so nice like this
Big up guys💯💯☑️
koma Dami samayenera kufa yi😏
Movie koma iyi yophunzisa yosangalasa kwambir....never give up Mr Akila ndima organizer ose omwe atengapo mbali pa chinthu chimenech kutichitheke big.
Koma ndimafuna part 1 sindinaonere please
Vividy speaking, this is nice movie and I almost cry. Keep it up.
Nice movie big up to u akila u deserve much respect what a sad ending
Akila apa ndiye mwaitha. We are expecting more from you. Big up man.
Ohhh wow!! what an emotional movie, with brilliant actors👌💯
Mmmmmmm God continue bless you Akila
Film iyi muli uthenga wabwino
Movie yabho kwambiri komanso yopereka phunziro.. Congratulations guys wherever you are!
It’s a movie that deserves likes and support muli phuzilo larikulu kwa both achinyamata and makolo some decisions can lead to non reversing results ….
Excepting more from you guys congrants
To the extent that a fan from Nigeria appreciate this talent. So who I'm I not to salute this talent. Akila you deserve an award again this year.
Well done Akilla,you are the best brother,it's a nice movie...kumapetoko tikanalira nao maliro a dam ....all the best brother man
So nice ndaphunzilapo waiting for part 3
WOW nice movie i like it and we need part 3
this film is not just move but attractive and educative 🥰🥰🥰🥰🥰🥰 i like it
So attaching at the end 😢 this very nice guys
This movie is astounding 🔥💫🌠
A very good one for a starter,mupitilize munthu wamkulu.
It's a WOW for me 🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Well done big up MALAWI
Indeed it's more educative movie, keep it up guys
Wow 🥰🥰 movie iyiyokha ndagwanayo mchikondi,ndiyopatsa phunziro komaso kusangalatsa
Dami wandivetsa chisoni ndisaname, koma muli phuziro❤🎉🎉!
Esshhh! Wandisiya opanda mawu aise eshhh Akira your the best ever palibe amene angapikisane nawe pankhani ya ma film kuno ku Malai 😢😢😢😢 kundisiya ndikulira aise 😂😂😂😂
School days Sha!!!! 😢 Down this is number 1
❤❤❤ Koma iyiyi iyii kutchaya kugwetsaadi eeeee well planned and organized. Well done to all participants.
Malawi❤❤❤❤ nice movie❤
Nice and we need more 🎉
That's awesome ndakufilan
This is very great guys lets push up as Malawi,
What a wonderful movie ❤
That's nice movie let me finish and I will come with another comment
Can't wait to watch part 3
Ndi angt akulir😢😢 mu nthawi ino chifukwa ifa ya dam,best movie 🎬
Respect guys mmmm this is another level
Very impressive 🔥 movie, continue to give us the best 🔥, Mandota Dickson 🔥
Congratulation that movie eeee is best
This is amazing eish I like it keep the 🔥 burning❤
Job done well. Fanta marvellous
Excellent Akila.