Iwe ka (Y) unafa kale nawenso monga Pali infa zina umavomereza kuti yaaa mulungu wamukondadi munthu kufa kwa chilima grace chinga plus ngozi izizi 10 patsiku iwe basi mvwiiii😬
We put ourselves in this situation, n we can help ourselves by voting this government out, there is nothing good about this government from the time of Dr Banda, voting them out will help
Kunena zoona chiripo chiripo ngozi imeneyi ndiyodabwitsa ngozi ya moto imatelo kuno ku south Africa Tacoma ngozi koma iyi, chabwino mulungu ndiye akudziwa zonse
Ndiye Malo moti Muziuza a Malawi kuti all the National tikhale pamodzi tisale kudya ndi kupemphelela Malawi mukulimbana ndi Munthu olengedwa ndi Mulungu kwinaku ndi kusauka ndi ma jelasi basi...
A Malawi ndale za umbuli siyani mungobweretsa matemberero mdziko. Ngozi ndi ngozi osamapaka munthu osalakwa koma dziwani kuti Mulungu aliko ndipo amumenyera nkhondo Chakwera. God is going to prepare a table for him in the presence of his enemies. Ngati Chakwera ndi mfiti inunso ndi mfiti chifukwa mwaona kuti ndi amene akupangitsa ngozi. Umbuli umenewo sukuikani pampando
Ngozi sumakozekera let God be a God koma tikamalimbana ndima jadgement anthu apasi pano palibe chomwe chingachitike coz mukungoganizira kut atha kukhala wakut wakut koma choona chen chen chichokera kwa mulungu ngakhale atasogoza wina kumanda koma iye azapitaso komweko
Shame on you like u don't know bushiri agenda guy take him out if south Africa government still need him so this is dangerous to have kind of person like bushiri in Malawi
At point of view guys let's think wise be afraid with the almighty God and I don't think you ave a normal sprits in your heart coz this not true and osamazikonda zokamba ixi kumaikamo anthu osalakwa
Ine ndi akunyumba kwanga timamukonda chakwera inuyo zitsirunu muzisapota zinazo do u think ma proganda anuwo sitiwaziwa? Do u think that we are all savage's? Siife mabulutu agalu inu mwamva muuzane ndi galu wako akumapanga pretend ngati wakumpotoyo kuti ndinu ma idiots
Ambuye tithandizeni ndinu Nokha wamphamvu Pali Ena akufa imfa zowawa tichotsereni satana ngozi za daily ndi ngozi za mtundu wanji ambuye tikulilila kwa inu
Ndipo guys nkhani izii sizaboza koma ndizoona chakwela atitha ndizake bushiri😢bingu amamukana uyu asakhare Ku Malawi kuno mukaona ngati akudana naye lero ndizii titha bas😢😢😢😢
@@DigleDafter kkkkkk anthu opanda chiyembekezo inu, ana a njoka, inuyo musanabadwe munape za mau akut mudzafa ndye mutsutsana ndi mau a mulungu
Ndipo ndiwe chisiru ukungotaya nthawi yako
Iwe ka (Y) unafa kale nawenso monga Pali infa zina umavomereza kuti yaaa mulungu wamukondadi munthu kufa kwa chilima grace chinga plus ngozi izizi 10 patsiku iwe basi mvwiiii😬
Inuyo ndi amene simudziwa kulankhula chilungamo @@yowasschitsosa5348.
Ndani asamadziwa kuti imfa ilipo ndipo kuli asataniki amene akupha through ngozi,matenda...
iwe bushiri zikumukhudza bwanji tamalimbana ndi chikangawa wakoyo osaphatikizap bushiri wava
Bushiri ndi chakwera ndi anthu oipa atitha ife kuno pano ngozi zinatha atangochoka bushiri kumalawi kwaonjeza kwambiri
Umbuli ndi chinthu choipa kwambili
Tisamakonde kulandila zaulele tiziluza nazo miyoyo
Komaso chipongwe chanji chopanga abale anu omwe anthu akuphedwawo ndi anthu oti anali odalilika mamanja mwawo😢 ndiye inu akumidima mukufuna kumaliza anthu kodi muzikhala ndi mu dziko la umphawi ngati limeneli komaso omwe mukulandila thandizo la Bushili musakondwele kwambili chikuza mawa simukuchiziwa
Anthuwa ndiziwanda ndithu😢😢
It makes sense this is not normal. Our heavenly father please protect and guide your people from evil
Koma ku Malawi 🙌🙌🙌🙌
We put ourselves in this situation, n we can help ourselves by voting this government out, there is nothing good about this government from the time of Dr Banda, voting them out will help
Kunena zoona chiripo chiripo ngozi imeneyi ndiyodabwitsa ngozi ya moto imatelo kuno ku south Africa Tacoma ngozi koma iyi, chabwino mulungu ndiye akudziwa zonse
Mzimu wawumphawi umapangitsa kulimba ndiamene yehova anawadalitsa ukulankhula zonyela zenizeni tamagwilani ntchito kwinako kumapemphela mulungu amayankha
Kodi Bushiri zikumukhuza bwanji my fellow Malawians do not bring curse on yourself
So like you don't know bushiri this is life of bushiri don't take Malawi to be home of satanic every way people knows about bushiri be careful Malawi
Curse bushiri ayitenga Kati?
Umbuli ndi chonchitu
Remember we're u come from n u see y pipo r saying dat
Ambuye tilanditseni ana anu
Ndiye Malo moti Muziuza a Malawi kuti all the National tikhale pamodzi tisale kudya ndi kupemphelela Malawi mukulimbana ndi Munthu olengedwa ndi Mulungu kwinaku ndi kusauka ndi ma jelasi basi...
there is time to fast and pray, another time to stand and arise up and shine. this time is for action.
😭 Mulungu mlikuti tithandizeni
Uyu ndi satanadi atha anthu ameneyu
Adzibusa okhaokha akuti ma man of God akuti ,wina kuuthawa ku man of God nkuzajoina live dza dziko pamene a ,,,,😈😈
Koma anthu mmayankhulatu only God knows eeee. Ambuye atichitire chifundo.
Boza ilo,,,
Dpp vote
Allah akibr
Bushiri akanakhala Mzungu bwenzi zonsezo kulibe
Ngozi ijadi ndiyokayikitsa kuti singozi yachilengedwe komano Zoti apangotsa ndi bushiri ndi chakwera Sitingadziwe Koma Mulungu yekha.
Now I know chomwe Bingu samamufunira Bushiri 😢 of course onse the believe pansi pa nyanja koma anaziwa kuti Bushiri ndiolimba mtima heavy pa kupha
Mulungu atiyendele pazikolanthu ili l amalawi tizingokhalila kulila sikundisiku
Osamati bushiri koma chakwela bushido mikhanimusakupha athutu koma akungo landila nongovernmental zawo 😢😢
Ooho Allah only you can protect us
Komaso Atumbuka..... aaahh ndege aphedwa, munthu adwale waphedwa, achite ngozi waphedwa.
A Bushiri analakwa kukhala ochita bwino??
Anthu yonse tiyeni mawa chakwera achoke atule pasi udindo
🤗🤗🤗 ALIYESE PA MALO AKE 😅😅😅
A Malawi ndale za umbuli siyani mungobweretsa matemberero mdziko. Ngozi ndi ngozi osamapaka munthu osalakwa koma dziwani kuti Mulungu aliko ndipo amumenyera nkhondo Chakwera. God is going to prepare a table for him in the presence of his enemies. Ngati Chakwera ndi mfiti inunso ndi mfiti chifukwa mwaona kuti ndi amene akupangitsa ngozi. Umbuli umenewo sukuikani pampando
Fix Malawi guys everyone knows bushiri death is his hands so take care with our family'
Malawi tsopano tingodulilana malile ndi ncheu kumwerako zipanganizanu.
Zowona
Ndipake achakwela kuzamuthawisa bushiri Ku South Africa
Malawi bodza mwangodananaye muthuyi,mukatenge Obama alamulire Malawi tione ngati ngozi sizimachitika,mabodza basi!!!!!!!
Iwe sukuva pat awo ndima Lucifer bushili ni chingangawa
Amalawi tiyeni tipemphere kwA ambuye ndipo timulilire kosalekedza chifukw tonse titha ndithu mulungu wakumwamba tetedzani anthu anu onani tikupululuka sayana akutipha mopanda kumva chisoni
Anthu enanu musamankhale nditimaeu topusa kapena nditi osamankhala tiyanthu tamakan izi zikuchitikazi zikudzidzimutsa kwabili sikuti tikamati ifa iyi zikuyenda bwanji siku tikutanthawuza kuti modziwo ndikalerose munalibe ifa komano mukamafusana chochi zimankha kuti zawonjeza zinthu ndiye kaya enanu muli mugulu lomwelo ayi mudzanwera poyela atafa akumabanja akwanu kuti mudzave zomwe amalawi azanu akutanthauza kumwamba kuli mulungu akuva zosezi
Ndipo nzoona koma nthawi ikubwera apyanso ndi moto woposera pamenepo😢
Aliyese amaganiza choncho taxi kuyaka moto mmm sitikuvesa ndithu
Ndipo I can believe these cz moto unapha martse uja umandidabwitsa kwambli
Busy kumalankula za chakwera munkaona ngati malawiyi ndi wakwa muthalika anjani.. Tatopa nanu tsopano
Zowona moto wongofikila pakati mm no, singoZi. Ya galimoto iyi
Ngozi sumakozekera let God be a God koma tikamalimbana ndima jadgement anthu apasi pano palibe chomwe chingachitike coz mukungoganizira kut atha kukhala wakut wakut koma choona chen chen chichokera kwa mulungu ngakhale atasogoza wina kumanda koma iye azapitaso komweko
Shame on you like u don't know bushiri agenda guy take him out if south Africa government still need him so this is dangerous to have kind of person like bushiri in Malawi
Musakambe njhani yolemera nkhani apa ndiya Grace chinga basi
Inu inu ama page,,,muziwona kaye Topanga post osamangotithela Bundle ife zachamba ife ayi utiwapanga post chiyani apa
Usi sufuka popanda moto
No wonder Chakwera wakhala akumuchita protect kuti asabwelere ku South Africa kukayankha Milandu.
Chilungamo Bushiri ndi Chakwela mmmmmmm
Bwanj track sinayake bwanj koma minibus inagunda track why malawi, tsoka mtunda ndi nyanja pakuti oyipa watsikila ku malawi 👿👿👿☠
Pakufunika Bon kalindo ayitanitse national prayer dziko lonse tisare kudya
God is great, let us vote for DPP
Samalani malakhulidwe chifukwa oweluza ndi Mulungu
Nonse mubwebweta apa ndinu ana a dpp ngozi za galimoto zayamba lero? Amalawi nsanje ndimene idakula.. Choti mudziwe chakwera ndi mmalawinso. Ndinu zitsilu nonse mulankhu zopusazi.
Zoonadi kukhala ngati inatcheredwa Bomba opanda ophupha
Pakufunika kumupangira mademo achoke ku Malawiko
koma anthuni kaya mkufuna kutchuka kaya koma anthu aja enafe we know them n takula nawo plz msafalise zaboza
Ine chomwe kugwilizana nacho choti zoona kuno ku southafrica ngozi zapuma ndipo zoona
Mbuli imaloza zala munthu ikakanika, God bless bushiri
Mabatire ako ase
Iweyo ndi Bushiri wakoyo pamtumbo panu ndinu zitsiru nonse
Iweyo ndi mbushiliro Machende anu
God continue bless bushiri
Mukudziwana ndi iyeyo bt ine sindimamusapota aayi.
God knows 😢😢😢😢😢😢
This is true believe or not but it's true
Ngozi imeneyija ndiyodabwitsadi tisanamizane popsnda opulumuka mmin bus
Zoona zimenezoy
Ndichifukwa chake ku malawi mulungu alinako mkwiyo chifukwa anthu ake ndinu zisiru mumadziwa kupeka nkhani yamunthu yaboza, munthu akalemera ndi mfiti, chonde anyamata a DPP musiyeni Bushiri plz plz ndiyemweyu wakuthandizani kwanu kuja kutagwa cyclone fred, pamene amene mukuti ndiye wanuyo anangokhala, komaso kukhala ku south africa pompa pobwera pa truck apapa musaone ngati mwapambana guys kumeneko ndikupusa
Kaya kuweludza mkwamwini namalenga
Komatu munthui akunena zoona gyz bushili amaliza Malawi sure
My Malawi
Mulungu yekha atiombele mu zosamwitsa zimenezi 😢
Atraffic amavomeleza bwanj galimot mpaka anthu 26 ,kumangolandila 5000 bas zipitan ,apa zaphesa anthu ambir
Ineso ngozi imeneyi yandidabwutsa moto ungangoyamba olo oganiza zozimitsa motowo kuungofooka mmaganizo ada awa amandikayiikitsa kwambiri.
Ndipo inu, munthu amene anakhala mpando wapakhomo bwanji sanatsegule chitseko mmene moto unayamba? Mmmm zodabwitsadi eeish
Inu Pangani zandalezo Bushiri akulowa Pati apa
Kunja kuno kuribe chaurere munadya chimanga chamwini munkat ndi chaurere rero ndi izo muripira mwazi mmaro mwachimanga osamakonda zaurere amarawi
Like ifa ya matse kukanika kumupulumutsa anthu akuwona ayi zafika penapake
Zabodza zimenezi iweee tumbuka guy kutipusika yayi musiyeni chakwela amalawi vuto lanu ndi chani kodi
Ukavota na gogo ako dpp yo
Ndizoona sibodzatu ilili
Nkhani yaikulu bishiri zichimanga akumalandilitsazo tinanena kaletu ife
Zoonadi anthu oipa kwambiri bushiri ndi chakwera
Uyu akuti osaloza muthu chalayi osamudabwa ndiwasatanic guys
😂😂😂😂😂😂
Zoona
Stand for our right
Zilibe umboni maganizo anthu osapita kusukulu ndi amenewa
@@SebastiaoErnesto-mh6ec mbulidi
Ndizisiru kwa basi amafuna kuti bushiri akhare osauka
Ena akunena kuti ukupangitsa ngoz ndiweyo ukuyanjhurawe
Munthu oipa mdzimuonera maso ndi pankhope
At point of view guys let's think wise be afraid with the almighty God and I don't think you ave a normal sprits in your heart coz this not true and osamazikonda zokamba ixi kumaikamo anthu osalakwa
Muli ndi vuto akulu imunso ndinu a satanic mwadziwa bwanji zimenezi?
😂😂😂😂 koma kumalawi chakwera akupq andu e😢
Akutumani nkhalamba yanuyo ya chipani cha kubanjacho. Fokofo inja zachabe chabe mulibe nzelu mmutu mwanumo
Koma sembe😢😢
Zoonanadi abale anga kulibe galimoto yingapse chonchi kupanda wotulukapo m'mozi wopupumuka. Chakwera ndi bushiriyu atimaliza
bushiri ayi iwe pa thako Palo iwe
Usaveji uwu
Palibe chomwe Ukuziwa,,,undipeze
Komaso how possible anthu 15 ose kupsya 1 time opanda olo mmodzi otulukamo mu min bus
Mbuzi iwe
Tikamache azipita bushir
Koma tisaname amene amakonda chakwela ndi thakatii sizoona zomwe zochitika zijaa ndipo chakwela kungowina 2025 Malawi anukha ndipo kuzakhala khondó yosayambaa
Ine ndi akunyumba kwanga timamukonda chakwera inuyo zitsirunu muzisapota zinazo do u think ma proganda anuwo sitiwaziwa? Do u think that we are all savage's? Siife mabulutu agalu inu mwamva muuzane ndi galu wako akumapanga pretend ngati wakumpotoyo kuti ndinu ma idiots
Bushili tamutumizani Ku south Africa akayankhe milandu yake ili phyiii yakuba yakupha
Ulesi inu
Zitsilu za anthu izi
Chakwera ndi Bushiri ndi fiti
Zoonadi chakwera ni bushiri ni masataniki kwambiri ndipo atha anthu mwava
Opusa amalawi kwaamene analandila zakudya zake mudziwona sizinati kumulange anayamba kulandilisa zakudya .samalani anthu inu mukulandila zakudya
Onse guys akutsutsa guys osawadabwa ayi ndi ngulu la bushiri ndi chakwela asatanic onse akufuna atithe amalawi
Ambuye tithandizeni ndinu Nokha wamphamvu Pali Ena akufa imfa zowawa tichotsereni satana ngozi za daily ndi ngozi za mtundu wanji ambuye tikulilila kwa inu