Nde mwati apolice anapakula 5 million yomwe achilima ananyamula? Pa times pa yaka moto

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 17 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 8

  • @DouglasBizaliyeli-kb3qm
    @DouglasBizaliyeli-kb3qm 2 วันที่ผ่านมา +2

    Mwalankhula chilungamo simunarakwitse anthu ife umunthu ukutitaika pang'ono pang'ono koma mulungu atithandize ndithu

  • @HopefulCoralReef-tx4vx
    @HopefulCoralReef-tx4vx วันที่ผ่านมา

    Ulemu wanu big God bless you

  • @LucyJimmy-z6z
    @LucyJimmy-z6z 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kod chimwendo uja anamukaniza kukwera ndege ija pa reason yanji? Mmmmmmmmm tiunikepo apatu iyaaa😢😢😢

  • @MadaNyirendaMakanjila
    @MadaNyirendaMakanjila 2 วันที่ผ่านมา

    Kwathawi yoyamba mwayakhura zazelu 100/o

  • @OlakwaNdani
    @OlakwaNdani 2 วันที่ผ่านมา

    Amene adatenge ndalama nd ameneso adasowesa mfuti

  • @RuthTimothyChirwa
    @RuthTimothyChirwa วันที่ผ่านมา

    😢😢

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi a chipatala
    analipo pofufuza ndege

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 2 วันที่ผ่านมา

    Apolice wose kaya ndi asilikali wose anatumidwa ndi Chakwera kupanga zose awo