ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Mwandiyankhulila bwino kwambir mayi kaliat
Akwini is the best mama
Koma Mrs Kaliyati 100%perfect speech above all
Amanganya mpando wakomatu mwakhalira Moto akulu😢
😂😂😂😂 koma pilizi
Lets call Mai kariyatiwa MOTHER MALAWI. she is our last hope. ❤
Kuyankhula kwanzeru, my God bless you 🙏 ❤️
Alire bwanji Mai Kaliati
Opanda chifukwa munthu uyu
Inuso msiye bodza Kuti chakwera ndi owopa mulungu satanayo
Mayi kaliyati kuyankhula mau achilungamo akadakhala kuti mwezi wa June amauchotsa pa calendar ndithu tidakachotsa mwezi umenewu mwezi wa masautso taluza anthu ofunika kwambiri mau oliratu amenewo.
Wabwera Bo Kweni wanga
Dr. Michael Yudas Ussi vice president wagulisa chilima kwa zigawengaza mcp
Kwen akanagokhal president bas uyu Sali ngt Mai wanthu joice
❤ zikomo kwambiri poyankhula machilimbikitso
Mmmmm mwezi WA June wosaiwalika tataya anthu ofunikira ambiri
Mai uyuu salingatitu a Manganya Ayiii
Manganya ndi kape
Very wise woman ❤❤❤ 4:25
Ndipo zoona sukunama
Bwana Chimwendo akuti ndaima pano ku mmawa wa chimasanasana hahahahaha
Mai uyu amandiwaza sasuthika pa chithu
Nthawi yimaphunzitsA
Kodi uyu otupa mutuyi ndindani? 19:23
KZN kodi nchifukwa ninji sapasidwa mwai wolankhula?
Mama kaliati mumatiyimila 💪💪
Manganya wasongolatu pa danger chair😔
Mwayi urankhura pamwambo waukuru ngati umenewu bon kalindooo samaupedxa bwanji ...... akhodza kufusa mulungu.ambuye kodi kumwaliraku azingomwalira a utm okha .ku mcp simungatengeko atatu kapena 4.ambuye tabwerani mwatenge awa akudxudza malawi .ambuye tamutengeni uyu chonde kkkkkk
Kuchulutsa zayankhula mpaka kiiwala chipani 😂😂
Mwagwila mawu mayi
Kodi uyu otupa mutuyi ndindani?
Koma utm mmmm zodandaulitsa pepani kwambiri ndithu
Rest in peace
Mayi olimba mtima uyu si manganya ayi
Rest well sir Banda
Zilibwino
Sopano chakwerayo
Koma Mr Chikangawa akuwowozedwa kwambiri Mu Dziko muno
Zamanyazi. Kuowosedwa
Who's Mr Chikangawa? Koma aMalawi eh! Adakonza
CHAKWERA KUWOPA KUYANKHULA CHIFUKWA CHANKHOPE YAWUSATANA
Guys leave Chakwera alone please 😥😥
Good speach by Kaliati but long, making it boring.
Kulankhura konyengelera udindo mayiyu
Somehow.....
Totally agree 👍